Pastor Demba follows

Pastor Demba follows

You may also like

Kento
Kento

Preaching word of God

26/09/2022

Wina aliyese amene anatembelera dzina lako kuti uzikhala ndi moyo odwaladwala muchaka chino ndikulamula mudzina lambuye wanthu yesu kristu kuti back to sender.

26/09/2022

Landila chisomo mudzina lambuye wanthu yesu kristu Amen.

26/09/2022

Ndikunenela moyo wako kuti usiku uno matenda omwe ukudwala mulungu akukhudze ndikulandila machilitso mudzina lambuye wanthu yesu kristu Amen

15/09/2022

Ndikulamula matsoka,minyama, matsenga, matemberero, umphawi, ngozi,ifa zomwe anaziika padzina lako ndikusamutsa mudzina lambuye wanthu yesu kristu kuti zisatenge gawo ndi ulamuliro mwa iwe.

15/09/2022

Ukamakhala udziwe kuti sionse omwe amakufunila zabwino pamoyo wako.koma mulungu amapanga njira yokupambanitsa kuti oipayo achite manyazi (usaope ompha thupi koma opa ompha mzimu)

15/09/2022

USIKU walero mulungu akumane ndimoyo wako ndikusitha komaso kuchotsa chitozo pamoyo wako.mudzina la mbuye wanthu yesu kristu

12/09/2022

Ndingofuna tikumbutsane kuti ulendo wopita kumwamba sitidzatenga China chilichose monga tichitila ulendo wakudziko ayi,paulendo wakumwamba aliyense adzayenda ndi m'tima basi,Kodi ndichifukwa chiyani anthu Ife timalimbana ndi katundu wadziko?
YAKHO
Chifukwa chakuti tilibe maso akuzimu omwe angationetse pa chabwino komaso choipa.
PHUZIRO
Tiyeni titaye zonse zakudziko lapansi kuti paulendo opita kumwamba tisadzakhale otanganidwa AMBUYE AKHALE NANU POMWE MUKUZIYESA NTCHITO ZAKUDZIKO LAPANSI KUTI ZOPANDA PHINDU AMEN.

11/09/2022

Ndaona iweyo ukulila chifukwa choti wina sanakwanilitse malonjezano ake pamoyo wako, ndifuna ndikulimbitse m'tima kuti usalire ndizomwe muthu nzako analonjeza pa iwe. dziwa kuti munthu ndiye ongolonjeza koma sakwanitsa, itana mulungu wako thawi zonse poti akalonjeza ndiyekhayo amakwanitsa ukadziwa izi sudzalilira chifukwa chamuthu nzako (AMEN)

11/09/2022

Ngakhale wina atakuyesa kuti sindiwe ofunika kwa iyeyo, koma ngati iwe ndimulungu wako Pali ubale okwanila dziwa kuti zilibwino

11/09/2022

Mulungu amadziwa chomwe iwe ukufuna ndipo sangalole kuti phazi lako leteleleke,tangokhulupilila kuti zomwe wapepha mulungu wamva🙏

11/09/2022

Happy Sunday

08/09/2022

Ngati kuli moyo omwe ukuvuta ndi kukhazikika moyo wauzimu, chifukwa ndichomwe chimaoneka chovuta ku chasamala,,,,koma ndifuna ndikulimbikitse kuti ngati kuli chithu chomwe chifunika kusamala ndi moyo wauzimu ngati mwa iwe mulibe chauzimu funafuna yesu kuti agonele mwa iwe ndikulamula moyo wako.

07/09/2022

Pomwe tili mukhomaliro tiyeni timuyamike ambuye potifikitsa muthawi ino,tidziwa ena anadzuka ndimoyo koma pano muthawiso yomweyi achita ngozi,agonekedwa kuchipatala, pomwe Inu ndiine tili ndimoyo tangonena amen ngati muthawi imeneyi uli ndimoyo

05/09/2022

Pomwe wadzuka ndimoyo lero tangonena ambuye zikomo chifukwa chamoyo mwandipatsaso lero nditsogoleleni patsikuli amen

04/09/2022

Dear heavenly father lrejoice today at your word that's building my faith strong and influencing my actions . your word is my life, and the light that shows me how to walk on the path of victory prosperity, and success from day today in Jesus name amen.

04/09/2022

PEMPHERO
Atate ndikufunani tsopano mukalamulile moyo wanga,mukakhale nane pamavuto komaso pamtendele,ndikafuna kukhala wachimwemwe thawi zonse za moyo wanga,mukandilimbikitse ndikuphuzila komaso ndikukhulupilila mawu anu,kachulukitseni masiku achimwemwe pamoyo wanga"ndiyamika inu poti simudzandisiya ndekha pitilizani kugonjetsa ondizinga , pitilizani kundipatsa zosowa zanga, mudzina lambuye wanthu yesu kristu Amen

04/09/2022

Iwe amene ukuwelenga mulungu akwanilitse chosowa cha pamoyo wako

04/09/2022

Chipambano chili kuseli kwa khondo limbikani pomenya khondo yomwe mulinayo kuti mupambane.

04/09/2022

Matenda omwe ali pamwana wako ndikunenela mudzina lambuye wanthu yesu kristu kuti wachira Alleluyah

04/09/2022

Chibwana chomwe ukuchita siya chifukwa mulungu akuona usayese kuti wapambana pomwe ulipo panja mulungu adziwa zamun'tima

04/09/2022

Mau amene akuchoka pa mateyo 4vs18 ,,,,akutitsimikizila kuti pane Ife titsata yesu tidzakhala asodzi awanthu ,,, chifukwa yesu atakumana ndi Petro komaso Andrea yesu anati kwa iwo nditsateni,,,, ndikufuna kunena chiyani pa Inu okondedwa yesu akati timutsate tiyeni okondedwa mwambuye timutsate taonani kuti tikasiya ntchito zanthu zonyasa zomwe timachita ndikumtsata iye mulungu adzaika chokoma mwa Ife tiyeni tidziwitse azathu zabwino zomwe mulungu wachita kuti nawoso atsate yesu ,,,,, yambani Inu lero kuitanila azanu kwa yesu,,,, ambuye akudalitseni pokhala inu asodzi awanthu

29/08/2022

Mwadzuka bwanji okondedwa mwambuye konse komwe muli?

25/08/2022

Ulendo wina ulionse umayamba ndikuponya phazi limodzi kape giya imodzi ukaona kuti ukutheka ndipomwe umaonjeza phazi lina kapena giya ina apatu timati ulendo wathu ulibwino,,,koma nanga pomwe tikuyenda tikudziwa komwe ulendo wathu ukathele? dziwani kuti ulendo opanda cholinga umakhala ngati muthu amene mutu wake sumagwila ,,,lero dzifuseni kuti Kodi tsiku lanu laulendo mukadzanyamuka mudzafikila kuti GAHENA/PALADAISO? tiyeni tipange chisakho chokhala ndimalo ofikilako pathawi ya ulendo wathu ambuye akudalitseni.

25/08/2022

Pomwe ena akuyesa ntchito yako kwa iwo silibwino, ndipomwe iwe ulimbike kugwila kuti adziwe kuti mulungu sachititsa manyazi olimbika, chaka chino utola chikwama chako chamadalitso tangolimbika kufulila kwa mulungu.

23/08/2022

Morning

19/08/2022

Ndikudziwa kuti watopa ndikupemphera mwina chomwe wakhala ukupepha koma mwina sukuyakhidwa ndifuna ndikulimbitse m'tima kuti mulungu akapeleka chako sichidzasowa chidzakhala chodekha komaso choopa mulungu,, chomwe mulinachocho musachinyoze mulungu alinacho cholinga chako sichimasowa chako sichiopsa chako chimakonda. Amen

18/08/2022

God loves everyone poor and rich

18/08/2022

Usadandaule pomwe nyengo zako sizikuyenda bwino dziwa kuti mulungu ndipomwe amafuna aone kukhulupilika kwako ,,,, yemwe akuyesa iwe opanda ntchito ndipomwe mulungu adzakutola ndipupuputa matope onse ndikupanga kukhala chida chake chodalilika ndipomwe mamuna unja ukufunayi adzapezeke,or nkazi unja ukufunayi mulungu adzakupatsa khala odikila.

Want your business to be the top-listed Clothing Store in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address

Area 7 Machinjiri
Blantyre
0981144698

Opening Hours

07:30 - 02:00
Other Baby Goods/Kids Goods in Blantyre (show all)
Baby diapers shop Baby diapers shop
Machinjili, Khama
Blantyre, MACHINJILI,KHAMA

we sell good quality baby diapers and wipes at an affordable price

Abmakay mw Abmakay mw
Blantyre, 817117

Taka mbulu Taka mbulu
Chilek Airport
Blantyre, RICHPOP

Emiss baby shop Emiss baby shop
We Are In Blantyre Limbe Mahawa Arcade Opposite Nbs Bank Shop Number 26b Ground
Blantyre, BOX1212BT

Trinnie Baby's Botique Trinnie Baby's Botique
Blantyre

Your one stop shop for your kids goods

HELLO BABY HELLO BABY
Kameza And Ndirande
Blantyre

Peek-a-Boo Baby Shop Peek-a-Boo Baby Shop
Ginnery Mall
Blantyre

Welcome to our charming baby boutique, a haven for all things adorable and essential for your kids.

mommy.andme mommy.andme
Victoria Avenue & Independence, Https://maps. App. Goo. Gl/icGSBrCoDrzYunEc 7
Blantyre, 265

All things baby, mommy and Maternity

hagos_kids hagos_kids
Mall Of Africa, First Floor, Shop# B9, Ginnery Corner, Mw
Blantyre

stockist of quality children wear,essentials,furniture,decor, travel systems,toys and gifts.

Classic diapers supplies Classic diapers supplies
Limbe
Blantyre

New stock of baby brackets!!!!!

Twins Baby Bedding's and Accessories Twins Baby Bedding's and Accessories
Blantyre
Blantyre, 265

we are professionals