B NAY VII

A writer and a graphic designer //
JOBBADECH GRAPHICS

21/02/2023

Class iliyonse mukabwera new comer wa mkazi anyamata ambiri amasanduka ma comedian 🀣 at atamidwe udolo πŸ˜‚

19/02/2023

Anthu aku Zomba zoona kundikakamiza kugula nkhuku yokufa nkumandinamiza k*t ikugona 😭mulungu akuwoneni ndthu πŸ₯±πŸ˜­

18/02/2023

Design your music artworks with us GRAPHICS πŸ‘Š
0882642337 Tikupangiren artwork.

16/02/2023

Atathesa chibwenzi anandinenaso k*ti nyumba yakwathu imafanana ndi toilet πŸ˜”

14/02/2023

Boma pankhani ya chitukuko cha mvula nde likuyesesa πŸ˜”πŸ˜‚

14/02/2023

Za Valentine ndi za satanic πŸ˜‚πŸ€£πŸƒβ€β™‚οΈπŸƒπŸšΆπŸšΆ

12/02/2023

Atangoti amene sanauzidwe lero "I love you" apenga misala. Are you safe or tikakumana ku bin konkoπŸ€£πŸ˜‚πŸ’”

30/01/2023

Kodi chinsaru chakuchigayo chija amachapa nthawi zanji ?? i think cholera akuchokelatu patali πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

29/01/2023

Ngat dzina la mulungu silimakupatsa busy
Talemba mulungu zikomo pondifikitsa nthawi inoπŸ™

28/01/2023

Akazi okongola sikwenikweni kuphoda πŸ™„ koma milambayi πŸ₯Ί Eish 🚢🚢

24/01/2023

Happy birthday to me βš‘πŸ…

07/01/2023

Zikomo ambuye poti tawonaso tsiku la lero ❣️πŸ”₯

05/01/2023

Mkazi km mawu ngt abambo ake πŸ™ŒπŸ€£ ay simunafike achimwene 🀣

31/12/2022

Anthu opanda ndalama tiyen ku overnight tikamwe tea 🀣🀣πŸ₯‚πŸž

29/12/2022

Ndalama mulibe km muli busy kusamba daily,,,azik*taman ndan πŸ™„

06/12/2022

MOROCCO ijayo πŸ”₯πŸ”₯πŸ™Œ

14/06/2022

We learn through mistakes ,km sikumalawi kuno zimenezo aaaπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Want your business to be the top-listed Computer & Electronics Service in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Zomba

Other Graphic Design in Zomba (show all)
Amonya Visuals Amonya Visuals
Zomba

Graphic designing ⚫ Branding ⚫ Marketing 0886900215

Emmanuel Chikonso Emmanuel Chikonso
Zomba

If it's about Media then it Concerns Us. Let us handle that.οΏ½οΏ½οΏ½

FeDu FeDu
Zomba #songani Street
Zomba, @NTONDOQUA

@Frank Donald Maloya β€’Content Creator β€’Rapper β€’Story Teller β€’Songwiriter β€’ Graphic Designer

Elite Designs Elite Designs
Zomba

Your Design is our priority

Plugs Plugs
Zomba

We do website and graphic designing

James Designz 26 James Designz 26
Zomba
Zomba

HGraphics Official HGraphics Official
Matawale
Zomba

Facebook - @HGraphics101 Instagram - @HGraphics YouTube - HGraphics Official #Our Future_Our Design

Creativ Brenz Grafix Creativ Brenz Grafix
Namiwawa Road
Zomba

Graphics designer

CW Designs22 CW Designs22
Malawi, Mwanza & Zomba
Zomba

Kay nitro 03 Kay nitro 03
WhatsApp
Zomba, MAKHUVA

Graffiti