Nyerere zolusa

The Mighty manoma MA NO MA

05/01/2024

Mighty Mukuru Wanderers FC yalengeza kuti Blessings Singini ndi osewera watimuyi.

Singini yemwe anali osewera wa Ekwendweni Hammers wapita kutimuyi pa mgwirizano wadzaka zitatu.

01/01/2024

Akuluakulu a Timu ya Mighty Mukuru Wanderers ati nthawi yakwana tsopano yoti alande ukulu wawo omwe anabwereketsa ku Timu ya FCB Nyasa Big Bullets pankhani ya kuchita bwino.

M'modzi mwa akuluakulu a board ya Wanderers a Limbani Magomero alankhula izi lolemba polandira Timu yawo yaing'ono yomwe yatenga chikho cha Nyasa Capital Finance itagonjetsa dzulo Ntaja United 1-3 ku Machinga.

A Magomero ati akhazikitsa ndondomeko yoyamba kudalira osewera ochokera kutimu yawo yaing'ono omwe azikwezedwa kusewera Timu yaikulu yomwe yamaliza season ya 2023 osatenga chikho chirichonse.

Iwo anakumbutsa ochemelera kuti Bullets nditimu yaing'ono yomwe inachokera ku Wanderers koma anailekelera kuti iyambe kulamura pamasewero a mpira wamiyendo m'dziko muno.

Naye Dinesi Chisulo, Mkulu wa ochemelera ku komiti ya ochemelera anati ndizokhumudwitsa kuti Timu yaikulu sinatenge kanthu zomwe zikuonetsa kuti osewera ambiri akungobwelera ku Lali Luban kuzadya ndalama.

01/01/2024
Photos from Nyerere zolusa's post 01/01/2024

Action photos from the 2023 Nyasa Capital Finance Cup finals💙

31/12/2023

Lero pa 31 DECEMBER 2023 kumaliza chaka mukuganiza kuti team yathuyi

Ikonze pati chaka cha mawa monga inu nyerere zolusa?

Photos from Nyerere zolusa's post 29/12/2023

New year yowawa ku pannel ya noma pomwe yaonesedwa msanga wanjira
Atachosedwa Harrison ngati mphunzitsi wamkulu, dzulo team ya noma yasesaso ena omwe anasala ku pannel monga Albert Mpinganjira,Foster Namwera ndi Simplex nthala

Photos from Nyerere zolusa's post 28/12/2023
27/12/2023

Team ya mighty mukuru ngakhale tamaliza opanda kathu inagwiritsa ntchito ndalama zokwana 30million kugula osewera mu 2023 season
Gaddie chirwa
Lawrence chaziya
Christopher kumwembe
Mphatso kamanga
Dalitso khungwa
Emmanuel Nyirendah

Photos from Nyerere zolusa's post 24/12/2023

Mphunzitsi watimu ya Mighty Mukuru Wanderers Mark Harrison wayimika manja ngati Mphunzitsi watimuyi.

Chiganizochi chinaza potsatira nkumano omwe anali nawo ndi akuluakulu atimuyi lamulungu Timuyi isanasewere masewero a semifainolo a Castel Challenge Cup nditimu ya FCB Nyasa Big Bullets omwe agonja 5-2 kudzera pamapenote mumphindi 90 atathera 1-1.

Harrison wafotokoza kuti wayimika manja kamba kazifukwa zomwe zikuchitika kutimuyi komanso zina zomwe zikukhuza Mpira wa kuno ku Malawi.

Mphunziyi wayamikira ochemelera a Timuyi kamba ka chikondi chomwe anamupatsa munthawi yomwe anali mphunzitsi wa Manoma.

Munthawi yomwe Harrison wakhala kutimuyi ngati mphunzitsi walephera kutengetsa Timuyi chikho chirichonse.

24/12/2023

FCB Nyasa Big Bullets 1 (Patrick Mwaungulu 31')-1 Mighty Mukuru Wanderers (Christopher Kumwembe 46)

Penalties Shoot-outs
FCB NYASA BIG BULLETS
Yamikani Fodya✅️
Hassan Kajoke ✅️
Clyde Senaji ✅️
Precious Phiri✅️

MIGHTY MUKURU WANDERERS
Stanley Sanudi ❌️
Francis Mkonda✅️
Peter Cholopi ✅️
Vitumbiko Kumwenda ❌️

FCB Nyasa Big Bullets are though to the Castel Challenge Cup final

24/12/2023

Kwacha opanda dipo 2023

24/12/2023

Full Time
1-1
Richard Zipola Chipuwa walowa nthawi yama pelnaty

24/12/2023

Kumwembeeeeeeee
1-1

24/12/2023

30mins
Mighty 0 bullets 1
Mwaunguru

24/12/2023

LINE UP AGAINST BULLETS
William Thole 21 (GK)

Stanley Sanudi 12 (C)
Wisdom Mpinganjira 7
Lawrence Chaziya 15
Peter Cholopi 5
Balikinho Mwakanyango 23
Felix Zulu 25
Mphatso Kamanga 30
Gaddie Chirwa 26
Misheck Botoman 10
Vincent Nyangulu 9

SUBS
Richard Chipuwa 1
Emmanuel Nyirenda 22
Miracle Gabeya 27
Francis Mkonda 4
Francisco Madinga 70
Vitumbiko Kumwenda 11
Robin Ngalande 18
Christopher Kumwembe 20
Chiukepo Msowoya 14

24/12/2023

GAME DAY
CASTEL CHALLENGE CUP SEMI FINAL 2
MIGHTY MUKURU VS NYASA BIG BULLETS
KAMUZU STADIUM
2:30PM
5PIN OPEN STAND

21/12/2023

Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yavomera chigamulo chomwe FAM yatulutsa pamlandu omwe inasuma kubungweli yoti ilipire ndalama zokwana K22 million.

Izi ndimalinga ndichikalata chomwe Manoma yatulutsa chomwe chikufotokoza kuti ngakhale anali ndamaganizo otengera nkhaniyi ku Khoti lalikulu lomwe limamva madandaulo okhuza masewero a mpira wamiyendo.

Malinga ndichikalata chomwe wasainira ndi mlembi ku board ku Mighty Mukuru Wanderers Chancy Gondwe iwo ati avomera pofuna kuti Mpira upite chitsogolo dziko muno.

Akuluakulu a Manoma afuniranso mafuno abwino a Khirisimisi komanso chaka cha tsopano Komiti ya tsopano ya FAM yomwe yasankhidwa loweruka lathali mudzinda wa Mzuzu.

20/12/2023

DERBY ILI PA 4 PIN

Masewero a pakati pa FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Mukuru Wanderers mu Castel Challenge Cup ayikidwa pa mtengo wa K4,000 ngati akufuna kugula tikiti yokaonerera masewerowa.

Bungwe la Football Association of Malawi lomwe tsopano lili ndi katakwe komanso Namanyonyolo, Fleetwood Haiya, latulutsa mitengoyi yomwe ikuonetsa kuti omwe adzagule pa tsiku la masewero adzapereka K5,000.

Ku MBC Stand ndi K5,000 tikiti ndipo tsiku la Mpira ndi K6,000 pomwe ku Covered ndi K7,000 tikiti ndipo pakhomo pompo ndi K8,000 komansotu ku VIP ndi K15,000 tikiti pomwe pa geti ndi K20,000

19/12/2023

It's super Sunday 24 December
Castel challenge semi final 2
Kamuzu stadium the soccer maker
14:30
Mighty mukuru Vs Nyasa Big Bullets

16/12/2023

FULL TIME:
MANGOCHI UNITED 0-2 WANDERERS RSV
Chifuniro Kamenya 22' Stain Matengere 88'
The Junior Nomads cruise into the finals of Nyasa Capital Finance Cup!

13/12/2023

Semi final
Mighty vs Bullets
Malo sanasakhe tidikire a FAM

13/12/2023

STANLEY SANUDI

🥌 Most Clean-sheets
⚽ Most goals by a defender
🎯 Most Assists in TNM Super league
🏑 Most dribbles by a defender
🥇 Most Man Of The Match Awards

Captain season ino anali pampira

Photos from Nyerere zolusa's post 10/12/2023

Full Time
Mighty 3 Moyale 0
Misheck⚽⚽
Nyanguru⚽
Misheck man of the match
Zateremu tikumana ndi owina pakati pa ma team a Nyasa Big Bullets Vs Ekwenden

10/12/2023

GAME DAY
CASTEL CHALLENGE CUP
Mighty vs Moyale
Kamuzu Stadium
14:30PM

06/12/2023

FULL TIME: TIGERS RESERVE 2-4 WANDERERS RESERVE
The Mighty Wanderers Reserve advance into the semifinals of Nyasa Capital Finance Cup

06/12/2023

Line up for Wanderers Reserve against Tigers Reserve in Nyasa Capital Finance Cup Quarterfinals

Goalkeeper
Vincent Mdoka 21

Defenders
Lexon Osman 3
Samson Banda 18
Chembezi Chihoma 4
Ibrahim Awali 2

Midfielders
Felix Kamenya 8( C)
Dan Kudonto 15
Fatsani Juwawo 14

Strikers
Mayamiko Makasu 20
Wallace Adam 11
Chifuniro Kamenya 7

Subs
Maxwell Makupa 1
Everton Mponda 26
Blessings Saiti 10
Bob Mpinganjira Jnr 6
Lucky Sambani 12
Chimwemwe Masha 5
Albert Mpinganjira Jnr 19
Foster Milanzi 16
Madalitso Khamula 13

06/12/2023

MATCH DAY: NYASA CAPITAL FINANCE CUP
QUARTER FINALS
Tigers Reserve vs Wanderers Reserve at Mpira Stadium from 2:30pm
Tiyeni kuchiwembe manoma

03/12/2023

Zativutaso pa civil stadium
Civo 1 mighty 0

03/12/2023

Zili ku lilongwe
Half Time
Civo United 1 Wanderers 0

Photos from Nyerere zolusa's post 03/12/2023

Game Day TNM Super League
Game No:30
Civil united vs Mighty mukuru
2:30PM
Tiyeni tonse tikaonere kutha kwa lig

01/12/2023

Motsogozedwa ndi captain
Sanudi
Chaziya
Cholopi
Gabeya
Kaliat
Wisdom
Defence iyiyi ndi yokhayo yomwe yachinyitsa zugoli zochepa 14 mu ma game 29 am TNM Super League

Photos from Nyerere zolusa's post 30/11/2023

Happy birthday Gaddie Chirwa

Photos from Nyerere zolusa's post 28/11/2023

The blues 💙💙💙💙💙🔵🔵🔵

27/11/2023

Mphatso Kamanga
Jersey 30 wa Noma

26/11/2023

FULL TIME:
Red Lions FC 0-1 Wanderers FC
Gaddie Chirwa 68'⚽

26/11/2023

Mighty Mukuru vs Red Lions

21'| William Thole (GK)

12'| Stanley Sanudi (C)
5'| Peter Cholopi
7'| Wisdom Mpinganjira
9'| Vincent Nyangulu
11'| Vitumbiko Kumwenda
15'| Lawrence Chaziya
25'| Felix Zulu
26'| Gaddie Chirwa
27'| Miracle Gabeya
30'| Mphatso Kamanga

SUBS
1'| Richard Chipuwa
3'| Ahamad Kung'unde
4'| Francis Mkonda
10'| Misheck Botoman
14'| Chiukepo Msowoya
17'| Isaac Kaliati
20'| Christopher Kumwembe
23'| Balikinho Mwakanyango
70'| Francisco Madinga

26/11/2023

MATCHDAY
Mighty Mukuru vs Red Lions
Castel challenge cup
Balaka Stadium
2:30pm

24/11/2023

Log Table
1.Bullets 28 games 56pts
2.Silver 29 games 56 pts
3.Wanderers 29 games 55pts

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address

LALI RUBAN Road IN BRANTRE
Blantyre
Other Athletes in Blantyre (show all)
Artwork maker Artwork maker
Kanjeza
Blantyre

Athlete

Hugro toxic Hugro toxic
Newlines
Blantyre, THANKS

Mtendele Ghama Mtendele Ghama
Blantyre

#FOOT BALL IS MY BLOOD & IDICTATED FOR IT💪⚽💚🔞♨🍁☠

Mickel MW Mickel MW
Lunzu
Blantyre

Five six pears � on my right hand

Enock Berba Moyo Enock Berba Moyo
Naperi
Blantyre

Promoting Upcoming Players

VITU VITU
Blantyre

Just for fun

Talandira mbewe Talandira mbewe
Blantyre

Am footballer age 18 now I want to achieve my goal of football

Chawanangwa Gumbo Chawanangwa Gumbo
Blantyre

A professional Football player at FCB Nyasa Big Bullets.

Ephraim Kondowe Lovers Ephraim Kondowe Lovers
Blantyre

The pitch master

Francisco Madinga Francisco Madinga
Blantyre

Welcome to Francisco Madinga's official page

MStarkay 265 MStarkay 265
Chilomon
Blantyre

Innocent Jere Innocent Jere
Chirimba
Blantyre