Malawian Patriot News
_Vacancy, military training,border patrol, peace keeping mission+ to our citizens/May God bless๐ฒ๐ผโ๏ธ
M'zimayi woyendayenda kapena kuti ogulitsa nthupi wavulaza mwa mzathu m'silikali pomutema ndi botolo atapatsidwa ndalama yopelewela yokwana Mk 3000 m'malo mwa Mk4000 pagwilirizanano omwe anali nawo onkhalila limodzi
Padakali pano mayiyu ali m'manja mwa apolice kuyembekezela kukawonekela ku court
Today's best photo, keep up the good job ๐โค๏ธ๐ชโ๏ธ๐ฒ๐ผ
Nde pali a neighborhood kapena kuti achitetezo cha m'madela mukuchitila nkhaza anthu pomawamenya komaso kuwalanda zinthu akadeledwa
Samalani mukapezeka mumangidwa ndipo mukayankha mlandu pa court
Ngati mwachitilidwa chipongwe ndi a neighborhood kapena kufunsidwa kuti mupeleke ndalama ndicholinga akusiyeni, pitani ku Police mukadandawule kuti a neighborhood adela lakuti anandichita chipongwe ndipo mukafotokoze musawope mukathandizidwa
Pewani kuyenda ndi usiku!
Mongokumbutsana vackabond inathetsedwa
Zikomo
I couldn't Coment Before actually watching it... Ndaionela Yonse , This Is Really A way To Go, Ikufunikadi over A million Views ๐ฅ๐
Phwedo ๐ But overall, ma guy onse muli skill ya acting Yachabe ๐ฅ๐ฅ
The Production Team was also Very Serious..
Let's Support Them Ifikile Gulu..๐
No weapon formed against you it shall prosper ๐ชโ๏ธโค๏ธ๐๐ฒ๐ผ
Today's best photo, keep up the good work bro ๐ชโ๏ธ๐๐ฒ๐ผ
Happy new year to all our followers, May God bless you abundantly ๐๐ฒ๐ผ
Kusangalala muchakachi kunali motele muzithuzi๐๐๐
Zili motele kuno ku Lilongwe pokozekela Cup finals ya Castle Malawi ๐ช๐๐โ๏ธ๐ฒ๐ผ
๐ด Two more Palestinian journalists have been killed in Israeli bombings in Gaza, raising the total death toll of journalists in the enclave to 105, according to the Government Media Office. LIVE updates: aje.io/fdiiy5
Good morning ๐ ๐ฒ๐ผโค๏ธ
Hello Family, tapemphedwa kuti tidzitha kukupatsilani ma up date ku nkhondo yomwe ikuchitika ku Gaza_ Palestine ๐ธ๐ฉ,Hamas ndi Israel ๐ฎ๐ฑ
Nde musadabwe tidzipanga zimenezi mosakondela komanso mosamalitsa
Zikomo ๐ฒ๐ผ๐
Today best photo, keep up the good work top squad โค๏ธ ๐ฒ๐ผ๐ชโ๏ธ
โค๏ธ๐ฒ๐ผ๐๐๐๐
_Chidziwitso kwa ife tonse:-
Chitetezo chimayamba ndi iwe mwini,tiyeni tinkhale tchelu munyengo ino ya zisangalalo.
Munyengo imeneyi atsizina mtole amankhala kalikiliki kubela anthu
Yesetsani ngati mukuchoka pankhomo musachoke nonse ena atsalepo
Pewani kuyendetsa galimoto mutamwa chakumwa choledzeletsa komanso pewani kutenga banja lonse mugalimoto poti pa nsewu sipazoloweka
Musanagone yesetsani kuyang'ana zipangizo zamagetsi kuti ndi zozimitsa popewa ngozi osayiwalanso mbawula
Ngati mukuwona chokayikitsa mudela lani chonde adziwitseni achitetezo nsanga
Kondani dziko lanu,dzitetezeni nthawi zonse, Zikomo ๐ฒ๐ผโ๏ธ๐๐ช
Today Sunday mode best photo, keep up the good work bro ๐ฒ๐ผโ๏ธ๐ช
Today best photo, keep up the good work โค๏ธ ๐ฒ๐ผโ๏ธ๐ช
Peace of mind is part of the deal ๐ฒ๐ผโ๏ธ๐โค๏ธ
Nde mudzapezeke ndi military boots ngati awa popanda chifukwa choveka, mamama.....palinso number tcha!๐ค๐๐๐๐ฒ๐ผ๐ช๐
Chest vests and Crip belts ๐ฒ๐ผ๐๐ช๐
๐โ๏ธ๐ฒ๐ผ๐
Kenya follows Malawi in sending farm workers to Israel amid Hamas war Kenya follows Malawi in sending casual farm workers to fill a labour shortage on Israel's farms.
Military boots ๐ฒ๐ผ๐ชโ๏ธ
๐ฒ๐ผโ๏ธ๐ช
Russian helicopter shourt down by Ukraian troops
4.5-Gen Su-35 on SEAD mission was shot down over Ukraine by SAM Ukrainian air defense has shot down the Russian fighter of generation 4 ++ and the main fighter aircraft of the Russian aviation Su-35S Flanker-E, media report
We map the areas of territorial control in Ukraine on day 39 of Russia's war โคต๏ธ
๐ด LIVE updates: https://aje.io/dey5vc
British, US and Polish jets train for combat over Poland 10 fighter jets from Britain, America and Poland executed air to air combat training over Poland this week.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Videos (show all)
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Lilongwe
Opening Hours
Monday | 09:00 - 17:00 |
Sunday | 09:00 - 17:00 |
Sector 2, Area 47
Lilongwe, 207247
NewsDay Malawi is your news; political, entertainment, music and fashion website from Malawi. We pro
Lilongwe
Platform Where You Get informative Content, Current affairs & Entertainment News Promo 0997656111