Ndingo Brothers Band
One of Malawi's Oldest Acoustic Band,from Nkhoma in Lilongwe District.
Malawi duo hit all the right notes at WES concert | Kewanee Voice Their home is 9,000 miles away, but a pair of young musicians from the African nation of Malawi felt right at home performing their unique sound, produced in part by home-made instruments, for an appreciative audience of 340 students at Wethersfield Elementary School Thursday. The Madalitso Band, a....
Simangeni - Ndingo Brothers Band Simangeni- Ndingo Brothers BandFor more Ndingo Brothers Band music, search Rukuru live.
Simangeni Anapita kwawo.
Simangeni - Ndingo Brothers Band Simangeni- Ndingo Brothers BandFor more Ndingo Brothers Band music, search Rukuru live.
Video ya Simangeni titulutsa mwezi uno.
Pezani nyimbo zathu pa,
https://rukurulive.com/
Nyimbo zathu mu chimbale cha Ndilira bwanji? Komanso Kumabwinja, zikupezeka pa Rukuru live.
Kulipira pa Airtel Money, VISA, Mastercard, Tiago ndi njira zina.
https://rukurulive.com/
Zikomo kwambiri potipatsa mpata kuimba ku Zikomo 2023 Awards kunyumba ya boma.
Zikomo Awards 2023.anatipatsa mpata kuti tionetse luso.
Zikomo kwambiri.
Tafika mu Lilongwe town, posachedwa tikunyamuka wa ku Nsaru ( Chingalire Village),Pakhonde Festival.
Ma CD tanyamulanso, MK 1000 pa CD.
Chingalire Village, tikakhalako, sabata ya mawa.
Ku Nsaru, kwao kwa mfumu Chingalire, ifenso tikakhala nawo Tikaimba masiku onse awiri.
Bwelani tizaonane.
Nkoko ( Malo azakumwa za zipatso) pa City Mall pafupi ndi Police, ma CD alipo, Ndilira bwanji? komanso Kumabwinja.
Zikomo.
Acres Bar and Grill at Gateway Mall, get your Ndilira bwanji? And Kumabwinja CDs.
Feedback/Booking: 0999952495
Barber Village pa Bwandilo pafupi ndi Mafumu shop,ma CD alipo.
Ndilira bwanji komanso Kumabwinja.
Ma CD tikumatumizanso, imbani kapena message;
0999952495.
Kuyesa zida basi " iwe Julie".
Nyimbo imenei ili mu CD ya Kumabwinja.
Imbani 0999952495 kuti atumize CDs.
Zikomo.
Kuyesa zida basi " Iwe Julie Taona"nyimbo iyi, ikupezeka mu CD ya Kumabwinja
Ma CD tikutha kutumiza, imbani 0999952495,Zikomo.
Kuchokera ku Nkhoma,Ndingo Brothers Band, WhatsApp 0999952495.We send you Nyamule diya.
Nyamule Diya (full track) from our new recording,Muipila Njedo, we will release 12 tracks as we go ,2008 recording (Ndilira bwanji) and Agogo, our very old recording on several platforms.
Nyamule,imodzi mwa nyimbo zomwe tikutulutsa posachedwa.