Tiphuzisane za umfumu wa mulungu

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Tiphuzisane za umfumu wa mulungu, Fitness Model, Bangwe, Blantyre.

01/12/2021

Hello athu a mulungu

08/09/2021

Kd ubatz ndichan

16/07/2021

Hello ath amulungu

Profile pictures 25/04/2021

``` NDINAKHUMUDWA NDITAPITA KUCHIPATARA
Mlembi wa nkhani yi ndi "Aubrey That'sDhe Boss"
Lero on Sunday ndinapita kuchipatala kokaona nzanga yemwe adagonekedwa kuchipatalako, nditangolowa nchipatalacho, ndinalowera khomo lina lomwe kumachirira azimayi.
Ndikudutsa ndinao azimayi atatu komanso atsikana angapo achichepere omwe amatengeredwa ku room ina ya operation, anthuwatu adali ndimavuto oti kubereke sadakakhala ndi moyo ndipo amangoyenera kukawapanga operation ngati njira imodzi yofuna kupulumutsa miyoyo yao komanso ana akhandao, ndinari okhumudwa ndithu mkati mwamoyo wanga ndipo ndidangoima pachitsekopo ndikuyamba kupembedzere mkati mwa mtima wanga k*ti Mulungu awachitire chifundo anthuwa.
Ndinakhala pafupi ndichitsekopo mpaka kwa 30 minutes uku ndikupembedzera mkati mwa mtima wanga. Pambuyo pake ndinaona namwino atatsegula chitseko ak*tuluka koma okhumudwa, ndipo chovala chake chinali magazi okhaokha, nditawafusa za munthu wamayi yemwe analowa koyambirira k*ti operation yake yayenda bwanji, anandiyakha k*ti "sizinayende ndipo mayi ndi mwana onse amwalira, nditawafusaso zatsikana amene ndinamuonaoyoso anandiuzaso chimodzimodzi.
Apa achibale kunali kulira konvetsa chisoni muja poluza munthu wao komaso mphatso yao ya mwana😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
M'bale izitu kunjaku zikuchitika ndipo sinkhambakamwa ndipo enanu ndinu mboni mwaonapo ngakhaleso kunva kumene.
Kodi iweo umazitenga obambana kamba koti unabadwa wa moyo? Kapena umaona ngati mayi ako anali wamphavu k*ti izi zidawachitikira enawa iweo ndi mayi ako sizidakakuchitikirani? Nanga taona lero, mayi ako udawapangirapo chani pantchito yotamandikai imene adakusunga kwa myezi 9 nchiberekero chao? Sikudziwa k*ti adalimba mtima ndipo sadaope chirichonse ngakhale operation?
Nanga taona ma post ngati awa amene ngakhale Share sumapanga, kodi Mulungu anganve nawe bwanji? Ngakhale Kumuyamika kumene umakanika?
Lero lino muyamike Mulungu chifukwa adakukondera iweo nkubadwa wa moyo pamene ana Ake ena akumwalira.
Mukhale ndi Sunday yabwino lero pamene mukuwagawiraso anzanu ena uthengau k*ti akatheso kudalitsika, m***a kupezaso nkhani zolimbikitsa moyo wanu wauzimu pa WhatsApp group
+265994917253
```
Facebook group
https://facebook.com/groups/150396872450702
Story written by *"Aubrey That'sDhe Boss"*

Profile pictures 27/03/2021

*Lilongwe*🇲🇼
I WANT TO YOU GUYS

ZOTI MULI CHIOPSWEZO MU ANTHU SAKUSAMALA BOLA CARD AKHARE NAYO

ZATSIKIMIZIKA k*ti ambiri sakusamala za moyo wina uli nkudza koma wapansipano. Katemera ak*ti siokakamiza koma dziwani k*ti ndiokakamiza chifukwa yemwe akharadi osabaitsa yemweyo azazunzika, sazaloledwa kugula ndi kugulitsa kapena kulowa ndi k*tuluka maiko akunja:
ena akubaitsa chifukwa ndiama business amatuluka kunja koma sakudziwa k*ti Covid 19 mukaonkhetsa mu numerous number (roman) ama tulutsa 685 mukachotsa -19 = ndi 666 ndiye apanga virus kuzaipangila Astrazeneca mu phamvu ya chilombo k*tenga vaccine wamphavu ya 666 nkumaika mmatupi mwanu tsoka ilo chidindo chapankono chija ndichomwecho musaganize chidzakhara cholemba k*t 666 vaccine ndi sigh yoti mwaikidwa mphavu ya Satan k*t ndinu ake chikumbu ntima chakupemphera simukhara nacho ndipo simulapaso, mu vaccine muli mphavu ya satanic ndipo ikugwitsani ntchito po pembedza fano la chilombo popeza obaitsayo alikale mu system yake ya 666.


Kubaitsa kusabaitsa kulibe chitetezo chilichonse chifukwa vaccine sachilitsa covid19 kapena k*teteza ku covid ayi akukudindani sigh ya 666
Amene mwamvera wailesi ak*t mukabatsitsa musasiye kukharabe motalikana komaso kusamba mmanja ndi sopo osasiyaso kuvala mask chifukwa ak*ti muthu obaisayo sik*t sazadwalaso covid19 chifukwa choti wabaitsa. Ayi adzadwala ndithu koma kunama kwake ati sangadwale ngat ena amene sanabaitse aaa this is nonsense vaccine sateteza covid mwachitsanzo Chakwela ku Tanzania kumaliro a magufuli anavalaso mask chonsecho ak*t abaitsa astrazeneca wa covid 19 koma mask sakuchoka kukamwa.
Guys iyi ndi satanic mukulembetsa mu 666 kuphatikiza apo ngat simufa simuzabelekaso 🏽‍cholinga ndichoti akufuna anthu achepe kaye mdziko k*ti akamati akufuna apange Dziko limodzi chipembedzo chimodzi anthu anthu akhale ochepelako k*ti anthe kudyetsela bwino maiko ambiri akayamba kulamulilidwa..
vaccine yomweyo maiko oyambilira 13 anamuimitsa potengera k*ti akumaumitsa magazi ku Israel anthu ambiri akukana kulandila katemera chifukwa akudziwa bwino zotsatila zake nde boma la Israel laletsa yemwe sanalandile chizindikilo ichi kuyenda , kugula ndi kugulitsa nde yemwe akufuna chiphaso chadziko lapamsi kukhara mfulu akabaitse tsopano koma yemwe akufuna chipulumutso anzunzike pokana chizindikilo ichi cha chilomnochi or ifani ndinjara kunalembedwa paizi simugula or kugulitsa ngat simubaitsa kukhara ndi chiphaso ♀️share kuma group anzanu aoneso izi

*📝NEWS UPDATE*

24/10/2020

Muli bwanji madzulo ano athu a mulungu mwazisomo za ambuye wathu

Profile pictures 21/08/2020

OKONDEDWA VUTO LOMWE NDALIPEZA NDILOTI AMBIRI TIKUPUSA NDI MPHATSO ZOMWE TIDAPATSIDWA NDI MULUNGU,AMENN

Koma dziwani mphatso za maimbidwe,ulaliki,uneneri,ubusa,uphunzitsi,utumiki,ulangizi ndi mphatso zonse timaziona zimatha kugwira ntchito ngakhaletu mwa munthu osalandira Yesu,Amenn

Ndichifukwa chake mukamupeza wa PRAISE TEAM Ali hule komanso chidakwa,mukamupeza mneneri ngakhale mbusa Ali wakuba ndi wabodza chonsecho ak*tumikirabe za Ambuye.Mwachidule mphatso simathotholedwa mwa munthu ngakhale Ali mu ucimo.Izi zakhala zikupangitsa ochuluka kukanika kubvomereza k*ti ndi ochimwa.Amen

Kotero landirani Yesu pamene mukugwiritsa mphatso zomwe Mulungu adakupatsani.Amen

28/06/2020

Yehova ndinu linga lathu tikukuyamikani ndik*thokoza popeza ndinu woyeneradi kulandila ulemu zikomo chifukwa cha Chisomo chanu k*tiloraso kufika tsikula lero .
Ame

06/06/2020

Pamene umanganiza zomutaya mulungu chifukwa cha mavuto omwe timakumana nawo ndipamene ukulu wake umaoneka mwa inuyo khalani pafupi ndi mulungu machiliso ndimatamando zonse zili kwa iyeyo Amen.

01/06/2020

Ndi mtima wanji wa muthu umalolera kuchita tchimo koma umalekeka kuchita chabwino lekani kusata satana sinjila yabwino ai

31/05/2020

Palibe chomwe chizakupulumuse choposera chikhulupiliro cha mtima wako lapa ndikukhulupilira mulungu Amen

28/05/2020

Tiphuziseni njira yachoonadi ndi moyo yosatha ,tingatani k*ti tizindikire k*ti chomwe tikuchita mchabwino anafusa petrol ndipo yesu anati kwa petrol pereka theka lakatundu wako ndipo upase yemwe alikusauka ndimavuto nanga ife tikuchitanji

22/05/2020

Ngati muwerenga khani zomwe zimalembedwa zokhuza chipulumuso chomwe chikubwerachi ngati mumangowerenga osatengapo chilichose ndibwino usamawerenge chifukwa palibe chomwe umapindula zizak*tengera thawi yayitali k*ti uzindikire choonadi zikomo.

07/05/2020

Tikuyenera kugwilana manja ndikumanga chimozi ,tiyeni tilape abale ndayamba linja mkale kulakhula koma pakupezekabe wina sakulapabe machimo ake lapani lero ndipo akhululuka lero lomwe

02/05/2020

Chisomo cha mulungu chimabwera ngati ukuchita zabwino zomukodweresa mulungu

Awa ndimasiku omaliza khulupilirani mulungu muchoonadi ndipo muzapulumusidwa musalimbane ndikukonda za mdziko kondani mulungu wanu lero Amen

26/04/2020

Ngati mulungu wakudzusa ndi moyo lero tangolemba ( Amen) k*ti muone zokoma zake lero

04/04/2020

Hello

31/03/2020

CHITHUZITHUZI CHA MUNTHU OCHIMWA

Chimaonesa makhalidwe eni eni a muthu ochimwa amene walapa. Iye aona tsopano kukula ndi kuopsya kwa machimo ake ambili- mbili amene yesu anafera pa mtanda. Iye wazazidwa ndi mlapo chifukwa amvadi chisoni ndi kuchuluka kwa machimo ake. Mulungu ali pafupi ndi iwo a mtima osweka. Apulumusa iwo a mzimu olapadi. ( masalimo 34:18). Mwazi wa yesu mwazi wake utisambitsa k*tichosera uchimo wonse (1 yohane 1vs 7-9). Koma ndizayang'anila muthu uyu amene ali waumphawi, ndi wazimu wosweka, nanthunthimila ndi mau anga. (Yesaya 66:2). Ngati uzabvomereza mkamwa mwako yesu ndiye ambuye ndi kukhupilira mumtima mwako k*ti mulungu anamuukusa kwa akufa uzapulumuka. (Aroma 10:91). Amen

Ngati sunapangebe like page panga like k*ti khani zizikupeza mosamvuta ambuye akudaliseni nonse. Amen

22/03/2020

Tiope mulungu munyengo zake

Tiyeni tilape machimo chikukhulupilira mulungu ndikusata choonadi abale nthawi ndiye yatha onani zizindikilo zomwe zikubweraz matenda, kuba, kuphana, katangare, ziwawa ndichani amalawi tiyeni tilape. Ngati kukufuna khani zokhuza mulungu zisamakupjonyeni pangani like page k*ti zizikufikilani mosavuta zikomo .

22/03/2020

Hello mulibwanji mazulo ano

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Bangwe
Blantyre
Other Fitness Models in Blantyre (show all)
Ayiche Mtambalika Ayiche Mtambalika
Blantyre

Personal blog designed to share my personal life experiences and also advocate for mental health and fitness...

Lil GANG MW Lil GANG MW
Mbayani
Blantyre, GANGMW

Everybody who’s mentioning my EX on my page is getting blocked.

Shakira Ephdrina-model Shakira Ephdrina-model
Blantyre

Born Shakira Ephdrina Manjomo . Active acting since 2014 and an Active video V***n