MIGHTY WANDRERS FOOTBALL TEAM
Mighty Mukuru Wanderers FC
Happy new month to you all. We love you allπππππππππππ
Pa chi Sunday
Mwazuka bwanji manoma
Muli kuti ndipo mukutani
Osayiwaratu kupita Church kwa omwe kumapita lero
Mu 2nd round ya tnm superleague tasewera masewero anayi imodzi pakhomo atatu koyenda
Yapakhomo ndi mzunzu city hummers Aku away ndi dedza dynamo's civo komaso kamuzu barracks
Pa anayiwo tapambanapo atatu ndipo talepherana imodzi ndipo tatorera 10 points
Umu ndi mmene yochitira
Noma 8 0 mzunzu city hummers
Dedza dynamo's 0 0 noma
Civo 0 1 noma
KB 0 1 noma
Tayifotokozeni team kuti yachita bwanji
wabwera pa ine from Blantyre Chichiri LALI-LUBAN Road. Kodi Manoma mulipo? Nanga madzulo anu akuyenda bwanji? Mukulembera kuti mwina tingakudziweni πππβπππ
Anything can happen don't give up
Tikatero timati Nyerere zapata 3 points
Munali ndi ine ndipo ndinene kuti making mighty mighty again zikutheka
Ndapitaa
Kamuzu Barracks + ........0 Mighty Mukuru Wanderers 1
Full time
Kamuzu Barracks 0 Mighty Mukuru Wanderers 1
Lawrence Chaziya 27'
3 points in the bag
Amaona ngati tiluza kutipatsa 3 away games mowirikiza πππππ
We are in 3 minutes added time
Kamuzu Barracks 0 Mighty Mukuru Wanderers 1
Lawrence Chaziya
Tikupita mu nthawi yowawitsa
Still
Kamuzu Barracks 0 Mighty Mukuru Wanderers 1
Lawrence Chaziya 27'
Still
KB 0 NOMA 1
Still
KB 0 Noma 1
Sama ndi akatundu uyu kudutsa defence ya Kamuzu Barracks
Still
Kamuzu Barracks 0 Mighty Mukuru Wanderers 1
Last half underway
Kb 0 Mighty Mukuru Wanderers 1
Half Time
Kamuzu Barracks 0 Mighty Mukuru Wanderers 1
Lawrence Chaziya 27'
You are with me
Kaliyati kwa Singini kwa Siliwimba, kusunga mpira zikatheka
Still
KB 0 Noma 1
Lawrence Chaziya 27'
Lawrence Chaziya wabaya pa Chifuwa pa Kamuzu Barracks
Kamuzu Barracks 0 Mighty Mukuru Wanderers 1
Goal !!!
Noma
Sama aaa kumuchotsera
Komatu umalowa uwo
Still
KB 0 NOMA 0
20'
Kamuzu Barracks 0 Mighty Mukuru Wanderers 0
10'
Still
KB 0 Noma 0
5 minutes gone
Sama anayesa kupita koma goalkeeper wa KB kuchotsa
Still
KB 0 Noma 0
Frist Half
Starts
KB 0 Noma 0
Our team news against Kamuzu Barracks
Welcome from Civo Stadium
WE ARE HERE TO GIVE YOU THE UPDATES
As usual nthawi imakwana 2:30pm, from Civo Stadium akhale akutenga bwalo lino kuti atipatse mpira wathu
Kamuzu Barracks vs Wanderers
FOOTBALL MATCH TODAY!
Kamuzu Barracks vs Mighty Mukuru Wanderers*
When: Today!
Time: 2:30pm
Where: Civo Stadium
*Come and watch* your favorite team play!
*Support* your team with your friends and family!
*Enjoy* the excitement of live football!
Promise kamwendo and sama tajong
Now Manoma afika ku Capital City. We are here !
Kamuzu Barracks βββββ
Amene tikupita ku Lilongwe from Blantyre tilipo angati? ??? βββββ
Getting prepared ku mawa tiuyambe wa ku Capital City again.
Kamuzu Barracks ββ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Videos (show all)
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre
Kanjeza
Blantyre
Mighty Tigers is a Malawian Football Club based in Blantyre. It plays in the Malawian super league sponsored by TNM. it was founded on 3 March 1978.
Blantyre
Chilomoni cricket club is combination of chilomoni, mbayani and Chirimba zones
Namilango Ground/black Africa
Blantyre, 1996
Under 17 soccer team
Machinga
Blantyre
GROUP INO IDATSEGULIDWA NDICHOLINGA CHOBWERETSA UBALE KWA ANTHU OKONDA MASEWERO AMPIRA NDIKUDZIWITSANA ZOCHITIKA KUTEAM YATHU,ZA MDERA LATHU,MDZIKO LATHU NGAKHALENSO MAYIKO ENA