MUDZI UWALE

MUDZI UWALE

Solar Excellence, Every Time: With a passion for solar innovation, Mudzi Uwale sets the standards.

20/12/2023

Posachedwapa ife a MUDZI UWALE tikhala tili mmudzi mwanumo ndi Ma Solar osiyanasiyana apamwamba . Panopa dzalani Kaye nvula ndi iyi yayamba kugwayi sitikufuna kukusokonezani.

Photos from MUDZI UWALE's post 15/12/2023

Ma Solar a ma bulb atatu komaso 4 alipo , tiuzeni komwe muli , ka Mtengo kake pang'ono basi tilankhuleni

09/12/2023

OKONDEDWA OMWE MMATSATILA TSAMBA LINO!

Cholinga cha Page lino tsopano , ndikuonenetsetsa kuti anzathu omwe akufuna kumapezako ma solar nkumanyaudako mmakomomu malingana ndi vuto lalikulu lomwe tili nalo Ku Malawi kwathu kuno lakuchepekedwa kwa anthu omwe anakwanitsa kulumikizitsa magetsi a Escom. Mudzi Uwale ndi Compamy yanu yomwe yabwela kuzaonetsetsa kuti aliyese akukwanitsa kugwilitsa ntchito zounikila za makono komaso za mtundu uli onse monga inu mukufunila, kaya ndi ma pump a solar, solar yoti muzigwiritsa ntchito zinthu zomwe inu munagula kale mnyumbamo komaso mukafuna ena aja okhala ndi zinthu ngati TV kapena wailesi pompo muzitha kupezaso kuchokela kwa ife. Cholinga chathu nchakuti tikayamba tikwanitse kukhala ndi ma agent ochuluka mmadela ambiri mdziko muno. Sitisiya wina aliyese paulendowu aliyese azipezako malingana ndikupeza kwake .

OSAIWALA ! MUDZI UWALE, aliyense akhale mowala.

06/12/2023

Dear Valued Followers,

Exciting news! Our page has undergone a rebranding and is now MUDZI UWALE, a dedicated solar company. Our mission is to provide you, our followers, with access to Solar Home Systems and other impactful solar solutions. Together, let's empower thousands to embrace clean energy. If you have any inquiries, feel free to message us in our inbox—we're here to assist.

Best regards,

MUDZI UWALE

Telephone

Website