Torne01
Blessed
Koma Charisma Madness ndiwe dolo
Ndiwe selebu wa original.
Ching'aning'ani musadzipange compare ndi awo mudzagwa mphwayi.
Chifukwa kuti afike alipo simukudziwa kuti anatani kuti mudziwe simupitiriza
Limbikirani basi zonse ndinthawi .
Chachikulu Yehova patsogolo
Poti maso achimalawi timapanga follow anthu ontchuka kale.koma izi padera ndakubwereserani katswiri wina uyu
Ali muproject yotulusa inshallah Ep
Follow him for more
Inshallah EP
Idzakhala ndi nyimbo 7 osati 6 coz imodzi ndi bonus song.
List ya nyimbo idzatuluka pa 18 mwezi uno.
MwanaChe timenyereni hip-hop
Munthu wankulu or Wikise1992 ndi Waxy Kay akudziwa
Wikise1992 ex wandani uyu
Wina afune ,asafune ndimkwatira
Nepman ft ashie boy - Torne01 coming soon
dolo wa maartwork including atulusa kanyu track top skanka
Download yuzing'i this link below๐๐๐ kwatswiri plus
Osamanyoza anthu omwe mwacheza nawo padzana chifukwa chosiyana zochita.ngati muli ndichochita mzanu alibe ndikwabwino kumachezabe ngti kale .amapasa mosiyana
Sichomcho Che Mandota - Dr J.S.Chikakuda
Dolo wamapunch Nyasa-B come back bro
Alan Walker too munch taleted
Happy birthday to GOAT Piksy more years to you ngauzo
Makosana ndi Mikozi mwanatu wakusalimayi sukunvekatu zikuti BWANJI kapena inhouse media yamutula pansi
Alan Walker dj
Ngati umafuna kukhala osangalala pereka moyo wako mwayehova sanalakwisepo ndipo samakhumudwisa zizakhala better Gwamba amapraiser
Dear Sean Morgan Official osankhulupirila munthu panyasa pano chifukwa ngakhale mwini wake wa Tecno Spark amauser iPhone this life no balance
Happy befide youngest king Waxy Kay
Makosana ndi Mafo osaiwala Sean Morgan Official mukuona BWANJI Giboh Pearson Phalombe Musik kumeneko ndkhulupirila mundivomereza achina Nyasa-B
Ndipomwe ndadziwa kuti Mafo ndionabo amapanga zomwe zikumusangalasa
Chomwe ndimadziwa mulungu amatikonda mkona tili ndimoyo leroli ! kumapephera
Who is Dankal cee introduce yourself pliz
Yomweyo aaaah ! yomweyo aa yomweyoooo KA kwnako chani
Dax do you see my post ! I know I can't reach you but you are de legend who can do this for me. Help me with sharing this artwork below
Ndikufunaso ndituluse nyimbo pa. 15 June get ready Mr Gwamba support yanutu bas I'm waiting
Gwamba track imodzi yokha Timenye limonzi ndikufunaso kaja kot oowoooooo kamandiwaza
Wachikondi muli nayeyo mwina ndii ex wa Waxy Kay kapena Jhoofia Dadaking mwinaso Dankal cee nde chomatamikira ndi Chan ngati munamuyamba ndinuyo shupiti zanu
I've received 100 reactions to my posts in the past 30 days. Thanks for your support. ๐๐ค๐
Utha kumapewa kusuta chamba kumwa mowa kuopa kupenga nde umapezeka ukupenga ndi mkazi wagwa nayo ndikunama kapena Sean Morgan Official