Chiwamba Community Radio

Chiwamba Community Radio

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chiwamba Community Radio, Grocers, Lilongwe.

18/10/2023

Oyimba otchuka kwambiri ku Malawi Thomas Chibade wamwalira

15/10/2023

That's it! Thanks for following along.

Happy mother's day

Mwawakozera chani amayi?

(Or mutakhala kuti mulibe kuthekera kowapangira chinachake uthenga wanu ndi otani?)

13/10/2023

⚽BALANG'OMBE REAL BOMBERS ITHA KUZITAYA ZA MU FAM MOTO!⚽

Team ya Balang'ombe Real Bombers yomwe imasewera mu chipiku central region FAM MOTO yaopseza kuti ituluka mu mpikisanowu ngati a Central Region Football Association sakonza zotsatira za masewero omwe timuyi idali nawo pa bwalo la masewero la Mnkhupa la chitatu lapitali ndi Blue Eagles Reserve.

Masewero wa adatha 1:0 Bombers kupambana, koma mlembi wa Mkulu mu komiti yaing'ono yoyang'anira mpikisano aWells Kazonde adasonyeza kuti masewerowa adatha 1:1 .Izi zakhumudwitsa akuluakulu a Balang'ombe Real Bombers ndipo, malinga ndi Chikumbutso chimutu mkhalapampando wa timuyi Iwo ati ngati zochita CRFA zipitirire kukhala zimenezi Iwo angosiya kutenga nawo mbali mu mpikisanowu popeza bungwe la CRFA limawakhomelera mu zambiri. Iwo adapereka chitsanzo Cha nkhani yomwe idachitika ku nsaru pamene osewera koma ayang'anira timuyi osaiwala otsatira timuyi adamenyedwa ndi otsatira timu ya Nsaru koma a CRFA sadamve mbali yawo koma adangothamangira kupereka mapoint.

Zampira kudana ndi msunamo
Online reporting #

12/10/2023

Kuyambira lero kufika loweruka kutentha kwambiri, nthambi yoona za nyengo alengeza

Iwo apempha anthu munthawi yi kuti azimwa madzi pafupipafupi, kukhala pa nthunzi ndikupewa kumwa mowa mwauchidakwa

12/10/2023

Opanga malonda a Edward Chimenya ku Lilongwe achita mwayi opata 242 million kudzera masero otchedwa Aviator (Premier Bet)

Edward ati agwilitsa ntchito ndalama kuthandizira business yawo yogulitsa mowa

Mu Chaka cha 2017 a Chimenya adawinaposo ndalama zokwana K900,000 ndipo adali munthu oyamba kuwina kuchoka ku Lilongwe

Iwo ati sadzasiya kusewera masewerawa

11/10/2023

Chamba chopitira matani awiri chomwe eni ake athawa komaso sakudziwika chaotchedwa dzulo ndi a police m'boma la Salima

M'neneli wa Police m'bomali wati apitiliza kuotcha chamba komaso kukhwimitsa chitetezo pofuna kuthana ndi mchitidwe ogula ndi kugulitsa mankhwala ozunguza ubongo

10/10/2023

"Residents of Kavalansava and Gongoni villages in Lilongwe district are at risk of a cholera pandemic as they have not had a borehole since time immemorial. The villagers are living in fear of contracting waterborne diseases as they lack a hygienic water source. Despite efforts from village heads and community leaders to seek help from politicians and well-wishers, the issue remains unresolved. Concerned citizen Mr Macjowet Bakha raises an alarm as the rainy season approaches, urging authorities to take action before it's too late."

09/10/2023

⚽🏐LOCAL SPORTS NEWS !! ⚽🏀
🏆 Exciting Weekend in Chiwamba: Headteacher's Trophy Draws Enthusiastic Crowd 🏟️

Chiwamba residents were treated to a vibrant weekend filled with sports action as football and netball enthusiasts flocked to witness the prestigious Headteacher's Trophy 🏆 organized at Chiwamba Community Day Secondary School. The event, organized by the school's headteacher, Mr. Kapinga, took place at Balang'ombe Primary School grounds on Saturday, October 7th, 2023, starting from 8 a.m. and continuing until dusk. The primary aim of the competition was to foster a spirit of healthy competition and camaraderie among the students.

Both netball and football categories saw a robust participation from the students, creating a fierce competition atmosphere that electrified the crowd as each team vied for the coveted trophy.

In the netball category, Form 1 emerged victorious, clinching the trophy along with a cash prize of MK15,000. Form 4 secured the second spot, earning a cash prize of MK10,000, while Form 3 claimed the third position, receiving a cash prize of MK5,000. Unfortunately, Form 2 did not secure a prize in this category as they finished fourth.

In the football category, it was Form 4 that triumphed, winning the trophy and a substantial cash prize of MK20,000. Form 2 secured the second position, walking away with MK15,000, while Form 3 was awarded the third spot, along with a cash prize of MK10,000. Regrettably, Form 1 couldn't secure a prize in this category.

In an interview, Mr. Jeremiah Guguza, fondly known as "JENCO," one of the sports teachers at the school, expressed his delight at the resounding success of the trophy competition. He praised the headteacher, Mr. Kapinga, for organizing such a fantastic event that provided a platform for students to showcase their talents and skills.

"We are greatly honoured, and I would also like to commend our headteacher, Mr Kapinga, for organizing such an amazing event that provided a platform for our

09/10/2023

It was an exciting day at the Bingu National Stadium yesterday, as football enthusiasts from all over Malawi gathered for the finals of the FDH Cup. Fans of FCB Nyasa Big Bullets and MAFCO had been eagerly waiting for weeks for this ultimate showdown, and it sure didn’t disappoint.

A packed stadium witnessed some fantastic football as FCB Nyasa Big Bullets emerged victorious by beating MAFCO by three goals to nil in a match that saw Lanjes Nkhoma score twice, and Ephraim Kondowe score once.

The game was intense from the very offset, with both teams displaying some impressive skills. However, it was the Nyasa Big Bullets who got off to a promising start and put MAFCO under immense pressure with their stunning attacking display. MAFCO tried to hold on, but their efforts were not enough to stop the Nyasa Big Bullets.

Lanjes Nkhoma showed why he is one of the best strikers in the league as he opened the scoring with his first goal in the ninth minute. This was followed by another impressive goal, again by Nkhoma, in the twenty-second minute, which left MAFCO trailing by two goals.

MAFCO tried to find a foothold in the game, but their attempts were unsuccessful as the Nyasa Big Bullets dominated the midfield and kept the pressure on their opponents.

Ephraim Kondowe put the game out of reach for MAFCO by scoring the third goal in the sixty-seventh minute, which sealed a resounding victory for the Nyasa Big Bullets.

Nyasa Big Bullets had booked their place in the finals following an impressive five-goal win over Dedza Dynamos, while MAFCO had triumphed over Mighty Mukuru Wanderers.

The FDH Cup is one of the major events in Malawi’s football calendar, and this year's final did not disappoint. The supporters of both teams were vocal throughout the match and added to the atmosphere, which was electric.

Felistations to FCB Nyasa Big Bullets, and Hard Lucky Salima Based soldiers!

Photos from Chiwamba Community Radio's post 08/10/2023

Nkhani ya chisoni!

Mmodzi mwa oyimba odziwika bwino Atoht Manje wamwalira usiku wa dzuro pa 7 October,2023.

Atoht, yemwe dzinalake lenileni anali Elias Misi wamwalira atadandaula kumva kutentha mthupi pomwe amaimba kuchigawo chakumpoto pa sukulu ya ukachenjede ya UNILIRA ndipo adapita kukapuma mgalimoto ndipo pamene azake adapita kukamuona adapeza atakomoka ndikumutengera kuchipatala komwe achipatala adatsimikiza za imfa yake. Izi ndi malinga ndi mchimwene wake Katawala yemweso ndi oyimba koma amayimba nyimbo za chisilamu.

Katawala wati thupi la Elias lidakali ku Mzuzu ndipo madongoloso alimkati kuti alitengere kwawo ku Lilongwe kapena ku Mangochi.

Atoht Manje anaimbapo nyimbo monga Che Patuma, Phone ya bea komanso Huwa. Kingotchulapo zochepa chabe.

04/10/2023

Mwambo awoika mmanda a John Tembo ulikati m'boma la Dedza.

Boma ndi limene likuyendetsa mwambowu

27/09/2023

John Zenus Ungapange Tembo has died at the age of 91

Tembo was MCP leader from 1999 to 2013.

13/09/2023

Zotsatira za mayeso ophunzira aForm 4 zatuluka

04/09/2023

Lero lolemba pa 3 September 2023

Muli bwanji?

Tidziwitseni dera lomwe muli

Timakunyadira

27/08/2023

Kwa amene muli ndi malonda koma mukufuna tikulengezeleni pa Facebook pano

Imbani phone pa 0888 966 457/0999 966 457 kapena Whatsapp

Malonda anu adzalengezedwa mwa ulele. Zikomo

27/08/2023

Lero lokhala Sunday amene mumapehera tsiku la lero , mwabwerako ku Church?

Tiyeni tigawane verse ya lero

Amati chan ku Church?

15/08/2023

#
Malawi National Examinations Board (MANEB) has today released results of both 2023 Primary School Leaving Certificate of Education (PSLCE) and Junior Certificate of Education (JCE) examinations.

MANEB Executive Director Professor Dorophy Nampota said, out of 267 330 learners who wrote the PSLCE, 234 ,644 have passed representing 87.77% pass rate, an improvement over the 83% pass rate recorded last year.

For JCE, the board said out of 168 219 candidates, 98 753 have passed. This is a pass rate of 72.06 percent.

Meanwhile, Minister Education, Madalitso Kambauwa Wirima speaking earlier thanked MANEB and all the stakeholders for administering leakage free examinations four years in a row.

# 14/08/2023

27/07/2023

NKHANI YANGOTIPEZA KUMENE!

Bungwe la super league of Malawi - SULOM lalengeza kuti lipereka sabata ziwiri kwa ma timu omwe akutenga nawo mbali mu mpikisano wa TNM supa ligi kuti athe kugula kapena Kugulitsa osewera.

Malingana ndi uthenga umene uli pa tsamba lawo la mchezo, zikuonetsa kuti ma timu ndioloredwa kupeza osewera ena kuchoka pa 1 august kukathera pa 14 August.

Ngakhale zili chomwechi ndondomeko ya masewero a supa ligi siyisintha pamene mlembi wamkulu wa SULOM Williams Banda wati sipakhala tchuthi pamene tikuchoka mu ndime yoyamba kupita mundime yachiwiri..

community Radio #

23/07/2023

CRFA FAM Moto Division One League


Young Professional vs Dzimbiri FC


Hope Academy vs Lizulu Super Star

Chisomo Academy vs Balang'ombe Real Bombers


Simlemba United vs Mitundu Baptist
@ Simlemba

Spearhead FC vs Blue Eagles

:2:30pm

Community Radio #

23/07/2023

*CRFA K15.MILLION FAM MOTO DIVISION ONE LEAGUE WEEK 12 RESULTS 2ND ROUND*

*WEDNESDAY 19/07/2023*

Lumbadzi United 1 - 1 Nsaru United, Oscar Emmanuel (Andrew Tsilizani)

*SATURDAY 22/07/223*

Chezi FC 1 - 0 Make Sure Pirates, Pilirani Wotchi.

Obings Pirates FC 0 - 0 Green Rangers FC.

Dickson United 2 - 2 Shama FC, Emmanuel Kamoto *brace*, (Bruno Chiusiwa, Stonard Kapakasa)

Chatoloma Admarc 4 - 3 Young Talent Mapokezi Academy, Lameck Ngulube, Godfrey Sibale *brace*, Laston Pingeni (Dieume *brace*, Emily Nyikora)

Mtengenji Monaco 2 - 4 LL. Airwing, (Amadu *brace*, Sangwani Chirwa, Innocent Ng'ombe)

*CCR*

20/07/2023

12:21
Do not be overcome by evil, but overcome evil with good

19/07/2023

CASTEL CHALLENGE CUP - CENTRAL REGION

Preliminary Draw underway at Civo Club House, Lilongwe.

1.Airbone Rangers FC vs Hope Football Academy

2.Young Talent Mapokezi vs Ekas Freight Wanderers FC

3.Mangoni Warriors vs Lumbadzi

4.SpearHead FC vs Carolyte Salima FC

5.Dedza Young Soccer vs Green Rangers FC

6.Namitete Zitha FC vs Santhe Admarc FC

7.Mchinji Boma Strikers vs Wimbe United

8. Luanar vs Kamba

9.Mtengenji Monaco vs Simbi FC

#

18/07/2023

Superleague of Malawi has given a cold should to Mighty Mukulu Wanderers as well as Silver strikers to have their game shifted to next Month.

17/07/2023

HON KAIMAPANJIRA K200,000 BONANZA

16/07/2023
Game 1. Bombers FC 2 - 0 Mchemani FC
Game 2. KafumbaFC 3 - 2 Dam Rangers (On post match Penalties)

NOTE!
Mchemani FC did not Show up at Nkhupa ground

Finals
- Bombers FC Vs Kafumba FC
Third place
-Dam Rangers Vs Mchemani FC
**Date will be communicated for the Finals and Third place**

16/07/2023

HON KAIMAPANJIRA (MP)K200,000 IPITE BONANZA
16/07/2023
- Bombers FC 2 - 0 Mchemani FC
- KafumbaFC 3 - 2 Dam Rangers (On Penalty's)
Note
Mchemani FC did not Show up at Nkhupa ground

Finals
- Bombers FC Vs Kafumba FC
Third place
-Dam Rangers Vs Mchemani FC
**Date will be communicated for the Finals and Third place**

16/07/2023

Malawi have ended their run in COSAFA Hollywood bets competition on position four following the loss in the post match penalties after a goalless draw in the regular 90-minutes of the game.

Malawi lost goal scoring opportunities despite having the FCB Big Bullet's super star Patrick Mwaungulu and the former Silver Stricker's Chawanangwa Kaonga in their prime form of attacks.

The duo attackers were ill-fated as the team failed to convert their freekicks they won in both halves and they were saved by great saves Brighton Munthali made in both halves.

The game ended goaless hence prompted the referee to call the teams to the deadly spot to display their knowhows. Kaonga scored an opener spot kick followed by other two teammates while Kumwembe's kick resonated the hurting message as his kick was blocked by the cross bar before the Bafanabafana's neted their fifth kick.

Bafanabafana have denied the flames from winning the bronze medal as they have finished fourth.

Flames have never lost a game in regular time in this year's COSAFA Hollywood bets competitio

By Sam Joseph 16/07/2023

16/07/2023

In the COSAFA Cup 2023 match between Malawi and South Africa, the game ended in a goalless draw. Malawi had several opportunities to score, particularly through Patrick Mwaungulu's superb freekicks and Chawanangwa's freekicks. However, Christopher Kumwembe's missed penalty ultimately cost them the game.

Despite Brighton's excellent saves in both halves, Malawi couldn't find the back of the net. The match then went to post-match penalties, where South Africa emerged victorious with a 4-3 scoreline. Unfortunately, Munthari's failure to clear the last penalty for South Africa led to Malawi's defeat.

George kamadya 16/07/2023

16/07/2023

MABEDI TWISTS LINEUP IN TODAY'S GAME.

Coach Patrick Mabedi has made six changes to the Flames first eleven which battles it out against the hosts South Africa in third-place play-offs at King Zwelithini Stadium in Durban, South Africa.

Daniel Chimbalanga, Frank Willard, McDonald Lameck, Lawrence Chaziya, Chrispin Mapemba and Chifundo Mphasi will for the first time showcase their skills at the tournament since the onset of the tournament.

Mabedi has put on resence captain Stanley Sanudi, Lloyd Aaron, Christopher Kumwembe, Nickson Mwase and Alick Lungu who have been starting in all the group matches as well as the semi-final.

Chimwemwe Idana will lead the Mabedi's boys this afternoon.

The first 11 is as follows:

Brighton Munthali (GK), Daniel Chimbalanga, Lawrence Chaziya, McDonald Lameki, Denis Chembezi, Chrispin Mapemba, Frank Willard, Chimwemwe Idana (C), Patrick Mwaungulu, Chawanangwa Kaonga, Chifundo Mphasi.

George Kamadya

16/07/2023

MALAWI THE FLAMES TO WRAP UP IN ANOTHER STYLE IN COSAFA 2023 CUP TODAY!

The flames of Malawi are set to take on South Africa's football team in the COSAFA 2023 finals for third place. This match is highly anticipated as both teams have shown great skill and determination throughout the competition. The game is scheduled to take place today at 3 o'clock pm and will be followed by the final between Lesotho and Zambia at 6 o'clock pm.

The Malawian team has had an impressive showing in the competition thus far, with solid performances in their earlier matches. They narrowly missed the opportunity to play in the finals after being bested by Lesotho. However, they have another opportunity to make their mark and secure third place in the competition.

The Flames team has a strong line-up with players such as Chawanangwa Chawononga Kawonga and Lanjesi Nkhoma, who have proven to be formidable assets on the field. They have shown great teamwork and coordination, with the ability to create scoring opportunities with ease. Their fans are eager to witness their dynamic playing style and hope to see them secure a victory.

South Africa, on the other hand, has also showcased great skill and tenacity in their earlier matches. They have a talented squad and they have played aggressively and have been able to dominate their opponents with ease.

Both teams have a lot to prove in the match today, with the hope of securing a podium finish. Their fans are excited about the prospect of seeing a closely contested match, with the outcome being determined by the team that puts up the best performance.

This match promises to be a thrilling affair, with both teams eager to make their mark. Football enthusiasts from across the region are eagerly awaiting the kickoff, and the stadium is expected to be filled to capacity. All eyes will be on this fixture, and only time will tell which team will emerge victorious and secure third place in the COSAFA 2023 finals.

George kamadya 16/07/2023.

11/07/2023

MALAWI YAFIKA NDIME YA SEMI FINALS CHINKHO CHA COSAFA

Izi zachitika pamene Flames yamaliza pamwamba ndi 9 points

Pakali pano tiimu ya Malawi ikuphunzitsidwa ndi Patrick Mabedi ndipo lero yangonjetsa Comoros 2-0.

10/07/2023

Ngati muli ndi nkhani yomwe yachitika ku mdera kwanu

Ndipo mukufuna ife a Chiwamba Community Radio mukufuna tiisindikize pa tsama lino

Tidziwitsitseni potilembe uthenga ku inbox, kapena kuimba phone,/kutumiza pa Whatsapp ku ma nambala awa 0888 966 457 / 0992 822 66

Ndondomeko ndi malamulo zidzatsatidwa

10/07/2023

Anthu okonda komaso kutsatira masewero osiyanasiyana akhamukira ku sukulu ya asitikali ya mafco ku Salima kuyambira lero lolemba pa 10 July mpaka lachinayi komwe asitikali akhale akupalana mamba masewero osiyanasiyana monga mpira wa miyendo, wamanja, volleyball Ndi ena ambiri mu mpikisano otchedwa inter-unit. Chiwamba community Radio ikupatsirani tsatanetsatane wa masewero wa.

Izi zikudza pomwe nako ku police, mpikisano wa commissioner's trophy 🏆 uli mkati.

Reported by George Kamadyapa

10/07/2023

Nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo yati dziko lino likumana ndi nyengo yozizila kwambiri

Nthambiyi yati mphepo za Chipironi komanso Mwera iomba pa dziko la Malawi kuyambira lero pa 10 July mpaka loweluka pa 15 July.

Nthambi ya za umoyo wauza anthu kuti anthu akhale osamala maka kwa Iwo omwe amadwala matenda a mphumu

10/07/2023

Malawi yapambana masewero ake achiwiri mu mchikho cha COSAFA itagojetsa timu ya Seychelles 2 kwa 0

Izi zinasangalatsa a Malawi ambiri ndipo zapeleka chiyembekezo kwa Malawi kuti zoterezi zichitikachitika

Zigoli ziwiri zi zinagoletsedwa ndi Lanjesi Nkhoma komanso Christopher Kumwembe

Timu ya Flames idzasewera masewero ake otsatira ndi Comoros lachiwiri pa 11 July.

09/07/2023

Matthew 5:9 ~ Blessed are the peacemakers, for they shall be called sons of God.

06/02/2023

Remember God has forgiven you. “Make allowance for each other’s faults, and forgive anyone who offends you. Remember, the Lord forgave you, so you must forgive others” (Colossians 3:13)

01/01/2023

Happy new year 2023!

02/12/2022

2 December, 2022

Ghana vs Uruguay @03:00PM,
Korea Republic vs Portugal @03:00PM,
Cameroon vs Brazil @ 07:00PM,
Serbia vs Switzerland @07:00PM

iti?

01/12/2022

world cup update
Half time
Morocco 2-1 Canada
Crotia 0- 0 Belgium

01/12/2022

Lero, 1 December,2022

Crotia vs Belgium @ 05:00PM

Canada vs Morocco @05:00PM

Japan vs Spain @09:00PM

Costa Rica vs Germany @09:00PM

Inu mwakwera iti??

Want your business to be the top-listed Grocery Store in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Lilongwe