Tadala

Tadala

Tadala is a Malawian Hip Hop artist.

26/12/2023

Munaawona Atcheya amatutumuka?

24/12/2023

Lero chishango changa ndi yesu

24/12/2023

Chotsa dzanja pa tsaya mchimwene!
Life is too short for so much sorrow.
Play the music, masula mtolo.
jNathan shot it

22/12/2023

Pepa neighbor ngati zimakunyasha ๐Ÿ’จ

20/12/2023

Mukachisi mwalowesa hustle
Yesu chachikhumi abusa ka mphatso
Pomwe ayimangilira
Anzawo tikulira
Si chamba nkafila maso
Maonekedwe anga mumaziwa ku judger
One thing I know zonse amaziwa ndi Jah Jah
Mumudziwe obadwila mu yudeya
Njala sizamva azandiuza uyu deya
Chipulumutso chikanakhala pa nsika
Ma prophet ambiri ali ndi mavenda
Munthu ndi munthu samayamika
Yopanda khini nsanje ndi matenda
Ndale ku guwa kuguwa nyanga
Bola ndimudziwe mlengi mu mtima mwanga
Ntchito za Mulungu palibe sungandipose
Nkuseseleka ndi malamulo ngati Mose

20/12/2023

Pamene lipenga lidzalilanso
Mpamene ine sindidzalilanso
Pamene tidzamuona ndi maso
Tidzachoka mu m'dimaso

19/12/2023

Nde chibaluwa ndizilembela mnyamata?
Apapa nde mwanama a Papa

19/12/2023

Diamonds are forever.
Rest In Peace Jafali.
Akamwile to the world.

18/12/2023

Tadala ndi ine. Koma Tadala ndi ife.
Skuva Fashions

17/12/2023

Control those who control those who decide how long to cover a story and where it goes in the paper, and you control the news. Its politics everywhere.

16/12/2023

Amayo koto,chaku mpoto wina amuphika ngati ali mu mpoto...

14/12/2023

Stand Under The Music To Understand The Music
๐Ÿฆโ˜ฏ๏ธ

10/12/2023

Thanks to all the guys who participated this morning. Most of y'all got it right but unfortunately there could only be one winner.

BUT!

Heres another one. Four winners. 5k per winner.
Share the links,tag me and Sagonjah when you do. The most engaged posts will be our winners.
Remember, this one we'll get 4 winners for 5k per winner.

Links in the comment section
๐Ÿฆโ˜ฏ๏ธ

10/12/2023

The first person to correctly name the song title which has the lines below wins a TNM weekly bundle.
Lets go!!

"Chipulumutso chikanakhala pa msika
Ma prophet ambiri ali ma vendor
Munthu ndi munthu samayamika
Yopanda khini nsanje ndi matenda"

10/12/2023

Good morning fam.
@7:30 we do another QuickQuiz.
TNM family, get ready.

09/12/2023

Quick Quiz to airtel users and the first person to get it right will win a Mofaya weekly bundle.
Mention the song in Mtolo Vol. 2 which has the lines below

"Nde usaiwalire, usanandiwalire
Allah wa Ta'ala ndi ekha ndingamuswalire"

TNM users we go again madzulo.

Sagonjah x Tadala - Wakutowa ft K.I.T 09/12/2023

๐Ÿ–คโ™ฅ๏ธ๐Ÿ’š

Sagonjah x Tadala - Wakutowa ft K.I.T

07/12/2023

Sizokakamiza....
Chilungamo chimamasula...

Photos from Tadala's post 06/12/2023

Ndamvapo kuwawa ndayenela ku Stupa!

[MTOLO VOL. 2 LINKS IN THE COMMENT]

Photos from Tadala's post 05/12/2023

Guys, lero tikambilanepo pano!
To everyone who's listened to Mtolo Vol. 2, I'd love to know, whats your favorite jam so far?

Sagonjah x Tadala - Mtolo Vol. 2 04/12/2023

Pepa neighbor ngati zimakunyasha!

Sagonjah x Tadala - Mtolo Vol. 2 Stream Mtolo Vol. 2, an album by Sagonjah x Tadala. Release Date: November 17, 2023.

04/12/2023

Kuyamika mu zonse ngakhale zonse ndi chabe
๐Ÿคฒ

04/12/2023

Osamatha mawu pama campaign
Tili Tonse bwanji ukundisungila ka mpeni
Ndikalowa m'boma zanga ndipakule
Chikwama cha mloma or mphasa ndiyalule
Ntchito kumalembana akubanja
Muzilimbikila kumatiuza akunjanja
Sitingaiwale wa nzeru asunga mawu
Samakhazikika okudya thako lagalu
Tadya nawo usipa matemba dzana lija
Likulemba lokha pa khoma dzanja lija
Ngati sakuwona muphamike mate mmaso
S***m ndi Gomorrah owelenga khala maso
Tawonana mawanga,mwangokoma pakamwa
Zonse sungaphangile tawonani mwatsamwa
Nde pano tadziwana
Chinamfuna m'bale chilipo
M'bale ife tidakalipo

02/12/2023

Ndikupanga zanga
Mukubwela zanga ndikuphanga
Oyenda ndi mpeni ndi lako lidzakupha lupanga

01/12/2023

Zimene nyuzipepala yalemba...

29/11/2023

Saimba Ng'oma...

29/11/2023

Ntcheu Classic tomorrow!
DON TARZ
Chizmo Njuchi
Blasto (IMVA!)
Saint-Realest
Queen Fyah

Backed by The Tuff Lionz International Band. Tikumane kumeneku mawa

28/11/2023

Yo check it
Moyo umakoma ndi inu pambali
Mumandiuza zonse ndi nthawi sunga sabali
Keep your ears on the ground maso penya patali
Mukayankhula I have to listen, makani kwangali
Ndine dolo ndimadziwa
Moyo ndi madziwa
Samala masewela samachitila pa diwa
Khala olimbikila muli m'nyozo mu usiwa
Chisoni mkumatenda kuli zinkhani kusiwa
Dziwa adzakuiwala palibe chamuyaya
Dziwa ndi ife tadala kuli konse ukukhala
Khala chitsanzo, nthanga mu chipatso
Osaiwala kumapemphela moyo ndi mphatso
Palibe chingakulake
Ndiwe chimfana cha lucky
Nzeru za mwana zagona pakulemekeza make
Ndi atate
Siya phazi
Osakheza mwazi
Maso m'maso mwa munthu osayang'ana pansi

27/11/2023

Pepa neighbor ngati zimakunyasha ๐Ÿ’จ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ’š

27/11/2023

Satsogoza mthenga mavuto akamadza
Mu mtima kusandusa balaza
Mu bongo angozaza
Yekha yekha angodwedeza mutu wangofasa
Yekha yekha angolakhula zi nkhawa kusanza
Limenelo ndiye dziko mwakula
Limagiligisha limamanga nyakula
Kaya umapemphela umapanga maula
Pena zitenthe ngati uli kunsi kwa mbaula...

26/11/2023

Hello ๐Ÿ“ž
Akuti sanamvelebe Mtolo Vol. 2?
Chifukwa chani? Muuzeni asadande.
Links in the comment section!
jNathan shot it

25/11/2023

Kuyamika mu zonse ngakhale zonse ndi chabe
Zisachite kufika poti mpakana tikabe
Zochepazi ziphukile
Mtima wanga ukhutile
Ngati Chinga Gire nkabwelela mundichingamile
Zinsinsi za moyo mundiululire
Zipatso za moyo mundipululire
Moto wanyanya nkhuni mutifumulile
Dziko kuzungulira osadabwa zizungulire
Sinkumila ndikuyandama
Osaodzela ndikuyang'ana
Zisomo zake zingotsagana
Ndinali yani dzana
Lero ndine nyali dzana timangonamizana
Sinditama munthu kuwopa mwina andimana
Mu m'bwaa zanga ukhwepa
Panga zaine mpakana mtembo useka
Kumbwambwana ambwana
Kumazinyenga kupambana
Zako nzake, zake namana kumkhwapa napana

24/11/2023

Now Playing: Amayi ft QUEST MW
Album: Mtolo 2

Mtolo, Vol. 2 by Sagonjah & Tadala 24/11/2023

๐Ÿฆโ˜ฏ๏ธ

Mtolo, Vol. 2 by Sagonjah & Tadala Album ยท 2023 ยท 9 Songs

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

Goodmorning famHere's Chikondi Wiseman doing a soulful rendition of Thandizo ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ. I must say, this is so dope ๐Ÿ‘Œ๐Ÿ”ฅ https:/...
NP: Nyimbo Yanga
Rehearsing Nkumapeto with K.I.T
#Chilimwe #mtolo #Sagonjah #Tadala #Tumaini
Pali dzuwa #rebellionswarfare #itsonhere #tadala

Category

Telephone

Address

Blantyre