MY Hijjab MY Identity

Men and women Islamic attires

06/11/2023

We appreciate for your presence
Ngati simudalowebe ku Whatsapp group kwathu Siyani number yanu tikupangeni add, anzanu akutchena katundu wabwino pamtengo okambika uku ,
Bwelani Bwelani zabwino zisamakuphonyeni,
Siife opambana kuposa ena onse omwe mukuwaziwawo koma ndife Odalilika 💯, achilungamo🤝 komanso a Dongosolo 👏
My Hijjab My Identity since 2018 Simuzakhumudwa Nafe , Try us Today

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 01/11/2023

Inuyo mutchene pamtengo okambika , New Model , Best of 2023🔉🔉🔉🔉 Ma 🗝️ otchenela Ali ndi inu , mtengo pang'ono malingana ndi kuvuta Kwa pa ground,
Ngati simudalowe ku wap siyani number yanu tikupangeni add ku group
My Hijjab My Identity since 2018 we are Here for You 🤗
Siife opambana kuposa ena onse omwe mukuwaziwawo koma ndife odalilika komanso a dongosolo, ngati simudalowebe ku Whatsapp group siyani number yanu tikupangeni add

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 25/10/2023

My Hijjab My Identity Kuyambila 2018 simuzakhumudwa Nafe , nthawi zonse timakubweletselani Best Designs with Best materials , Mukhonza kunena kuti siife opambana kuposa ena onse omwe mukuwaziwawo inde , koma ndife odalilika komanso a dongosolo afunseni Aneba, Ngati simudaguleko ku My Hijjab My Identity Bwelani muzagule mtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, Timalola kupelekanso kawili, Ngati simudalowebe ku Whatsapp group kwathu Siyani number yanu tikupangeni add ku Group
Kutchena Kuli mmanja mwanu a Customer
🍿🍿🍿New collections for Adults and Kids

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 13/10/2023

New Collection 2023 Kutchena pamtengo okambika kuja kwaphwekelaaatu♨️♨️🔉

Mukawaona anzanu aja atachena nkumakubisilani komwe agula Ziwani kuti ku Malo Kwake ndi ku My Hijjab My Identity.
Mukasankha My Hijjab My Identity nde kuti mwasankha shop yanu mbambande imene muzitchena pamtengo wabwino malingana ndi kuvuta Kwa Pa ground 😔

Ngati simudalowebe ku group tangosiyani number yanu tikupangeni add ku group, titumizileni Message ku inbox 📥 pa page pompano tikupangeni add, zabwino zisamakudutseni.

Kutchena kuli mmanja mwanu,
My Hijjab My Identity since 2018 simuzakhumudwa nafe🔊🤗

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 10/10/2023

My Hijjab My Identity Kuyambila 2018 simuzakhumudwa Nafe , nthawi zonse timakubweletselani Best Designs with Best materials , Ngati simudaguleko ku My Hijjab My Identity Bwelani muzagule mtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, Timalola kupelekanso kawili, Ngati simudalowebe ku Whatsapp group kwathu Siyani number yanu tikupangeni add ku Group
Kutchena Kuli mmanja mwanu a Customer

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 05/10/2023

Mwana Atchenetu apa mtengo pang'ono kupeleka kawili , Ngati simudalowebe ku Whatsapp group kwathu musachedwe siyani number yanu mukamve kamtengo koganizilana malingana ndikuvuta pa ground
My Hijjab My Identity kutchena kuli mmanja mwanu

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 02/10/2023

Ka matching outfits aka , inu ndi a Hubby aja zanu phee same colors waku Jumuah, waku out ndi kamtengo kosaboola mnthumba, tipedzeni ku wap group zisakudutseni, ngati simudajoine siyani number yanu tikupangeni add ku group,
My Hijjab My Identity since 2018 simuzakhumudwa Nafe

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 26/09/2023

Another 2023 New Collection, Mtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, pamene Madam akutchena inunso mutchene , Nanu madamu pamene Dad akukutchenetsani atutumutseni ndi ka surprise ka 2023 New Collection.
Ngati simudajoine ku wap tipedzeni posiya number yanu mu comment box tikupangeni add, kapena titumizileni message ku page kwathu mupangidwa add , muzimvele nokha kamtengo kosaboola mnthumba ku inbox 📥

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 18/09/2023

2023 New Collection, Mtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, pamene Madam akutchena inunso mutchene , Nanu madamu pamene Dad akukutchenetsani atutumutseni ndi ka surprise ka 2023 New Collection.
Ngati simudajoine ku wap tipedzeni posiya number yanu mu comment box tikupangeni add, kapena titumizileni message ku page kwathu mupangidwa add , muzimvele nokha kamtengo kosaboola mnthumba ku inbox 📥

Photos from Scarf House Malawi's post 15/09/2023
Photos from MY Hijjab MY Identity's post 18/07/2023

Inuyo mutchene pamtengo okambika , New Model , Best of 2023🔉🔉🔉🔉 Ma 🗝️ otchenela Ali ndi inu , mtengo pang'ono malingana ndi kuvuta Kwa pa ground,
Ngati simudalowe ku wap siyani number yanu tikupangeni add ku group
My Hijjab My Identity since 2018 we are Here for You 🤗

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 16/06/2023

Ma skirt aja afika Ku Malawi tilankhuleni Mupedze yanu pamtengo wabwino, skirt yopanda mistake yotchenetsa osaonetsa Miyendo kapena kuDinda,
Kutchena kunzikiti bwino bwino🎉
Ngati Muli serious tipenzeni ku inbox Mupedze yanu Skirt Mbambande💥
Wap +265995292925
+201120454008

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 15/06/2023

Tabwelani kuno muzatchene pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, Tipedzeni ku Whatsapp group yathu posiya number yanu ku comment box tikupangeni add mukatenge nawo katundu pamtengo wabwino,

My Hijjab My Identity since 2018 we are Here for you🎉

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 21/05/2023

Gulani skirt Mbambande kwaife ndipo simuzakhumudwa Anzanu akutchena ndithu , Ma skirt opanda mistake kuvala ku Nzikiti bwino bwino.
Tipedzeni ku Whatsapp group yathu kuti Mupedze yanu pamtengo okambika,

https://chat.whatsapp.com/Ce2rXiGcbXN9cU1yde28o8

Ngati simudalowe ku group siyani number yanu tikupangeni add.

My Hijjab My Identity Kutchena kuli mmanja mwanu

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 19/05/2023

🛑🚨🛑Mukasankha My Hijjab My Identity ndiye kuti mwasankha kutchena mbambande, pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground , Ngati Simudakhale nafebe ku Whatsapp group Lowani ndi link iyi
👇
https://chat.whatsapp.com/DcRDyp9SMv1AlhsS4h5g92

Kapena siyani number yanu tikupangeni add ku group

Kutchena Kwa phweka , ndipo phukusi lotchenela mukusungila ndinuyo🛍️🎁

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 28/04/2023

🛑🚨🛑Mukasankha My Hijjab My Identity ndiye kuti mwasankha kutchena mbambande, pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground , Ngati Simudakhale nafebe ku Whatsapp group Lowani ndi link iyi
👇
https://chat.whatsapp.com/Ce2rXiGcbXN9cU1yde28o8

Kapena siyani number yanu tikupangeni add ku group

Kutchena Kwa phweka , phukusi lakutchena mukusunga ndinuyo🛍️🎁

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 25/04/2023

After Eid tabwelanso ndi Ma design apamwamba, Kwa onse amene adapanga oda kuti atchene pa Eid Tiyamikile pa support yanu komanso kuti mudalandila katundu wanu ndendende amene mudaitanitsa ,
Ife kwathu ndikuthandizani kupedza katundu wabwino pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground.

Ngati simudalowe ku Whatsapp group kwathu musachedwe anzanu akupedza katundu wapamwamba kuchokela Kwa ife , siyani number yanu kuti tikupangeni add ku group

22/04/2023

*EID MUBARAK TO ALL OUR CUSTOMERS TIKUKUFUNILANI ZABWINO ZONSE PACHISANGALALO CHA EID , PAJA KUTCHENA KULI MMANJA MWANU MUTCHENE BWINO 🥳🥳*
*TIMAKUNYADILANI POKHALA NAFE NTHAWI ZONSE*

22/03/2023

✨Ramadhan Mubarak🌙
Okondedwa ma customer athu kuno ife a tikukufunilani Ramadhan yopambana , Allah akufewetseleni ndikutifewetselanso ife kuti Ramadhan wathu akhale opambana ndikutinso akatilipile zabwino zambili mmoyo umene uli nkuza.
Tiyeni tiisale Swaumu imeneyi ngati ndiyomaliza mmoyo mwathu sitikuziwa ngati tizakhalenso ndi mwayi ozasalanso Chaka chinacho Zabwino zonse
🥳Ramadhan Mubarak 🥳

13/03/2023

9 Days Until Ramadhan Bwelani Ku My Hijjab My Identity Muzasankhe katundu ozatchena pa Eid pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, Lowani ku group pogwilitsa ntchito Link 👇

https://chat.whatsapp.com/DcRDyp9SMv1AlhsS4h5g92

11/03/2023

aCustomer Mukuchedwatu anzanu apedza kale Zozatchena pa Eid pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, tipezeni ku Whatsapp group yathu musankhe katundu wakumtima kwanu 👇
https://chat.whatsapp.com/DcRDyp9SMv1AlhsS4h5g92

We are always available for you since 2018 simuzakhumudwa nafe

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 04/03/2023

Once mwasankha My Hijjab My Identity nde kuti mwasankha kutchena katundu wabwino pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground

My Hijjab My Identity
Since 2018 We are Here for You
👏👏 Few days until Ramadhan
👏👏Few days until Eid
Choose us simuzakhumudwa

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 25/02/2023

Ramadhan idakali pafupi Eid nso idakali pafupi , musakhale ndi nkhawa kuti a bundle of joy aja azatchenanji🤔
Ife tili pano kukuthandizilani kuti atchene pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground,

Agulileni nthawi yabwino

My Hijjab My Identity since 2018 Simuzakhumudwa nafe.

Whatsapp group 👇

https://chat.whatsapp.com/DcRDyp9SMv1AlhsS4h5g92

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 24/02/2023

Anzanu aja ngati simudawaonetsebe komwe angapedze katundu otchena pa Eid mukuwalakwila😛 Aitaneni azasankhe nawo pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, Ramadhan is Coming, Eid is coming

Lawilani posankha katundu wakumtima kwanu kuti akupedzeninso nthawi yabwino, Tiyeseni ife a My Hijjab My Identity simuzakhumudwa anzanu akutchena ndithu.

Ngati simudalowe ku Whatsapp group yathu siyani number yanu tikupangeni add kapena titumizileni message ku inbox 📥

Since 2018 Kutchena kuli mmanja mwanu.

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 20/02/2023

Pamene Ramadhan ikuyandikila, Eid nso yayandikila Musakhale ndi nkhawa kuti zotchena pa Eid mukazipedza kuti pamtengo okambika malingana ndi kuvuta Kwa pa ground, ife a My Hijjab My Identity tili pano kufuna kukutchenetsani pamtengo Wabwino,
Tipezeni ku Whatsapp group musankhe katundu wakumtima kwanu pamtengo Wabwino.
Ngati simudalowe ku Whatsapp group yathu siyani number yanu tikupangeni add, kapena titumizileni message ku inbox 📥 .

My Hijjab My Identity Kutchena kuli mmanja mwanu 👏⭐⭐

Photos from MY Hijjab MY Identity's post 15/02/2023

Phee pa Eid Inu ndi a Bundle of Joy anu aja pamtengo wezi

Kulawila nkwabwino kusiyana Ndi kuchedwa

Ndi My Hijjab My Identity yokha imene ingakupaseni mtengo wabwino malingana ndi kuvuta Kwa pa Ground

Ramadhan is coming make your purchase early

Tipezeni uku👇

https://chat.whatsapp.com/DcRDyp9SMv1AlhsS4h5g92

Olo siyani number yanu tikupangeni add ku group ngati simudalowe.

11/02/2023

*AITANENI ANZANU AJA, ANEBA AJA AUZENI KUTI KUTCHENA KULI KU MY HIJJAB MY IDENTITY 🧕🏽PA MTENGO OKAMBIKA, MTENGO OGANIZILANA MALINGANA NDIKUVUTA KWA PA GROUND, EID IS AROUND THE CORNER MAKE YOUR ORDER EARLY*

*AGAWILENI LINK ATCHENE NAWONSO* 👇🏾
https://chat.whatsapp.com/DcRDyp9SMv1AlhsS4h5g92

Want your business to be the top-listed Clothing Store in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

🧿🧿

Category

Telephone

Website

Address

Blantyre
MALAWI
Other Clothing Stores in Blantyre (show all)
Global Fashions Malawi Global Fashions Malawi
Platinum Mall, Limbe
Blantyre

We specialize and women clothing and casual clothes. Platinum Mall, 1st Floor, Room No 48 near Jusab, Limbe. +265 (0) 880 486 857 or +265 (0) 996 705 909

Amshop Malawi Amshop Malawi
Limbe
Blantyre

The home of modern outfits for both men and women

Pre-loved Pre-loved
Blantyre City
Blantyre

We sell the best preloved clothes for your bundles of joy

DAPP Retail SHOP at BUS STAND DAPP Retail SHOP at BUS STAND
Dapp Blantyre 1shop P. O. Box 2732 Blantyre
Blantyre

Dapp retail shop is the home of second hand clothes and shoes. We sell different categories of clothes and shoes at a very affordable price.. and our prices do go down every day.....

ishmejnr22 ishmejnr22
Blantyre

We deal with football team jerseys and any sports materials

NEAT Closet NEAT Closet
Blantyre, 0000

Uptown Kaunjika Plug Uptown Kaunjika Plug
Blantyre
Blantyre

Your one-stop online Kaunjika shop. We send anywhere. Talk to us. We deliver

Khama Khama
Malawi University Of Business And Applied Sciences
Blantyre

Dreaming big, working hard, and turning ambitions into achievements Gen-Y streamlined 🇲🇼

Rare Fashion & Accessories Rare Fashion & Accessories
Chirimba
Blantyre

Rare Fashion and Accessories is a Both Online and Physical Unisex Fashion and Accessories Shop. The P

TYRAH DREOH TYRAH DREOH
P. O. Box 30644 Blantyre
Blantyre, 312216

Munthu woganiza bwinobwino 1. Uzintchena 2. Uzisamba 3. Uzinunkhira

Guava.MW Guava.MW
Naperi Road
Blantyre

Thrift store for second hand clothes and Apparel. We also help find specific items if needed. Every Wednesday 3pm we post on the WhatsApp group then Instagram and Facebook after.

RIFA Fashions RIFA Fashions
AT TONDOLE STAGE, NAMIYANGO
Blantyre

Wide range of quality overalls at the most competitive prices. Request a quote. Come to us for all y