Ben 1 Music TV, Lilongwe Videos

Videos by Ben 1 Music TV in Lilongwe. – "Ben1musictv πŸ‡²πŸ‡Όβ€

Eeh πŸ˜‚mmatchalitchi namo mmapangidwa zinthu,,,, wa zifufu ngati ine nditha kubwenzela iyaaπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Click to enable sound Next

Other Ben 1 Music TV videos

Eeh πŸ˜‚mmatchalitchi namo mmapangidwa zinthu,,,, wa zifufu ngati ine nditha kubwenzela iyaaπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Chemwali athu kuselikutu ndiye yokha yokha mpaka week yatha pano ndithu πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Choir master of the year πŸ˜‡πŸ˜‡πŸ˜‡πŸ˜‡πŸ˜‡πŸ˜‡πŸ˜‡πŸ˜‡πŸ˜‡πŸ˜‡

Komatu muphana abale sikunache mutsiyeni munthu please πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

Katunduyi kapena mwina sindikuwona bwinobwino eeee Kwachema πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Anthu akuwoneka kuti akukondwera naye kwambili chimwemwe chokhachokha 😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊

Mwakhaula tu?πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Kodi panja nyimbo iyi anayimba ndani?? Good morning neba πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

Kkkkkk happy weekend 🀣🀣🀣🀣

Kumenya kugwetsa kaya ndiye ndani eeee full video on the link

Komatu mukamapeleka mayinawa chabwino πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

Kkkkkkkk koma Chipi amatha 🀣🀣🀣🀩ati azi Auntie ena ku maliro kkkkkk Azi Auntie ngat amenewa ndamene amayambitsa mapokoso ajaπŸ˜‚

Akuti Amwene tivetsetseni πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

Eishii vuto lau batchalaπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚