Offer corazon mtegha mw

Offer corazon mtegha mw

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Offer corazon mtegha mw, Musician/Band, .

01/04/2024

KYC Nyimbo Ase masana ako anali bwanji

19/03/2024

Koma Cozizwa waswerako bwanji masanawa am your top fan Ase koma mukanaimbako ndi ngati munaimbapo kale pliz send me

19/03/2024

Koma pena Gibo Gift Lantosi unja amandionekera ngat geit kaya bwanji๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™

23/01/2024

Amaka Musiq mwasowat momie

07/01/2024
03/01/2024

Koma ine Cozizwa amandiwaza hevy Kaya bwanji kaya

12/12/2023

Rest in peace qeen Zahara๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

10/11/2023

Mastol Makharana anthu inu mulungu azikusungan

21/08/2023

Et Kodi Gwamba ndi blake chontchuka ndichani??? Mikozi tiyankheni๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Photos from Offer corazon mtegha mw's post 28/07/2023

Ma teacher anga I miss you so much
Nyanda Madeit & Thandizo Jezman

23/06/2023

Bro
Henmago

21/06/2023

Dear God help me to know that you are with me in this situation.
Take me away my fear and reassure me that, because I have committed my life to you, your are in control of my circumstances and you know what is the best for me. Help me to trust you God.

20/06/2023

Momie๐Ÿฅฐ๐Ÿฅฐ makhaku??
AmAmaka MusiquAmaka Musiq

17/06/2023

Joe santiago Mw
Funa uyike vest munyimbo yanga.

15/06/2023

NDIWE DUWA

30/05/2023

Success is not final; failure is not fatal: It is the courage to continue that counts. It is better to fail in originality than to succeed in imitation.

28/05/2023

Maloto saletsana

04/05/2023

Ndakusowan anthu inu

26/03/2023

Emm Zibry Mw tinvanetu ukugona bwa???
Za music koma et.

16/03/2023

You better now

13/02/2023

Ase iwe ndi dolo a matha kwambili
Emm Zibry Mw
Shasha umandipanga motivat

11/02/2023

TITLE :MWANA WANGA
ARTIST: OFFER CORAZON MTEGHA MW

Life is not easy ukaitengera utha kuluza /
Nayo moyo kumazichepetsa osapupuluma/
Uzikhara odekha ngati palivuto kumafotokoza/
Ngakhare zimavuta kuti ena akunvetse/
Anthufe timadutsa nyengo zosiya vuto /
Ukanena anthu sathandiza anzako amathawa/
Achibake saoneka papeto ake zimathera infa/
Ndiye ukamwalira ndipamene amabwera /
Ndikumati munthuyo tinkamukonda dziko/
Ndilovuta ena akupita ena akudzipha nawo/
Naf muzatikonda nzimu wathu ukangosowa/
Ndie ndikakhara chisoni chimandipeza/
Kuti nanga Ine bwanji mavutowa kukakhara/
Kukakha ndie tikukakha koma osasitha/
Life is too short ndie sindiopa infa/
Kapena munthu ndimaopa ondilenga namalenga/
Vuto anthu tikukonda moyo kuiwara infa/
Tikukonda chuma kuiwara otipatsayo/
Malo mumukonda namalenga takonda/
Zapadziko za chabe zongotsara

Dziko usalitengere mwana wanga
Uike patsongolo namalenga mwana wanga
Chilichose ndichotheka mwana wanga
Ingokhara odekha ofatsa

COMING SOON

10/02/2023

AS THE PREACHER OF GOD A CALLED CHILD OF GOD DETERMINE OR STRIVE TO BECOME A GOOD CHRISTIAN AND NOT A GOOD PREACHER!!!

10/02/2023

No matter how heavy your problems may be, he says come unto me, I will give you rest, Reach out and touch the Lord take your own blessings. Good evening family and friends

Videos (show all)

Chi video chanyatwa chowoneka bho coming soon ๐Ÿ”œ chiumbuza mbeta๐Ÿ”ฅ video yochoka KWA madara SiSir PatricksaSir Patricks

Website