Mlambe Free Methodist Church Mvera Dowa Malawi.

Mlambe Free Methodist Church Mvera Dowa Malawi.

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mlambe Free Methodist Church Mvera Dowa Malawi., Religious organisation, .

18/02/2022

One of our branches Mvuo Free Methodist Church wind destroyed the roof we need you prayers.

27/01/2022

Mlambe Free Methodist church programme Misonkhano ya azimayi ndi ya achinyamata malo sadayikidwe,koma masiku okha aikidwa.Choncho board ya kuunika ndi ya achinyamata akhala akutidziwitsa za malo a misonkhanoyo.

26/12/2021

1 Sam 16:7 (Koma Yehova ananena ndi Samuel,Usayang'ane nkhope yake kapena kutalika kwa msikhu wake popeza ine ndinankana iye, pakuti Yehova saona monga awona munthu,pakuti munthu ayang'ana chooneka ndi maso koma Yehova ayang'ana muntima) Nthawi zina akristu timalemekeza zooneka ndi maso timalemekeza maonekedwe amunthu mavalidwe kapena mayendedwe ndikumati mmene akuonekera awa ndi akhristu amphamvu adzapulumutsidwa koma mulungu amalemekeza chochokera muntima mwa munthu, ukhoza kukhala ooneka onyozeka pamanso pa anthu koma ngati mulungu akuona chiyero mumtima mwako ndiwe opulumutsidwa. Choncho akhristu azanga ndibwino tizisamaritsa za muntima kusiyana ndi zimene anthu amaziona pa ife.Ngakhalenso mmoyo wathu wa thupi anthu ambiri akulira kamba koti pamene amasankha zinthu zina mmoyo mwawo monga abwezi ndi okondedwa, anasankha pongoyang'ana maonekedwe awo osati muntima.Choncho pa zisankho zonse zomwe timakhala nazo tiyeni timupemphe Mulungu kuti atitsogolere kuunikira za muntima osati kungokopeka ndi maonekedwe ayi,maonekedwe apusitsa.Pali mitundu iwiri ya zipwete(zipatso),zowawa ndi zozuna,koma simungathe kusiyanitsa zipwetezi pongoziona pokha ayi,kuwawa kapena kuzuna kwa chipwete kumapezeka mkati mwenimweni mwa chipatsochi. Munjira yomweyo simungadziwe kuti muthu uyu kapena zinthu izi ndi zabwino pongoyang'ana, mpemheni Mulungu yemwe amayang'ana mkati mwa munthu kuti akuthandizeni kusankha zinthu zoyenera. Mudzina la Yesu amen.

22/12/2021
21/12/2021

Let us think about this word: John 3:16 For God so loved the world so that he gave his only beggotton son that who ever believes in him should not perish but have an everlasting life. If God loves us in this way let us respond to him by repent our sins,and recieve him in our hearts as Lord and Savior of our souls. It is our prayer as a church that during this cerebration days,many people may recieve Jesus lather than adultery drunkerdness which are contrary to God,s will. May God bless you.

Website