Kwagwanji Kunjaku
We keep you updated everytime. Try us l!!!
IS DEMOCRACY GOOD?
(i). Democracy gives mandate for people to express their views. This provides a room for freedom of expression, but it is very lethal in nature. Demonstrations have destructed businesses and infrastructure in Malawi. In 2011, at least 20 people died when they were protesting in Mzuzu. Some people once attempted to stop the construction the Six-Lane road in Lilongwe, in the name of democracy. Like seriously?
(ii). Holding elections as frequently as every five years will see us depleting alot of finances. In 2020, the election budget was known to be $6,000,000 (MK15 billon). In a struggling economy like Malawi, these finances would be very useful in relevant government sectors such as health, education, Agriculture, infrastructure, among others.
(iii). Democracy interrupts developmental projects. Every government has developmental projects to be implemented. Some developmental plans and projects might require enough time i.e a minimum of 10 years to be adequately accomplished. If the government changes, most developmental projects are trashed out by the new government. Examples: the Wanderers and Bullets stadia, do not even show any progress. The community Technical College project introduced by the DPP, is forgotten. Public funds just went in vain.
(v). Voting might change good for worse. We are witnesses of our own livelihoods in Malawi. We thought the DPP regime was worse with corruption, nepotism, tribalism, maladministration, among others. Now look, corruption is reportedly the worst so far, nepotism on the verge of its satisfaction. The prices of commodities are rising by the day and inflation is too much. Change right?
(VI) The government does not emphasize on developing the country but how to win the next elections. The government's first priority is to keep power. So the government has to amass more resources to aid in their campaign for the next elections. That's why corruption is rampant in Malawi.
REST IN PEACE SPYRAL MWENYA😢💔
Witness Supporter naye kudzangotulukira😂😂😂
SILVER DRAMATICALLY DROPS POINTS: 2-2 DRAW
Super League leaders Silver Strikers have failed to collect maximum points at Kamuzu Stadium after a two-all stalemate against Waka Waka Tigers despite having attempted twice to clinch all the points.
The Bankers opened the early lead at the 5th minute through Duncan Nyoni who fired in from Mark Fodya's free kick. A the 53rd minute, Messiah Kachimgwe of Tigers levelled the game following a rebound from George Chikooka's save. Nixon Mwase restored the lead for the Bankers at the 78th minute which gave Silver the hope that they have already won the game. However, things turned astray when Tigers attained a free kick in the last minute of added time just outside the 18 yard box. This made Chimwene Ibrahim to emit a very spontaneous shoot that saw Chikooka collecting the ball from the back of the net. And few minutes letter Mwai Msungama blew the final whistle to signal the end of the match. 2-2 draw!
Silver finished with one man down following a head injury on Silvers' Binwell Katinji who was immediately rushed to hospital. And Steve Nkhoma of Tigers booked a red card following a second yellow in the process. Chimwene Ibrahim was voted man of the match.
I the other match, Kamuzu Barracks draws against the struggling Baka City following a goalless stalemate.
Silver remains on top with 26 points, followed by Kamuzu Barracks with 19, then Wanderers with 18 points having played 10 games each.
Ma team akutamanga😊😊⚽🔥
Malawian Haaland is back.
Mighty Mukuru Wanderers striker Christopher Jacama Kumwembe fondly known as Haaland for his outburst goalscoring talent, is back on the score sheet with a Hatrick.
Jacama attained a Hatrick in a 3:0 victory over Civil Service United at Kamuzu Stadium.
On the other hand, the struggling FCB Nyasa Big Bullets has scooped a point in their one-all encounter against Creck Sporting at Civo Stadium in Lilongwe.
So far the Nomads move to the second position of the Super League with 18 points while Maule remain stagnant on position 5 with 15 points having played 10 matches each.
Ma team akutamanga Kwabasi😂😂
CHILIMA TO GO THROUGH TURBULENT TIMES- Liabunya
The controversial cm self named Senior Prophet, Prophet Austin Liabunya continues to articulate more so called prophecies to Saulos Klaus Chilima. Liabunya has divulged that vice president Saulos Klaus chilima will go through turbulent legal hearings with the corruption charges levied against him, a situation will lead to his distortion of his political career hence the need for Malawians to pray for the VP.
Liabunya writes:
''💠The Vice President will continue to face problems with the court regarding his political future. As I said before the only way to get out of this is for him to humble himself or God will humble him.
Prayer!!! prayer!!! prayer!!!
~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~
Ezekiel 3:17 KJV
“Son of man, I have made thee a watchman unto the house of Israel: therefore hear the word at my mouth, and give them warning from me.”
The entire Believers' Gospel Embassy Church join hands with God's Servant, Senior Prophet Austin Liabunya and all Malawians, praying for our beloved country of Malawi.
He does not claim to be God but simply His mouthpiece in the end times.
This is one of the Prophecies taken from 2023 National Prophecies delivered on 1st January 2023 compiled between November and December 2022"
NTHENGA INANSO YATSOTSOKA KU DPP
Mkhalakale pandale mdziko muno, yemwenso anali mneneri wa chipani cha DPP, Brown Mpinganjira waikodzera DPP mkabudula.
Mpinganjira yemwenso amadzitama kuti ndi amene anabweretsa ma TV mdziko muno, ati asiya DPP chifukwa ndichipani chopanda dongosolo ndipo mikangano yawo siikuonetsa tsogolo lowala kuchipanichi.
Mneneri wachipani cha MCP yemwenso anauthawa ubusa nkulowa ndale ngati Chakwera, a Rev. Maurice Munthali, atsimikiza za izi ndipo ati a Mpinganjira alandiridwa masanawa ku likulu la chipani cholamula cha MCP kumwera ku chichiri mmzinda wa Blantyre.
Brown Mpinganjira yemwenso ndi mchimwene wake wa mkaidi wolemera kwambiri mdziko muno, a Thom Mpinganjira, anali imodzi mwa mizozodo ikuluikulu KU DPP.
* Kwaola matumbo KU DPP!*
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment update.
[Chithunzichi: Mpinganjira]
KELL KAY WAVOMEREZA KUTI SANALI KUGWIRIZANA KWENIKWENI NDI MARTSE
Woimba Kelly Kambwiri yemwe amadziwikanso kuti Kell Kay wayankhapo pa zomwe akuganiziridwapo kuti anapha Martse.
Kell Kay ati ati ali ndi chisoni kuti iyeyo mmene walimbikilira moyo wake wonse kuti afike pamene ali paja, nde anthu akufuna amuonongere mbiri.
Iye akuyankhapo potsatira kanema yemwe anatulutsidwa Prophet George Chinoko momwe Kell Kay akutchulidwa kuti anatengapo gawo pa imfa ya Martse. A Chinoko ananena kuti Martse asanamwalire anamuuza kuti Kell Kay akhala akudana naye chifukwa choti anali pachibwenzi ndi chibwenzi chake chakale. Kell Kay wavomerezadi izi koma wati ichi sichifukwa chokwanira choti angamaganizilidwe paimfayi. Iye wati atapeza kuti Martse ali pachibwenzi ndi mkazi wake wakaleyu, sizinamsangalatse koma anazamkhululukira ndipo anayamba kuchezanso koma ubale wawo siunali ngati kale ngakhale anali kuti amkhululukira.
Kell Kay wanena kuti anamsiya Martse kumwambo wotsegulira album yake chifukwa cha khalidwe lake la Martse lomwe sanamasuke kulitchula. Iye wadzudzulanso anthu omwe amamuganizira kuti Ali limodzi ndi Prophet Shepherd Bushiri kuti izi sizoona ndipo sapemphera kumpingo wa ECG monga ambiri akuganizira koma ndi wa SDA.
Iye walangizanso akubanja la Martse kuti imfa ya mbale wawo, isawapangitse kubweretsa mapokoso koma aonetsetse kuti sakusokonezeka ndi anthu ena alionse odanitsa.
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates.
LIABUNYA AKUFUNA KUDZISOWETSA
Mneneri wosadziwa kunyenga mdzikomuno Prophet Austin Liabunya, akuoneka kuti zake zada.
Liabunya wasiya mawu patsamba lake la mchezo kuti, 'A Malawi amamkonda mneneri akawasiya' kenaka pansi pamawuwo pali chithunzi chomwe akubaibitsa zomwe zikuonetsa kuti mwina akufuna kulisiya dziko lapansili.
*Mkamva kwathu sipadziko, msadzadabwe waneneratu mneneri paja anzathuwa pankhani zolosera imfa ndi akatakwe. 😊*
Like KKwagwanji KunjakuKKwagwanji Kunjakufor more news and entertainment updates 🔥🔥
[Chinthunzi ndi cha Liabunya]
Kwachitikanso scandal ina kuseliku. Anthu akumasuka kumajambulana maliseche inu hmmm
Follow this link to join our WhatsApp group of scandals to watch it
MA SCANDAL PA MALAWI WhatsApp Group Invite
'MWANG'OMBOKA', MLAKA MALIRO😂
Woimba Mlaka Maliro wachenjeza munthu yemwe amtchula kuti kuti sizitheka zimene akufuna kuchita kuti ampereke iyeyo [Mlaka] ngati nsembe kumidina.
Mlaka wanenetsanso kuti iyeyo ndi batani la POOPSA ndipo aliyense wofuna kumchita zakumidimazo aona nyekhwe.
*Ku Malawi kuno kulibe kupuma. 🙌🙌🙌*
Like Kwagwanji Kunjaku for news and entertainment updates🔥
[Chinthunzi ndi Mlaka Maliro ndi zomwe anatumiza papeji yake]
AMAYI BUSA AJA AMWALIRA
Mayi busa waku Lilongwe uja amatumizira zithunzi komanso kanema wamaliseche ake ku chibwenzi uja wamalira atamwa poison.
RIP mayibusa 😭😭
AMAYI BUSA AJA AMWALIRA😭
Mayi busa waku Lilongwe uja amatumizira zithunzi komanso kanema wamaliseche ake ku chibwenzi uja wamalira atamwa poison.
RIP mayibusa 😭😭
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates🔥
'MWANDILAKWIRA', NYONDO
Mneneri wa Prophet Shepherd Bushiri, Ephraim Nyondo wadandaula ndi zomwe achita mchimwene wa Martse.
Mchimwene wa Martin Martse Nkhata, Jerome, anatulutsa vidiyo dzana kufotokozera a Malawi kuti akhulupilire zoti imfa ya Martse inali yokonzedwa ndi anthu akumidima.
A Jerome, anali ndi foni ya malemu Martse yomwe akuti ndi yokhayo inapulumuka nthawi yamoto ija. Iwo anatsegula WhatsApp ya malemu Martse nkumawerenga mauthenga amene Martse amacheza ndi a Ephraim Nyondo. Uthengawo ukuonetsa kuti Martse anagwilizana ndi Nyondo akumane kwina ku project inayake yaku Mangochi yomwe iye Jerome akuganizira kuti ndi Goshen city. Mkufotokoza kwawo a Jerome amatsindika kuti Nyondo, poti amagwira ntchito kwa Shepherd Bushiri yemwe anthu ena oipa amamuganizira kuti amachita zausatana, akukhuzidwapo pankhaniyi.
Poyankhapo patsamba lawo la Mchezo, a Nyondo ati iwo akudabwa ndi zomwe achita [Jerome] pakuti iye amadziwana ndi Martse kalekale asanayambenso kugwira ntchito kwa Bushiri. A Nyondo akuti atayamba kucheza ndi Martse mpamene amazazindikira kuti Martse ndi Martin Nkhata, kenaka kudziwana kwawo kunakula pakuti mayi a Nyondo nawo ndi a Nkhata ndipo amatchulana pachisuweni (cousins). Iye ati kucheza kwawo kumakhala kwabwinobwino ngati asuweni ndipo zomwe zimawerengedwa mu foni ya Martse zizikusonyezapo kuti panali udani uliwonse kapena chiopsezo, nanga Jerome amazigwizanitsa bwanji ndi imfa ya Martse?
*Eish nkhani zake. Akudziwa ndi Mulungu yekha🙌🙌*
Like KwKwagwanji KunjakuuKwagwanji Kunjakuor more news and entertainment updates 🔥🔥
[Chinzunzichi ndi cha Ephraim Nyondo]
IMFA YA MARTSE YAVUMBULUKA!
Mkulu wa malemu Martin Martse Nkhata, Jerome, watulutsa kanema yofotokoza zimene zinamchitikira Martse tsiku limene anamwalira. Nkhani yake akuti anthu qkumidima amamutsata chifukwa choti anawakana kujoina nawo zipembedzo zawozi. Mukanemayi Jerome, akuonetsa phone yeniyeni ya Martse yomwe ndi chinthu chokhacho chomwe chinapulumuka ku moto uja, ndipo zithunzi, matsamba amchezo ake akuonetsa kutidi ndi Martse weniweweni.
Muvidiyoyi mkutchulidwa anthu otchuka mdziko muno monga Ephraim Nyondo komanso Shepherd Bushiri.
Oyifuna vidiyoyi ponyani manambala anu tikupangeni add ku whatsapp group komwe mkaipeze.
Continue RIP Martse😪
[Chinthunzi chili apa ndicha Jerome Nkhata ]
Nkhani ili mkamwamkamwa pano ndi ya amayi busa a imodzi mwa mipingo ikutumphuka kumeneyi ku Area 25 ku Lilongwe. Mayiyu anazijambula ma vidiyo olalula ndikutumizira chibwenzi kenaka atayambana ndi mwamunayo basitu atulutsa mavidiyowo pambalambanda. Hmmm kuyaluka kwa bwanjiku amayi busa.
Choyamba pangani like peji ino ya Kwagwanji kunjaku, ndikupanga share kenaka ndikuponya manambala anu mmunsimu tikupangeni add ku group muonere mavidiyo ya maibusa woyalukayu 😪
'DZICHOTSENI NOKHATU APULE,' Anthu M'ma Group
Patha pafupifupi mwezi president wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera atachotsa ntchito akuluakulu omwe anawasankha kuti amuthandize poyendetsa boma kuphatikizapo mkulu waku nyumba zaboma, mkulu wapolisi mwa ena komanso kulanda ntchito zomwe anadzipereka kwa wachiwiri wawo a Dr. Saulos Klaus Chilima. Nkhani yake inali yoti anthuwa maina awo akupezeka pa lipoti laku United Kingdom lamilamdu yakatangale yachikhwaya chaku ulaya Zuneth Sattar. Iwo anachita kunenetsa kuti achita izi pofuna kuthana ndi mchitidwe wakatangale mdziko muno.
Pano lipoti lina laku UK latumphukanso uku. Lipotili lina
lapezeka boma la UK litakachita chipikisheni kunyumba kwa Sattar ndikupeza nkhani yochititsa manyaziyi. Nkhaniyi ndiyokuti kunyumba kwa a Sattar kunapezeka zikalata zoonetsa kuti president Chakwera anasainira makontarakiti awiri mwachinyengo ndikuvomereza kuti Zuneth Sattar apatsidwe makontarakitiwa.
Ngakhale ena akuti president sangakhale wolakwa posainira chifukwa iyeyo ntchito yake nkungosainira basi moti sangadziwe kuti akusainira zachinyengo kapena ayi, koma
"Kodi iye angalole bwanji kusainira zinthu zoti sanazimvetse? Zikalatazi zikuonetsanso kuti Sattar anapereka makhobiri miyandamiyanda kwa president Chakwera ngati njira yomthokoza pompatsa makontarakitiwa. Nanga iye alandira bwanji mphatso ngati sakumvetsa tanthauzo la mphatsoyo?. Nayenso adzichotse yekha pamapando, ngati zikuvuta adzilande yekha mphamvu ngati muja anachitira kwa wachiwiri wake. Zisamakomere mbuzi kugenda galuyi, " anthu mma group.
Pakadalipano a Chakwera sanayankhulepo kalikonse pankhaniyi.
*Apa ndiye timati madzi achita katondo. 😜*
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates 🔥🔥
"KWATSALA INU A CHAKWERA," Anthu M'ma Group
Anthu akupitilizabe kupereka chenjezo kwa President Dr Lazarus Chakwera kuti atengerepo phunziro pa zomwe zachitikika ku Colombo mdziko la Sri Lanka.
Nzika zaku Sri Lanka zinachita zionetsero zomwe sizinayambe zachitikapo zaka zapanozi. Iwo anakwanitsa kulimbana ndi asilikali mpaka kuthyola nyumba yaboma ya president (state house) mmzinda waukulu wadzikolo, Colombo nkulowa mkati. Nzikazi zinayamba kujambula ndikutumizirana zithunzi mnyumbamu zikuvinavina, kudumphadumpha mmipando, kugona nkumasewera chipako pabedi imene amagonapo president wawo, kusamba shawa yapresident, kukakhala ndi kumasewera pampando wachifumu wapresident (womwe olo nduna olo vice president sangayerekeze kukhalapo), kuny*ra muchimbuzi cha president komanso kusambira mu swiming'i puu yapresident..
Monga mkudziwira mmene chitetezo chimakhwitimira kunyumba kwa president koma anthuwa mogwirizana, mosaopa komanso mosaopsezedwa anakwanitsa kukathyola. Asilikali anayetsetsa kuwakaniza, kuwaphulitsira teargas, kuwakuntha ena koma anthu sanawafookere, anakakamirabe mpaka kumgonjetsa wamfutiyo. Moti pofuna kumpulumutsa president asilikali anavutika zedi kuti amthawitse bwanawao poti anthu anali atazungulira siteti hausi yonse.
Chatsitsa dzaye kuti njobvu ithyoke mnyanga nchoti anthu anafika potopa ndi mavuto azachuma (maluzi), katangale komanso ulamuliro wosakomera anthu onse wa President Gotabaya Rajapaksab monga zilili ku Malawi kuno. Tikunena pano, president waithawa siteti hausi yake yomwe. Koma anthu akadasewerabe chipako ku siteti hausi ndipo ati sachoka ku siteti hausiku kufikra president Rajapaksa komanso Prime Minister wake (kuno vice President) atatula pansi udindo. Pakadalipano a President Rajapaksa koma prime minister wake alonjeza kuti atula pansi udindo lachitatu likubwerali pa 13 July 2022.
Koma anthu mmagroup ati uthengawu uwafikenso apresident athuwa ndipo augwiritse ntchito mwanzeru. Anthuwa ati ngati sizisintha chaka chino chino chikamatha, nayenso aona manzanganzime.
*Kwachema 🙌🙄*
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates 🔥🔥🔥
AKULUAKULU NDI MDAMBO MOZIMIRA MOTO [CHIUKEPO]
Mwambiwu waphelezera ku Joni komwe timu yampira wamiyendo imasewera ndi timu ya dziko la Lesotho lero mmpikisano wa COSAFA
Timu yadziko linoyi yavwapulidwa ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi chomwe wagoletsa Chiukepo Msowoya wa Mighty wanderers. Chiukepo yemwe akhala akuyang'anilidwa pansi ndi anthu ochuluka kaamba koti ali ndi zaka 40 zakubadwa ndiye wapukuta misozi a Malawi kuti asachoke maso atakomoka ndi manyazi.
Malawi ili pa nambala 3 mgulupu mwa matimu 4 kaamba ka chigoli Cha Chiukepo.
ike Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment Updates.
KUKWANIRITSA KHUMBO LA MALEMU MARTSE
Patha mwezi ndi masiku angapo thupi la woimba Martin 'Martse' Nkhata litaikidwa mmanda. Monga tikudziwa Martse anali ndi malingaliro ofuna kutukula maphunziro popezà ndalama kudzera mwa okonda nyimbo zake nkugulira madesiki, koma imfa inachita njiru.
Pano akubanja la Martse a Nkhata, aonetsa chidwi chofuna kukwaniritsa khumbo la m'bale wawo. Iwo agwirizana zosintha dzina la peji la pa Facebook la malemu Martse kuchoka ku ndipo pano lidzitchedwa . Iwo ati cholinga chawo ndicho kupitiliza lingaliro lomaliza la malemu m'bale wawo logula madesiki nkuthandiza ana asukulu mmagawo osiyanasiyana komanso kutukula nyimbo zake.
Chimwalilireni Martse, peji yake yakhala yotsalembedwapo kanthu koma kuyambira lero payamba kutumizidwapo zinthu monga zakusinthidwa kwa pejiyi komanso vidiyo ya nyimbo yomwe anaimba ndi Nepman ya 'Malume' ngakhale panali kusemphana Chichewa pakati pa Malemu Martse komanso yemwe anajambula vidiyoyi Ron Cz pavidiyoyi.
*Mzimu wake uziusabe mmtendere Martse*
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment Updates.
MWANA WAMMUNA ANALAKWANJI?
Pomwe akupitiliza kumenyera nkhondo kuti M***a John atuluke, magistrate winanso uku agamulanso zokaikitsa.
First Grade Magistrate dzulo waku Mwanza wagamula kuti mnyamata wazaka 19 Charles akakhale kundende zaka 7 pochita chibwenzi ndi kupereka mimba kwa mtsikana wazaka 16. Charles Walasi anamtsegulira mlandu wogwilira ndikumpeza wolakwa pamlanduwu.
Koma anthu ambiri akuonetsa kusakhutira ndi mlandu komanso chigamulochi ponena kuti anawa anali pachibwenzi sikuti Charles Walasi Christopher anachita kugwiritsa ntchito nthanana kuti agonane ndi mtsikanayu. Nanga chomangira mnyamata yekhayo nchani anthu anali pachibwenzi?
Ichichi ichi,sichilungamo ichi!
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment Updates🔥🔥🔥
THEY ARE STILL ACQUAINTANCES!
A week has passed since His Excellency Dr. Lazarus McCarthy Chakwera expurgated all his dedicated powers to his vice and political allyship companion Right Honorable Dr. Saulos Klaus Chilima. This implies Dr. Chilima is not holding any cabinet position but only holding the constitutional position of Vice President.
This move promulged some political pandemonium among others especially to the United Transformation Movement (UTM). UTM followers expressed discontentment with the presidential order and perceived Chakwera obnoxiously thinking he is doing this deliberately in order to dwindle Chilima's political morale and dismantle his reputation so as to make sure he flunks to succeed him as per rumors of what they concorded in their political-leadership alliance. However veraciously, Chakwera being a pastor and a man of his words would never or will never betray Dr. Chilima. Ernomous people are cognizant of how significant Chilima has been to Chakwera and without Chilima, Chakwera would never be where he is today, that is if and only if you are able to comprehend the verity.
Can you just imagine Dr. Chakwera withdrew all his dedicated powers to the VP yet he called for a cabinet convocation the following day with Chilima in presence? Chilima is the Vice President yes, but as it stands he is not holding any cabinet position hence it is senseless to attend any cabinet convocation. If Chakwera is really serious or disconcerted with what Chilima did, he would not dare summon him to avoid the public being pessimistic about his seriousness. But he did this just to look as if he is scrupulous and can act to such sensitive and rantankerous matter at hand as corruption just to make the public optimistic and taciturn but veridically he did not do anything prudent. This was just to blindfold us. They are still together and we can not hope for anything exquite from them any longer.
To UTM subjects, take heart. Chakwera would never and will be treacherous to Chilima. He is a very stupendous man. But the amalgation that exist between the two is very humongous such that any move that can be taken to stupefy us is a just mere stupy. Honestly we are yet to dance to such malodorous tunes of these harpsichordist.
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates 🔥🔥.
POLOGALAMU YATSOPANO
Kwagwanji Kunjaku iyambitsa pologalamu yatsopano yomwe idzitchedwa . Pologalamuyi idzisiyana ndi nkhani zina zomwe zakhala zikumatumizidwa pano pazifukwa izi:
1. Idzilembedwa mchingerezi
2. Idziunguza nkhani zikuluzikulu zomwe zikuchitika mdziko muno komanso kunja kwa dziko lino.
3. Idzikhutula konanso kubweretsa poyera mavuto, kuipa, ubwino komanso njira zopewera mavuto omwe achitika mnkhanimo.
4. Idzipereka mwayi kwa inu otsatira kupereka maganizo anu pankhani yomwe yaunguzidwayo.
Pologalamu yoyamba ya ikufikani usiku uno 8 koloko.
Khalani pompo!
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates🔥🔥
HIS MAJESTY VINCENT WANDALE I😂😂
Nkhani ija ikupitilirabe kuno. Anayamba nkukhazikitsa Mulanje ndi Thyolo kukhala dziko lake nkukanika.
Lero afika pochoka mantha ndipo walengeza kuti Malawi si republic ndipo kuyambira lero ndi monarchy kapena kuti dziko lolamulidwa ndi Kalonga.
Zateremu, nde kuti Mtsogoleri wa dziko lino ndi His Majesty King Vincent wandale I ndipo a Dr. Lazarus Chakwera ali pansi pawo ngati Prime Minister.
Mkufotokoza kwawo a Kalonga Wandale I, ati kusanabwere azungu Malawi linali kale dziko loima palokha komanso laufulu lolamulidwa ndi mafumu. Iwo ati kukhazikitsidwa kwa dziko lino ngati Nyasaland ndi azungu komanso ngati Malawi ndi Kamuzu nkophwanya Malamulo ndipo ati dzikoli silidzitchedwanso Malawi kuyambira lero ludzitchedwa kuti Kingdom of Myland (Ufumu wa Dziko Langa ).
Mkalata yomwe alembera akuluakulu aboma, a Wandale ati Boma likuyenera kuwapatsa ofesi ku Capital hill mnsangamnsanga ngati Mtsogoleri wa dziko. A Kalonga Wandale ati ngati sapatsidwa ofesi ayamba kugubira ku capital hill mpaka ampatse ofesi.
Pakadalipano boma silinayankhepo pankhaniyi. Mu 2017, khoti linapeza ndikugamula kuti a Wandale ndi munthu wamitsala ndipo zomwe akukamba ndi zopanda umunthu wangwiro. Koma dokotala wina atapanga kafukufuku wke wozama, anapeza kuti a Wandale si amisala ndipo ali bwinobwino ndithu ndi ungwiro onse.
*Mwawalandira bwanji a His Majesty Vincent Wandale I a Malawi anzanga?*😊
NKHANI YAVUTA NDI YAKUSIIDWA KWA NEPMAN KU AMERICA
Anthu ambiri akambapo zakusiidwa kwawoimba Nepman ku United States of America (USA). Nepman anasainiridwa ndi gulu la zamaimbidwe la Zembani lomwe likutsogoleredwa ndi Lucius Banda komwe amalandira ndalama pamwezi ngati mmodzi mwa oimba awo ndipo akhala akupindula zedi.
Koma dzulo anthu achita jenkha atapeza kuti Zembani Band yonse yapita ku America kukaimba kumsiya Nepman yekha ku Malawi.
Ngakhale anthu akumvera chisoni, koma Nepman mmayankhidwe akr akuoneka kuti zizikumpweteka ndipo naye Lucius Banda akuti amene akuona kuti Nepman akuzunzika ku Zembani amutenge adzikamdyetsa ndiwowo.
Inu mkuiona bwanji nkhaniyi?
'APULE YEMWEYO!!!'
A Malawi ayamikira koyamba President Dr Lazarus Chakwera pamawu komanso zimene achita dzulo kunyumba yachifumu.
Kwa kanthawi ndithu, anthu akhala akuonetsa ukali ndi president Chakwera ponena kuti amadziwa bwino kuyankhula chingerezi koma amakanika kukwaniritsa zimene amayankhulazo.
Koma ngati kutulo, president Chakwera wachotsa ntchito zonse zomwe anadzipereka kwa wachiwiri wake Saulos Klaus Chilima atapezeka kuti anachita nawo zakatangale kuchokera ku chikhwaya choctchedwa Zuneth Sattar.
Anthu ambiri amaona ngati President Chakwera sangamchotse Chilima chifukwa choti amagwirizana kwambiri komanso kuti sangampange chipongwe poopa kumukhumudwitsa komanso kuononga mgwirizano wawo pandale, koma a Chakwera achita izi pofuna kuonetsa kuti sakusekelera nawo zakatangale.
Ena omwe akukhudzidwa mu katangale wa Sattar ndipo aimitsidwa mmaudindo awo, ndi Mkulu wa Achitetezo Cha Mdziko a George Kainja, Mkulu woyang'anira nyumba zaboma ndi ena ambiri akuluakulu aboma.
Ulemu woposaposa waperekedwa kwa mayi Martha Chizuma, posaona nkhope koma kubweretsa poyera maina akuluakuluwa posaganizira chomwe chitamgwere.
*Mkaladi wangotsala chabe ndi mpando chifukwa chamalamulo, koma ntchito zonse amulanda 😊*
KWACHA YAGWA!
Nthambi yoyendetsa kayendedwe ja ndalama mdziko muno, yalengeza kuti ndalama yathu ya dziko lino ya Kwacha ya yagwa (kutsika nphamvu) ndi 25 pa 100 kwacha iliyonse.
Malinga ndi nthambiyi izi zachitika kaamba ka kukwera kwa zinthu dziko lonse lansi komanso nkhondo yaku Russia ndi Ukraine.
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates. 🔥🔥
APEPETSA AKUBANJA LA MARTSE
President wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera ndi mayi wa fuko Monica Chakwera apereka uthenga wawo wachipepetso ku banja la malemu Martin Nkhata.
Malinga ndi a Chakwera, imfa ya Martse, yawakhudza kwambiri kaamba koti samangoimba chabe iyayi, koma luso lakeli, amaligwiritsa ntchito polimbikikitsa achinyamata komanso kupereka chitsogozo kudziko lino ndipo dziko la Malawi lataya munthu wachichepere yemwe anali wofunikira kwambiri.
like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates🔥🔥🔥
MARTSE AIKIDWA MMANDA
Anthu amamvetsa komanso kuperekera umboni kuti aona maliro komanso kuvomereza kuti wawo apita akaona manda ake.
Pano katswiri wanyimbo za rap Martin Nkhata, yemwe amadziwika kuti Martse, waikidwa mmanda ku Area 18 ku Lilongwe.
Martse, amwalira lolemba ku Queen Elizabeth atapsa ndi moto nyumba itapsa ku Mangochi.
'TOO GHETTO, TOO GUTTER' yapitadi ngati bodza. RIP MARTSE tikusowa 😭😭😭
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates 🔥🔥🔥
ANACHITA KUBWELERANSO MNYUMBA!🙄🙄
Zambiri zayamba kutumphuka kutsimikiza kuti imfa ya Martse ndiyokaikitsa.
Pakhala pakunveka mphekesera kuti imfa ya Martse siinali yachilengedwe koma yokonzedwa. Ngakhale ambiri anatsutsa kuti izi ndi mphekesera chabe koma chilungamo chatumphuka.
Woimira kubanja la Martse, Uchizi Nkhata, waulula kuti nawo akubanja akudabwa kuti imfayi siyachilungamo. Malinga ndi Uchizi, chomwe chatsitsa dzaye kuti Njobvu ithyoke mnyanga nchakuti, moto utayamba mnyumbamo, anthu onse anachokamo kuphatikizapo Martse. Koma Martse anachita kubwelerelanso mnyumba yoyaka motoyo komwe anakapsa mpaka lero uyu ndi malemu?
Apa pakuphelezera mphekesera zomwe zakhala zikumveka kuti Martse anathawira ku Mangochi komwe amathawa gulu la oyimba anzake omwe amafuna kumupha kaamba koti anakana kulowa nawo gulu lopembedza Satana (Sataniki).
Mphekeserazi zikumveka kuti Martse anauza anthu omwe anali nawo kuti akusatidwa ndi oyimba anzake asataniki omwe omwe akufuna kumupha kaamba koti sanalowe nawo mgululi.
Inunso simngadabwe, munthu watuluka bwinobwino mnyumba, chimene chingampangitse kubweleranso mnyumba yoyaka moto nchani?
Pakadalipano nduna yazaluso ndizokopa Alendo, Michael Usi komanso yazamasewero ndi achinyamata a Richard Chimwendo Banda, ati Boma likhazikitsa kafukufuku wapadera kuti apeze chomwe chadzetsa imfayi.
Thupi la malemu Martin Martse Nkhata likuyembekezereka kuikidwa mmanda posachedwapa ku manda a ku Area 18 ku Lilongwe.
Autse mmtendere Martse 😭😭😭😭
Like Kwagwanji Kunjaku for more news and entertainment updates 🔥🔥🔥🔥
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre
Namiwawa
Blantyre, PRIVATEBAG437,CHICHIRIBLANTYRE3.
Escape Ordinary Radio🎙️ Stream: bit.ly/3OvGNVn Insta: capitalfmmw X @capitalfmmw #keepitcapital
Chichiri
Blantyre
A Malawian website for career listings including Local & International Jobs, Tenders, Consultancies,
Machinjiri Blantyre And Monkey Bay Mangochi
Blantyre
We offer both good quality pictures and videos
Blantyre
Khayalivenewzroom is a news and current affairs website covering local and international news.
Blantyre, HI!PLEASELIKE&FOLLOWTHISPAGE
🚩Quickest, Most Reliable Football Updates.