Grace Kwelepeta MP-abiti Malosa

Grace Kwelepeta MP-abiti Malosa

Official page of Grace Kwelepeta MP

01/12/2022

Tisiye nkhaza kwa abambo, amayi ndi Ana. Komanso nkhaza zokupha anzathu achi albino zisiyike.

01/01/2022

Tiwathokoze ana poyesetsa kupita ku national ndi district secondary schools. Chaka chatha tinapangila pa songani tdc Chaka chino tili pa mchengawedi TDC. Thawi 8 koloko.. congratulations...

25/12/2021

Finals finals finals.. mawa tikukapanga malosa select ..bwerani nonseee

11/06/2021

Bwerani tidzasangalale lamulungu lino pa domasi demonstration ground. Nthawi ndi 1.00pm. Kwelepeta select versus red lions.. anong'a akapezekako..

Photos from Grace Kwelepeta MP-abiti Malosa's post 15/05/2021

Wiki yatha oxfam inandipatsa njinga kuti idzindithandiza mayendedwe pothetsa nkhaza za ana, azimayi ndi achikulire ndi amaulumale. ..ndiye lero ndakumana ndi ma social workers onse omwe ali ma child protection workers ndi ma case workers a mwa senior chief malemia.. Talimbikitsana kuti tichotsa ana onse opezeka ma bottle stores komanso tiyendera milandu yonse ya gbv yomwe inafera mazira. Ndi zotheka ku malosa...

Photos from Grace Kwelepeta MP-abiti Malosa's post 14/05/2021

Happy eid mubarak. Lero ndasangalala ndi anthu kwachinyangala motero.. tadya tagawana mphatso ... long live malosa..

Photos from Grace Kwelepeta MP-abiti Malosa's post 17/04/2021

Lero ndinali kwa group chitenjele komwe timakambilana za nkhaza ya achikulile komanso kupita kuchipatala akadwala chifukwa abale athu ambili sakumapita ku chipatala akuti kuopako Jakisoni. Ndithokoze a UN women komanso ufa omwe Atlas trading inatithandiza kuti nkumano wathu ukhale opambana.

Videos (show all)

Tisiye nkhaza kwa abambo, amayi ndi Ana. Komanso nkhaza zokupha anzathu achi albino zisiyike.

Website