Pondo music xclusive
Music industry pope s
THANKS GOES TO FLEMZ potinvesa Ku koma big up
UTHENGA WA CHISONI OIMBA OTCHEDWA Y THIN(yohane liwonde) wa mwalila atadwala Kwa nthawi yochepa iyeyu amaziwika ndi nyimbo zomwe zimayasa moto mu chambe music industry
Mwambo wa maliro pakadali pano sitidalandile ndondomeko
MY HE REST IN PEACE
ZIKOMO KWAMBILI A MANEB CHIFUKWA CHONDITHANDIZA NDI MTEZA OSINJASINJA KUPANDA INU SINDIKANADYA KWATHU FUTALI KOMASO NCHERE UJA UTI SINTHAπππππππ
Za bwino kumayamikila mfanayu Ali bho Ku music industry let encourage him to push up
Rest in peace boss we will always remember what you said to us
I miss you my brother
We are now open a new whatsap page so like us and enjoy the newly sound drop your numbers for add
Guys kd track ya mafanawa titled ndani waifila osaiwalanso likhubulu R***r Premzy ΒΆ nayesso WA khila nao wait it you will enjoy it [prod by Nosher p records]
# sindinaziko ndehttps://www.malawi-music.com/M/2199-man-chi/12324-sindinazikonde/18581-sindinazikonde-prod-w-twice-x-trap-genius-x-oneness-records
ELI Njuchi 's Gu Gu Gu Music Video is now 664K Views on YouTubeππ₯π₯
Waxy Kay Introducing a Freestyle program, On his Channel..
First Episode Out, Top Skill, Go Check It, Remember Subscribing So that You always Catch Up...π₯π₯
https://youtu.be/kOA4H2vH4rM
Pocheza Timaziwana Mzangayi Mgwa Greedy Popeza Ndinube Wana Size Yanga Agide.https://youtu.be/Coz3R5U0kjA
BIG ANNOUNCEMENT
Kuti timvane bwino zinthuzi ndiyankhure mu Chichewa
Munthune anthu ambiri mumati ndine mwana ndipo ndizoona kutengera ndi misinkhu ya ma artist ena omwe mumandifanizira nawo aku Malawi kuno komano ineyo Paine ndekha ngati Waxy Kay ndimaziona kuti ndadutsa mu nyengo zambiri zoti ma artists ena sanazidutsepo komanso sanazionepo zimene zimandipangitsa kukhala ndi experience about fame komanso kupanga realize nyengo zina zomwe ndinadutsa pa nthawi yomwe ndinangotchuka kumene
Ndivomeleze kuti ndinatchuka ndili mwana monga mene bambo anga anafotokozelera mu interview ya Makosana, ndivomelezeso kuti kupanga decision nthawi imene ndinangotchuka kumene muja kunkaoneka ngati kondivuta koma sizinali choncho and ndili nzoti ndikuuzeni about the decision making issue
Anthu ambiriso ena amandiblema kapena kumandipanga tease pa nkhani yanga ya maphunziro without knowing the reasons and some people think it was all about FAME but no I have better reasons and this time around I owe any of my fans an explanation.
Mu interview yanga ya ku Makosana ndinatchuramo zonkhunza ex girlfriend wanga emwe ndinayamba naye from zero kenako zinazokonekera koma sindinafotokoze kuti zinasokonekera munjira yotani and olakwa anali ndani
So the BIG announcement this hour ndiyokuti munthune ndikupanga album imene iti ifotokoze za moyo wanga onse omwe ndinayamba kupanga experience nditangotchuka kumene kufikira pano kotero nkhani zonse zomwe ndafotokoza m'mwambambo komanso mafunso onse omwe mumakhala nawo okhunza ineyo mayankho ake ali mu album imeneyi nkuthekaso si ine ndekha pali anthu enaso kapena ma artist ena anakumana ndi mavuto omwe ndinakumana nawo ine koma ngati alipo sanakumane ndi nyengo zomwe ndinadutsa ine uwu ukhale mwai wao okuti they should learn from my story but before the album ndiyamba ndikutulusa INTRO ya album yo imene itazakambe za nkhani zomwe zitakhale mu album mo....and the good news is The album Intro will be out this coming Sunday with a Video.
Thanks for reading the announcements brain inabwelera
https://youtu.be/w_nzYq4GAFQ
π¨π¨π¨New Music Alertπ¨π¨π¨
K Brice Ft Afron26
Kayisala Prod by S-One Beats + Stich Fray
π₯π₯π₯πππ
Coming out on 15th August on Made On Mondayπ₯
WITH Dj Joy Nathu π₯π₯
Help us to share the messageπ
StayBlessedππ
Y tryp audio producer in an entervie says that tryp has produce a old song titled polani moto you can download it this page
Ni66as never see me but it ain't hard to find me π»..... π²πΌπ
Y try p is with his audio producer binzo f
Click here to claim your Sponsored Listing.