Brian 02
Shake that Boot
Lavida loca โฃ๏ธ
42sh*t๐ฅด
Kms ma lyrics a Phyzix amakhara anzeru kuposa aGuntolah ndan akutsutsa๐คฃ
Kms nzakhara oyamba kumuvotera Prophet Shepherd Bushiri ๐ฅด๐คฃ๐ฏmwina MW kutukuka
Happy new year ๐๐โฃ๏ธ
Mr Jordan flight ๐
Dear God ๐ I want a bright future ๐๐
Amen โฅ๏ธ
Mother's day ! mother's day!๐Gwambaa ndiwapangire chn ๐คง masten anga ๐๐๐จโ๐ฉโ๐งโ๐ฆ๐
Happy mother's day ๐๐๐๐
I love you ๐โค๏ธ๐momie ๐จโ๐ฉโ๐งโ๐ฆ
Bwana 6TH MW mukumamuyalusatu mwanayo kuti munkongoze dollar ๐๐ถ
Achina Gattah Ase munangonenepatu koyamba ndinkaonangat ndiwe chigawenga ๐
Dear Gwamba awonesere mapemphero amalawi Bello wavuta kuno๐๐
'Baby Okokae?'
'Spetlele๐ฅบ'
'Why Golla Barcadi?'
'Ke Birthday Ya Sgafi๐ญ'
My mama don't like you
Beib yuu should go &love yourself ๐๐๐
You'll never live a happy life if you always care about what others think about you
Dax Amen ๐
Dear Gwamba ndaremba kalatayi pokudziwisa zakupambana zamayeso anga,andisakhira ku chaminadi secondary School,pomwe feez ndi 1.5M makolo can't afford to pay that kind of feez it's too much.ndimati ngati kulikotheka ๐ฅบ๐ kundithandiza ......
Ndithokoza mukandiyankha ๐ฅฐ
Amalume kms Mafumu tandiuzireniko kwa Gwamba kuti ndakhoza mayeso a STD 8 ngosowekera feez yokayambira๐
Mafumu UTM imeneo inangozaza ndi anyapala okhaokha tapanga ndife anthusopano mademowoโน๏ธ
Guntolah Iweyoo ndikuthandizire ine .kuvala tunduma zilingati kuchokera ku toilet without using ttttshhuuu๐๐
Penapakeso Amalume Online mukumadandaura kwambir paline pano๐คง๐
Palmer King zikheberenj wena ๐
BRONG MAN
Uyu nde bale wanga osati zinazi
BelloSh*tโ๏ธ
Wtf is happening! yall are going absolutely insane๐ณ28 million ๐ฑ๐ฑ๐ฑ
BriaBrian 02Brian 02
Palmer KingNdikakhara pasi ndikulingarira dzinari limandivekera ngt kutukwana๐๐
president akanati akhare Major 1 Shepherd Bushiri Vic president kukhara Gwamba bwezi magesi asakuvuta๐
Bola kusacheeeeeh! Kukachaaa!mavutoooh kuchulukaaaa ๐๐๐ญ Gwamba utiuzzotan