HillCity Church

HillCity Church

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from HillCity Church, Religious organisation, .

08/02/2022

0999148377

02/07/2021

KODI HEALING SCHOOL NDI CHANI?

Healing school kapena (Sukulu yamachiritso) ndi utumiki wa machiritso wa prophet Ray umene cholinga chake ndikusonkhanitsa pamodzi anthu odwala matenda osiyanasiyanakubwakutaa zina kuti Prophet Ray awapempherere kuti achiritsidwe mu dzina la Yesu Khristu.

Ngati mukudwala kapena mukusausidwa ndi mavuto ena amene mwayesa kupita nao ku chipatala kapena kwa asing'anga koma simunapeze yankho la mavuto anu tikukuyitanani kuti mubwere muzakhale nao pa Healing school yomwe izachitika pa 10 July 2021 Kuyambira 8 kololo mmawa mpa 5 kololo madzulo Healing school izachitikira ku Blantyre kwa Khama kuseri kwa Mudzi Motel pafupi ndi Chigayo cha Mr Chimalizeni

Tikuyitana munthu wina aliyense amene akudwala matenda monga cancer, stroke, diabetes, Asthma, BP, HIV, Khunyu kaya kusabereka ndi mavuto ena kuti mubwere patsikuli kuti muzalandire machiritso.

Titengereponso mwai odziwitsa anthu nonse kuti Healing school ndi yaulele koma tikulimbikitsa munthu wina aliyense amene atazabwere pa tsikuli kuti mulembetse kulembetsaku ndikofunika kuti pokonza dongosolo la chakudya tikonze molingana ndi chiwerengero cha anthu amene atazabwere patsikuli titsindikizenso kuti kulembetsa ulere Prophet Ray samalipiritsa anthu kuti awapempherere machiritso bible limanena kuti munalandira kwa ulere patsaninso kwa ulere Mateyu 10:8

*ZOYENERA KUBWERETSA*

Zoyenera kubweretsa pa tsikuli ndi khadi lanu la kuchipatala kapena ripoti iliyonse yomwe ma dokotala analemba lokhudza matenda amene mukuvutika nao koma ngati mulibe khadi la kuchipatala mungathe kubwerabe ndipo muzathandidwa :

Alendo amene muzachokere ku ma boma akutali mukuyera kutiziwitsa kuti tsiku la healing school lisanafike kuti tikukonzereni malo ogona.

Kuti mulembetse imbani phone kapena tumizani uthenga pa nambala iyi: 0999934744 Ambuye akudalitseni. Zikomo

22/06/2021

Call 0999934744 l 0999148377

13/06/2021

Join us at Blantyre Hill City Church International this Sunday 13th June 2021 for Sunday of Holy Spirit Service and your life will no longer be the same again get us behind Mudzi Motel at Khama in Machinjiri Time:9am don't miss it for anything remember to bring your family and friends see you there!

Photos from HillCity Church's post 29/05/2021
26/05/2021

Jesus said “Every plant not planted by my heavenly Father will be uprooted,
Matthew 15:13

Tonight I stand on the scripture above and with the authority given me by my Father I uproot every evil plant the devil planted in your body, marriage, relationship, business, ministry etc in the mighty name of Jesus!

Videos (show all)

Call 0999934744 l  0999148377

Website