Stay Yeye
https://youtu.be/BMiWdfaKGnc?feature=shared Nfana Wa Yeye
Ndine Stay Yeye Eti! Mumandidziwa ndi Nyimbo iti pa list pó? 😻🥺
Say a prayer for me 😁
Let's go...
Goodness and BBlack SteelSBlack Steelshall follow you all the days of your life....
De repente phá
Weekend ino mpira sindikuwu ona bwino
Lirani mmene mungathere koma mukamaliza,Osadzaliraso pa chifukwa chomwecho
Mukafuna ma artwork osamba
Mupezeni Alisen kalikose mukufuna kamatheka
Pa art yanu
Até já família!
Vamos receber, no Programa tv📺 , o Cantor Stay Yeye. Fique ligado ao melhor do entretenimento e a conversa descontraída com o convidado.
Sábado às 16h.
HAPPY BIRTHDAY MY DEAR SISTER 🎂🥳🎂
I wish you the all best 💗💚
This birthday message isn't enough to express in words the amount of genuine & unconditional love I have for you ❤
Wishing you a very happy birthday to you my dear sister ElenaElenata Samuel AdrianoeElenata Samuel AdrianoaElenata Samuel Adriano
Allah bless You today and always
Vuto laketu mumapanga nane mpikisano ndisakudziwa, nde ndikawinaso mumakwiya!
Aliyense ali ndi nthawi yaketu💪🙏
HAPPY SUNDAY TO ALL MY FANS ❤️ GOD PROTECT YOU 🙏
Bola anzathu zikuk*thekelaniko !!!! 🙃
Ambuye muchite nane💔🥺
Kukhulululukirana ndikwanyatwa. Kusakhuluka kumamupanga kwambiri affect osakukhululukayo. Ambiri anatilakwira k*ti tipeze phunziro linalake lofunikira mumoyo wathu. Koma ambiri amene mukuwerenga uthengawu muli ndi munthu kapena anthu amene mumati simudzawakhululukira.
Kukhululukira munthu wina ndi kuzikhululukiranso wekha. Umakhala ukuzikhululukira pa zisankho zomwe unapanga usakudziwa. Kusakhululukira munthu kumakhala ngati kusadzikhululukira moyo wako onse pazisankho zomwe unapanga usakudziwa. Pena kusakhuluka ndi kuziimba mulandu pa zinthu zomwe zinatichitira. Kukhululuka ndikuzindikira phunziro lomwe munthu okulakwirayo anakupatsa.
Anthu ena anatilakwira asakudziwa. Olakwiridwawenso nthawi zambiri umakhala k*ti palibe chomwe ungapange. Nanga chabwino tinene k*ti inu mukanatani pamene bambo anu ankawakana mai anu ndi inu nomwe? Kapena ukanatani pamene okhala nawo ankakuzuza? Ambiri anapanga zomwe akanapanga malinga ndikaganizidwe ndik*thekera kwao munthawiyo komwe mwina kunali kungokhala chete ndikumazuzikira mumtima.
Enanso amene anatilakwiratu amapanga regret panopa akakhala. Kuteloko umatha kumamusungira mkwiyo munthu ok*ti naye amadandaula tsiku ndi tsiku k*ti anakulakwira. Mkwiyotu paja umafananizidwa ndi khala lamoto lomwe munthu wanyamula k*ti umuotchere munthu amene anakulakwira. Usanamuotchere munthuyo umakhala ukupsa kaye ndi iweyo. Mwinanso munthuyo mpata ozamuotchawo siumadzapezeka.
Aliyense mu moyo wathu amakhala akukwaniritsa mission inayake, k*tikonda ndi k*tiphunzitsa. Yesu anamukhululukira Yudasi popeza Yesu amadziwa k*ti Yudasi amakwanilitsa mission.
Kukhululukatu pena kumadzavuta chifukwa choona ngati kumukhululukira munthu ndiyek*ti ukuyenera uyambenso kucheza naye. Kukhululuka ndikukumbukira zinthu kapena munthu amene anatilakwira mopanda mkwiyo. Ngakhale usadzachezenso naye ndizotheka kumukhululukira. Nkhani ndiyoti ukamukumbukira munthuyo usamakwiye. Izizi ndizovuta koma ndizotheka.
Ndine Stay Yeye
Musana ganize zozipha
Munvele Kaye sizinganveke
😹
KOMA MWASWELA
???
Wonderful Sunday Family
Kumapemphera God Is Good 🙏
KULEPHELA SIKUGONJA 💔💯🙏
Ambuye Kufuna kwanu kuchitidwe 🙏
Nyimbo ikubwelayi ikudana ndi
Abwezi apamaso ngati sidze
Ndimakukonda
😥
Aliyense amatha kukhala ndi chonena, tanenani basi
Izi ndi tchito za Atumiki +258 nde ak*ti abwera kudzakonza zithu kunoko
Guys Kwabwera akulu Awa Atumiki Atumiki +258Atumiki +258
Follow page
Happy birthday p**o
Feliz seu dia crey🎉
Nyimbo ikubwelayi ikundipangitsa kusangalala
Ngati Zeze Kingston
Kodi phekesera ikumveka k*t
Ndikupanga chibwenz ndindan 😂🚶
Kumapemphera musanagone. Kaye Mulungu azimva kukoma ❤️
Mmene kwayakila dzuwa lero ndendende mmene iti iyakire nyimbo yomwe ndikufuna k*tulutsa soon 🔥
Step by step zik*theka
Kuku iwala nde ku kumandi
Chemela
😪🙌💔
Vuto lake mumaona ngati tikunamizila.
Enanu Mumaoneka Bwino Chifukwa Mumagosungidwa
😑
Chikondi chidjadi
Ndi nthenda imangonka i
Kulira kulira
TIYESERE ZIVUTE ZOKHA
The word “I love you” doesn’t matter if the actions doesn’t match the meaning but for some people, instead of saying “I love you” they say:
-Are you really okay?
-You can do it
-Be safe
-Have you eaten yet?
-I believe in you
-Take care
Some people truly love you and care about you but they just don’t know how to express ❤️
My mind
M'MDALITSO SUPHONYA MWINI WAKE.
Mukhale ndi usiku opambana
Não volte só a sonhar, volte a orar! Deus realiza sonho de quem ora.🦅🫀🛐💛
Mfana wa Yeye Vídeo Live mwaganiza bwanji zaku show
Bayala
Ife Timankhala okodwa Thawi
Zonse 😝 Ndi My Sister
Clique aqui para solicitar o seu anúncio patrocinado.
Vídeos (mostrar todos)
Categoria
Entre em contato com a figura pública
Telefone
Website
Endereço
Map**o
NATIONAL