Solarworks Malawi

Solarworks Malawi

Your Energy,Your Future

09/12/2023

Koma mmene anthu akulimbilana mbale ya mpunga wa nyama eehh 🙌🙌
Leroli Kuli mbale inaso
Musatalikile akasi

08/12/2023

2000222700830518
Tnm user
2161614682604857
Tnm user
2085400016666629
Tnm user
2788016253794130
Tnm user
2120120422902218
Tnm user

Taona kuti anthu atatu anachepa kwambili ndipo taganiza kuti tiyambe motele pufunabe kuthandiza nose omwe mwaitenga gawo kugawa mbale yampungayi...Airtel users get ready

08/12/2023

Mbale yoyamba ya mpunga wa nyama ili motele:
Kungotsitsilatu chintengo ma 20 watts panel kuchoka pa 25 000 kwacha kufika pa 12 000 kwacha 🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥inu Christmas ipose APA?

08/12/2023

Mpunga wa nyama promotion 🔥🔥🔥🔥
Solarworks Malawi
Yafikaso ndi chi promotion mbambande
Aitaneni aneba tikumane Pano 10:00 AM

Photos from Solarworks Malawi's post 06/12/2023

Tukamba Pano customer wathu wa Ku Zomba waitanitsa kale Fridge ndipo anyamata odziwa ntchito yawo athamangilako kale kukagwila ntchito yotamandika 🔥🔥🔥🔥tikuti kulikose kuti Ngweeee ndi Solarworks Malawi

28/11/2023

Muli uthenga wambili muchisangalalo ndipo mwayi umasankha anthu omwe asankha kusangalala munyengo zonse 🤗🤗🤗🤗sankhani kusangalala lero pogwilitsa magetsi a solar ntima uli zii opanda nkhawa iliyonse.
Imbani ma number athu ndipo muzayankhulana ndi ma agent athu omwe azakuthandizani kuyambila 8:00mmawa kulekeza 5:00 madzulo. Lolemba kulekeza lachisanu.ndipo loweluka amayamba 8:00 mmawa kulekeza 12: masana

27/11/2023

Give power to your future
Save money!
Save energy!
Eco-friendly!
Choose Solarworks Malawi
Affordable,Reliable and Durable
Kulikose kuti Ngwee 🔥🔥🔥🔥

22/11/2023

Kunja sikuli bwino uku kutentha koitana thukuta...koitana udzudzu....kothawitsa tulo🙌Mose ulili kudzikupiza usiku onse apapa Solarworks Malawi tangoona zoti Bola tagulitse anthuwa ma fan oyendela Mphanvu ya dzuwa ....apapa simuitanaso udzudzu kapena thukuta koma muitana ntendele chifukwa kantengo kake ndika ziiiii mudziwa kale za Fan 🙌🙌

21/11/2023

Nkuthekatu mmafuna mutapanga business ya nsomba koma nkhawa yanu mumaopa kuti zikuolerani.
Inde kwatentha ndipo business yatentha ndi ya zakumwa zozizila...Poona zosezi Solarwork yakupezelani ma deep freezer oyendela Mphanvu yadzuwa amene Ali opangidwa mochititsa chidwi kwambili 208 Litres capacity ...sizamwanatu mukafuna kudziwa zambili imbani phone pa ma nambala Ali mmunsiwa
09999017311/0887374809

20/11/2023

Kasungu Bonanza


Thank you Kasungu🔥🔥🔥🔥🔥🔥

18/11/2023
18/11/2023

Solarworks Bonanza at kasungu

15/11/2023

Umu ndi mmene anyamata azayambile masewera awo pa 18 NOV munzinda wa Kasungu.
Yolanu FC Vs 11 Spanners FC ndiomwe azayambe masewelawa
Kenaka chidongo FC Vs chankhonzi FC ndiomwe azatsatile ndipo opambana mumasewela azakhala akulimbilana chikho pamapeto pake🔥🔥🔥🔥🔥ukuku sikodzajomba inu!

15/11/2023

🔥🔥🔥Thank you Mibawa 🙌Kasungu tifika ndi Moto macheza ndinma customer anthu ngambwingambwi

Kampani ya Solarworks mu boma la Kasungu akonza mpikisano wa mpira wa miyendo wa ma timu anayi omwe uzachitike loweruka pa 18 November pa bwalo la sukulu la Chankhozi pulayimale.

Malingana ndi m'modzi mwa akuluakulu ku kampani ya Solarworks, Mabuchi Chimaliro wati cholinga cha mpikisanowu ndikufuna kuyamika anthu pogwilitsa ntchito katundu wawo.

A Chimaliro anaonjezela kuti iyiso ndi njira imodzi yotukula masewero a mpira wamiyendo mu delari pomwe anyamata a ma timu'wa azakhala akuonesa luso lawo.

Kampani'yi izaperekaso solar imodzi kwa mtsikana m'modzi yoti izimuthandizila pa maphunziro ake.

Ma timu a Yolanda, Spanners, Chankhozi ndi Chidongo ndi omwe akuyembekezeka kuzatenga nawo mbali pa mpikisanowu.

Phungu wa nyumba yamalamulo ku Kasungu West, Jailous Bonongwe ndi omwe azakhale mulendo olemekezeka pa mwambo'wu.

Ku kampani ya Solarworks ndi kuchimake kwa ma solar, PA system, ma screen ndi zambiri.

Olemba: Duncan Kaonga

14/11/2023

This was dedza 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
We are heading to kasungu this weekend
!!!!!!!

14/11/2023

Tichite motele kuti enaso akondwe
3529856137609861
3307377899273041
6142096849261212
Airtel

14/11/2023

0674106369486886
2301834872531463
Airtel🔥

14/11/2023

Zufunika changu 🙌🙌🙌

14/11/2023

0674837807593375
8314065918608385
8353333833237092
5343679068584858
8353410634465755
Airtel users 🔥🔥🔥🔥

14/11/2023

2515390550354520 tnm
2297199512995236 tnm
2893882688738805 tnm

14/11/2023

Wachangu!!!
2659685035363973
2147263801028711
TNM user

10/11/2023

Kwaomwe amafuna atakhala external agent wa solarworks Ku Kasungu mwayi wanu ozakumana nafe maso ndi maso pa 18 November 2023 inuyo muzangonyamula chaunzika ikamazati 8:00 madongosolo azakhala ayambika🔥🔥🔥🔥🔥🔥

09/11/2023

Plan ya pa 18NOVEMBER kukakankha chikopa pa chankhonzi School ground ikamazati 8:00 mmawa solarworks izakhala yathela kale mu kasungu🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥Sound ili nkati

06/11/2023

Yafikaso nthawi ija🔥🔥🔥🔥Pa 18November Ku Kasungu!!
Solarworks Bonanza 2023 at Chankhozi Ground Tiyeni tikaipatse Moto🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

Photos from Solarworks Malawi's post 24/10/2023

Umu ndi mmene tidamalizira Training yathu ya Renewable Energy Ku Don Bosco kufikila pomwe ophuzila anthu adalandila ma certificate owacgitila umboni za maphuziro awo ndipo tikhulupilira kuti akagwilitsa bwino ntchito ukadaulo omwe adaphuzitsidwa okhudza solar.

19/10/2023

Pomwe Pali Solarworks Malawi sipalephela ma Dance🔥🔥kupanga phokoso ndi ma PA Systems amphanvu.

Photos from Solarworks Malawi's post 19/10/2023

We work as a team and today
We gathered at Don Bosco Youth Technical Institute - Lilongwe Malawi to train the future leaders

19/10/2023

Day 1 of our Renewable Energy Training Don Bosco Youth Technical Institute - Lilongwe Malawi

18/10/2023

Development starts with Mindset change.
Let's Train the Youth!
Let's promote their skills!
Let's change their minds towards development.
Tomorrow we'll be at Don Bosco Youth Technical Institute - Lilongwe Malawi
For the Renewable Energy Training.
From 8:00AM-12:00PM
Your energy your future!

Photos from Solarworks Malawi's post 11/10/2023

VACANCY ALERT!!!
(Technician and Service Repo-Technician)
More details on the flyer
those with suitable qualifications
send you applications to the email:[email protected]
before the 19th of October.
Your energy,Yourfuture.

10/10/2023

Solarworks Malawi.
Your Energy,You future!!!

Photos from Solarworks Malawi's post 25/09/2023

Gift Noah's farewell party!

25/09/2023

Solarworks company considers itself Fortunate to have had Gift Noah who was serving at the Headquarters office from 15th April 2019 till 25th September 2023.
The board members management and staff of solarworks Malawi wishing you all the best!

21/09/2023

Are you an Electrical Engineer in Renewable Energy?
Here is an opportunity special for you,
Kindly send your Applications together with your CV to the email: [email protected]
Deadlines of receiving Applications is 28th of September 2023.
More details on the flyer.

20/09/2023

Mpira usakuphonyeni🔥🔥🔥🔥 Season muimalize mukuonela TV yanuyanu thamangani mukapeze yanu Ku ma shop onse a Solarworks Malawi pa ntengo wa ziiii

19/09/2023

Ayi ma system abweladi🔥💥
Okha a DJ
Okha a Agent
Okha a customer .
APA wangoganiza zotionetsa kuti system anagula ija Bar yake ikuyenda bwino chi ntibu chakeso pompo khaaa sound mwala mwala

19/09/2023

Nkhani yabwino Kwa ma kasitomala athu
Kuyambila pa 28 September kulekeza pa 29 September Solarworks Malawi yakoza maphuziro a "Renewable Energy Training" omwe azachitikile Ku Don Bosco Youth Technical Institute - Lilongwe Malawi mu nzinda wa Lilongwe.
Maphuzirowa ndiaulele ndipo anyamata ndi atsikana akhoza kutenga nawo gawo mumaphuzilowa.
M***a kulembera kudzera Ku email : [email protected]

18/09/2023

Mwadzuka bwanji akasi?
Ife kunotu basi APA
Tadzukila kuwelenga ma system
🤗🤗🤗tipange zoti afike dela lanu

15/09/2023

Tadikila kokwana ...Talimbana nako kulimbana kwabwino APA titha kutsimikizila kwa ma Customer onse, Ma agent nonse komaso ma Shop onse kuti ma System afika 💥💥💥🥳🥳🥳container ndiyomwe ikutsitsidwayi😂😅APA tiyambepo.

SolarWorks! Background

•Company: Modular Solar Home Systems and accessories, sold in Malawi and Mozambique through a Pay-as-You-Go business model. Currently has an install base of close to 25.000 households in Mozambique and Malawi.

•Company background: Founded in 2008 as a spin-off from the TU Delft. Sold over 100.000 solar products to regional distributors in Southern Africa. Changed business model from wholesale cash sales to Pay As You Go (PAYGo)

•Team: Talented team with local expertise and entrepreneurial expertise.

Videos (show all)

Pomwe Pali Solarworks Malawi sipalephela ma Dance🔥🔥kupanga phokoso ndi ma PA Systems amphanvu.
Solarworks Malawi.Your Energy,You future!!!
Solarworks Malawi kulikonse kuti Ngweee!!!!!💥💥💥💥💥💥💥💥💥
A Recap of The SolarWorks Cup held on the 28th of May 2022#solarworksmalawi#YourEnergyYourFuture#solarladies265#youthemp...
Solarworks cup underway in Mikundi Mchinji.

Telephone

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 12:00