Mama's Food Market

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mama's Food Market, Restaurant, Green corner along Chikwawa Road, after Stella Maris school, Blantyre.

09/10/2023

Kwa amene mumapita ku Zambia kukatenga ma sausage, tati tikudziwitseni kuti ife a Mama's tikupanga ma sausage exactly a Zambia koma okoma kwambiri moti mudzasiyanitsanso nokha mukalawa.

Order ikuyambila ma sausage 50 kukwela mmwamba.

Ngati mukufuna kudziwa zambiri tiyankhuleni

14/09/2023

Zipangizo zopangila ma sausage komanso ma cake zikupezeka pa Mama's Super Market pa Green corner. Call or whatsapp this number +265998519196

Fino whip 1 kg 11,500
Raisins 1 kg 8,000
Cocoa powder 1 kg 17, 000
Food colours 2,700
Food flavor 3,000
Icing sugar 500g 2,600
BBQ beef 21,000
Master club 8,500
Loliie 18,000
Six gun 2,500
Sausage Caisings 28/32 19,000 per kg
Chocolate 100g 3,000

The list continues

19/07/2023

Suppliers needed

We are looking for trusted suppliers of quality pork meat, broiler chicken, fresh fish, and goat meat.

Send us a message on whatsapp if you're interested.

Thank you

Photos from Mama's Food Market's post 01/07/2023

Woza weekend πŸ˜‹πŸ˜‹πŸ˜‹πŸ·πŸΊπŸ₯˜πŸ₯˜πŸ₯£πŸ₯“πŸŒ­πŸ•

Zikopa za ng'ombe za tsabola okwana bwino
Mutu wa Mbuzi Mbuzi onona bwino
Mang'ina a ngombe opsya bwino
Mang'ina a Ganda nkati
Local chicken
Nyama zowotchanso konkuno ziliko
Zakumwa za mitundu yonse ziliponso
Nyimbo zikulila kwinaku mukucheza
Zonse malo amodzi
's

Photos from Mama's Food Market's post 27/06/2023

Tiyeni zatheka

23/06/2023

Mama's pizza is backπŸ˜ŠπŸ˜‹πŸ˜‹πŸ˜‹

Photos from Mama's Food Market's post 21/06/2023

Let's go tikadye... ntchito osachita kuyikakamila ngati yakwanuπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚ kwacha nde ndameneyu wadayu🀣🀣🀣 koma ku Mama's mitengo ndiyomweija

Photos from Mama's Food Market's post 20/06/2023

Simunachedwe tiyeniπŸ˜‹πŸ˜‹πŸ˜‹

Photos from Mama's Food Market's post 17/06/2023

TiyeniπŸ˜‹πŸ˜‹πŸ˜‹ zatheka

16/06/2023

Osayiwala kugulilatu ndiwo kunyumba pa Mama's nkumakapanga bwino zanu zija

Photos from Mama's Food Market's post 16/06/2023

If you're a meatball and sausage lover, then Mama's is the place you can find the best... tisazichemelele tisiye ena anene za makomedwe ake. Mukhonzanso kudzagula kukaphika nokha kunyumba. Tati sausage not soyaseji😁😁😁

Photos from Mama's Food Market's post 15/06/2023

Lunch is ready... pliz bring a friend coz sharing the best food is caring...

14/06/2023

Amene mumakonda Goat soup aja🍲 watheka, nyamukani asanathe...πŸ˜‹πŸ˜‹πŸ˜‹

Photos from Mama's Food Market's post 14/06/2023

Lunch is read at Mama's... bring a friend. Ndalama yochepa chakudya chokwanila komanso chophikidwa bwino

Photos from Mama's Food Market's post 13/06/2023

Pure local.... yofewa bwino kuposa ujeni.... yonunkhila bwino tikuti. Mukudziwa inuyo ku Mama's kumapezeka nyama yodyetsedwa ndi mlimi osati zonenepa ndi ma yekisenizi🀭🀭 Mama's ndi mankhwala a banja

Photos from Mama's Food Market's post 13/06/2023

Oyimba anati mu bokosi mulibe Mama's, mu bokosi mulibe kuhahaza. Kodi tizifinyika🀩🀩

Finyikani nokha ngati kholigeti😁😁 chips ichi mukachipeza ku Green corner kokha ku Mama's...

Photos from Mama's Food Market's post 13/06/2023

Lunch is ready at Mama's....

Takulandilani.

12/06/2023

Gilibati wofewa πŸ˜‹πŸ˜‹πŸ˜‹ opanda uchimo uyuπŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€

Photos from Mama's Food Market's post 12/06/2023

Ikungowona kuvuta ndi forex koma ife nde kuyesesa tikuyesesa kuti anthu a ku Blantyre azidya zabwino koma zotsika ntengo sure😁😁😁 inu kwanu mwadyela chani?πŸ˜‚

Photos from Mama's Food Market's post 11/06/2023

Lero pa Mama's tamaliza motele.... mumatha kucheza ma dona inuyo... Mubwelenso izizi tizipanga every weekend mukuwona bwa???πŸ˜„πŸ˜„

11/06/2023

Akunena za bread wa Mama's osati winawake oponda ndi zijombojombo ujatuπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Zalaweni mutiwuze ndi inuyo

Photos from Mama's Food Market's post 11/06/2023

Ya mam'mawa ya mutu wa mbuzi ndi masamba osakaniza aja yapsya bwelani... mukachedwa mupeza amalizamo anthu sakusewela awa... ndi mmene munalili dzulo muja ndi thiyi wa mbatata sikugwilatu ankolo🀣🀣🀣

11/06/2023

Kamlopa inuyo mumakwana kwabasi... lero tizakuwonjezelani ndiwo zambiri mukabwelanso ndi anzanuπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒ

11/06/2023

Bwana Henry Mazco Bandah akuti Marketing ili bwino... Nde ife ngati a Mama's takambilana kuti bwanawa lero azadye mutu wa Mbuzi ndipo adzamwele nsuzi asadzalipile awine ndi iwowoπŸ˜›πŸ˜›πŸ˜›πŸ₯£πŸ₯£

11/06/2023

Happy birthday our two beautiful customers.... we at mama's are celebrating with you on your special day ❀️ and we are more than ready to host you again today.

Ena nonse mukuyitanidwa ku befide ya azimayi osamba lero pa Mama's 🀩

Zakumwa muzikagula nokha koma eti😁

Nanunso mukafuna kudzapangila phwando lanu pa Mama's bwerani. Just buy food and drinks from us, and you will have a DJ and sound for free...

Photos from Mama's Food Market's post 11/06/2023

Good morning Malawi. Good Morning Blantyre.... kokapeza breakfast mukukudziwa kale.... bread othila zonse zofunika osati kungokandakanda fulawa ndi madzi nkupondaponda ndi zijombojombo πŸ˜†πŸ˜†

Komanso Man City yatiwonjeza tisanameyi... Naye Lukaku siza soccer aaaaπŸ’”πŸ€¦

10/06/2023

Try Mama's fried chicken and chips.... mpamene mudzadziwe kuti kwinaku timangofela lebulo😁😁😁 Nde akati anene ntengo eeee sorry kwabasi. Mama's ka ntengo kokwela ndi mwana yemweπŸ˜πŸ˜πŸ˜‹πŸ˜‹

10/06/2023

Amene mukubwera ku Club XL kudzavina, musadele nkhawa za njala. Mama's ili cha pompo patsogolo pakepo....

Want your restaurant to be the top-listed Restaurant in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

Happy birthday our two beautiful customers.... we at mama's are celebrating with you on your special day ❀️ and we are m...

Category

Website

Address

Green Corner Along Chikwawa Road, After Stella Maris School
Blantyre

Opening Hours

Monday 07:00 - 21:00
Tuesday 07:00 - 21:00
Wednesday 07:00 - 21:00
Thursday 07:00 - 21:00
Friday 07:00 - 21:00
Saturday 07:00 - 21:00
Sunday 09:00 - 17:00
Other Restaurants in Blantyre (show all)
Bob vay 509 Bob vay 509
Blantyre

Best rap kreyol

Food Masters investment Food Masters investment
Manase
Blantyre

Food masters investment is a group of people specialized in food science and recipe amendment we als

Old House Bistro Old House Bistro
Along Victoria Avenue Next To PSI Regional Offices
Blantyre, 265

Blantyre's eatery offering tastefully-cooked local lunches, sizzling grills and a modest bar setting.

Bizzo'S Kitchen Bizzo'S Kitchen
Blantyre

Bizzos kitchen is a catering company,specializing in home made local dishes,we cater for any kind of event,be it weddings,birthday parties,engagement luncheons, etc.

Mbombwe Lodges Mbombwe Lodges
Cape Maclear/Mangochi, , Kanjedza And Namiyango In Blantyre
Blantyre

We offer Accommodation, Bar, Restaurant and Conference Center. Experience comfort like never before

Odala shops Odala shops
Machinjiri
Blantyre, 198420

we sell food like rice,chips ,sima at cheapest price.

Pias master Pias master
Bazare Sukuru
Blantyre

LeRoca House LeRoca House
LeRoCa House, Nyambadwe, Brereton
Blantyre

Eat-Meet-Drink

Jaffu foods Jaffu foods
Limbe
Blantyre

We offer catering services at birthday parties, engagement parties, weddings, and any other occations

MAYBE MARS CAFE MAYBE MARS CAFE
Along Mandala Road
Blantyre

Great-tasting gourmet coffee & meals, Great place to hangout.

Redd Ginger Restaurant Redd Ginger Restaurant
Blantyre, 265

This amazing rooftop restaurant is within Mall of Africa in Blantyre where there's Chipuku Stores is

La Manna Caterers La Manna Caterers
Blantyre, 5597

La Manna Caterers was established since 2017,with the aim of providing excellent healthy food to eve