Nothern Vocals
We are a music band based in Mzuzu.
Ife ndi a Northern vocals, tabwera kuti tikupatsireni luso lapamwamba. Posachedwapa tikhala tikutulutsa nyimbo yoyamba ngati gulu. Support yanu tiifuna kwabasi.
Good morning.
Hello people, how are you here?
This is the page guys,,, follow it kuli zabwino. Chonde chonde help us glow the page. Thanks. Amene mwavomera to join am still waiting to see you 🤗😁
Hello people, tilipo koma?
Paja hit song ikubwera can't wait. Tiyeni tifalitse uthenga kwa anzathu apange follow page zabwino zisawadutse. Prëcïøüs Ëm Käy IVZohar ShaunMr WriterDanny Kellz
Hey guys, we have to make it happen before Monday, people must know our page. Friday tiiyakitse moto basi.