JETU

JETU

This is the official page of JETU. for bookings contact: +265 882 666 672

21/12/2023

Mawa Ndukayimba Nyimbo Yanga ya GOSPEL uku ... For the first Time .....

20/12/2023

Thank You For ... 200K Views ... One million is that you??

19/12/2023

Akuti Chani Kwanuko Za WAKALAMBA WAFUNA ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Photos from JETU's post 19/12/2023

Kandalama Ka peanut kaja talowa nako mu sitiduyo๐Ÿ˜Ž ... Friday Tigwese Ina????

18/12/2023

Ndalandila K100,000 ya Christmas yochoka kwa fan wanga wina ku Mikozi. Zikomo International Export. Tsopano ndikudyela luso langa ๐Ÿ™๐Ÿพ

16/12/2023

A Zeze aja ndasiya ndapeza mamuna walokosi๐Ÿ˜

16/12/2023

Wolenga mvula ife tizamuyimbila ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

15/12/2023

MBC 2 Visited ๐Ÿ˜Ž ...

15/12/2023

Chaka Chatha Kale ichi๐Ÿ˜Š

JETU naye ndi munthu amafuna galimoto....! PIMP Malawi Motors is building a Gusheshe for Her which will be given to her next year in January....

14/12/2023

Hello .. December Wamaluziyi alibwanji kumeneko??

14/12/2023

Koma Anjira Ayiponya Kutali๐Ÿ˜

14/12/2023

Inu Zabwino Ayhi??? ... Pezani Malo Otchipa awa

13/12/2023

Mukapeza nthawi muzikondwerako
Dollar yanu osamaumira
Moyo ndi Kamodzi si kawiri katatu
Ine ndi Dorothy Kingston - Cashie Madam ndife anjira ๐Ÿ˜‚

13/12/2023

Happy Befide Anjira๐Ÿ˜Ž

13/12/2023

Inu Zabwino Ayhi???? BAMA WORLD yatchipisa malo ndi holiday imeneyi... Pamene zinthu zikukwela Uku malo atchipa ... Mangani Nyumba Yakumtima kwanu ndi BAMA WORLD powayimbila phone pamanambala awa 0982275297 / 0880001936

11/12/2023

Zowinila,Zodyera,Zapaboma pa UK

11/12/2023

Dolo amakhala ndi malo ๐Ÿ˜Š... BAMA WORLD Yabwela kuzaonesesa kuti aliyense akhale ndi malo ake ake December ameneyo ... Ndi 350 sauzande Kwacha yokha m***a kukhala nawo malo anu ... ayimbileni Phone Pa Nambala izi ...0997291320 / 0882193933

10/12/2023

Koma amene wamanga mvulayo wandilakwira๐Ÿ™Œ

09/12/2023

A Song By AmoG..... Download it here ๐Ÿ‘‰๐Ÿ‘‰๐Ÿ‘‰ https://www.malawian.com/music/c/927

Photos from JETU's post 09/12/2023

Get Ready For Something BIG๐Ÿ˜Ž JETU

08/12/2023

Timafupa mma 5pin ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

08/12/2023

Ndikamwela zanga ndikumwela za pinati๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

08/12/2023

Pa 15 TIYEN TIYENI

07/12/2023

Timabebhesa ๐Ÿ˜Š

07/12/2023

Zikomo for sate sauzande Folowazi๐Ÿ˜‚

05/12/2023

Tonse Timauser TNM Tiyeni Tipange Comment Smiling Emoji ๐Ÿ˜

05/12/2023

Mukapeza Nthawi Muzikondwelako .... Dollar yanu osamaumila๐Ÿ˜Š

04/12/2023

Ine Ndi Doro Ndife Anjila๐Ÿ˜Ž

04/12/2023

THANKS FOR 100K YOUTUBE VIEWS
WAKALAMBA WAFUNA... amene sitinayionele Here is the Link ๐Ÿ‘‰ https://youtu.be/wVSvO6UlMhw?si=ViTV2N1926SQnoBx

03/12/2023

Lero Tajomba ๐Ÿ˜‚ Dzulo kunali Ntchito msanamee๐Ÿ˜‚

02/12/2023

Lero kujambulisa ndiine ulere๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ Nyamukani Tizipita pa 24/7 ....

01/12/2023

Zomwe wapanga Ching'aning'ani mukuona bwaa?? Tigwese ina?

30/11/2023

Kodi Ching'aning'ani ukudelera eti???

30/11/2023

Fili miloyoni๐Ÿ˜Ž

30/11/2023

Zikomo Pamafuno anu abwino ... Befide Inakoma iyi๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

29/11/2023

Tafika Uku Kawoneleni Interview Ya Pa Befide๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

29/11/2023

Osamangoti Happy Birthday
Tumizanu Kenakake ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
0990029418

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

Akuti Chani Kwanuko Za WAKALAMBA WAFUNA ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
Inu Zabwino Ayhi??? ... Pezani Malo Otchipa awa
A Song By AmoG..... Download it here ๐Ÿ‘‰๐Ÿ‘‰๐Ÿ‘‰ https://www.malawian.com/music/c/927
Pa 15 TIYEN TIYENI
Watch Full Video https://youtu.be/44o8tc-FSv8?si=J1_MkcReOuOr4sv1
This is the Official JETU page
Thanks For 11K Followers ๐Ÿ”ฅ
Kuipasa moto ku launch ya @jayjaycee
Wapepesa Basi๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚Mukuona bwanji amalawi???
Nthawi Zina ..#IneNdiNda??

Category

Telephone

Website

Address

Blantyre
Blantyre