Heaven Promotions Videos

Videos by Heaven Promotions. Strictly for entertainment business and this is an Eastern Region Music outlet..

Ayao pa theba eeh

Click to enable sound Next

Other Heaven Promotions videos

Ayao pa theba eeh

Nsanje si Umuna , mwana uyuyu Greazy Moh Ndamooh ndi nyimbo yatsopano wagwetsayi ndithudi achina Burna Boy amusilira kwabasi eeh πŸ”₯πŸ™Œ Mutu wanyimbo "Alhamdulilla" , tiyen tumupase tikaonere ku YouTube konko https://youtu.be/Lkb_G_hbIek?si=GBnKd_ki9NSRyb5h

Osamadandaula ngati nyengo zanu sizikuyenda bwino, chifukwa chithu chomwe Mulungu adati azapanga painu ndichanu basi, olo ena akukhomeleleni ndichanu basi.

Nyimbo iyi idatchuka kwambiri mmakwalalamu komano anthu samamuziwa yemwe adaimba, nde mwini wake wangoti odi mjambule video.. Dzina lake ndi Zacks Chihana - Mwanalume https://youtu.be/e3Ja7wZK0sY

Anyamata ama Skru Skur abwera πŸ”₯πŸ‘ Uyu ndi KEE GAN & H Flavio ndi kanema watsopano "Gang" ..

You know the song and still single ? Why πŸ˜‚

Nyimbo yatsopano ya Bandera "Elube" πŸ™ŒπŸ”₯ Komatu mwana uyuyu aaah, check the first comment πŸ‘‡

Mwamukumbukira Vinco Max ? Waswa nyimbo yatsopano "Kumusiko Ngwinga".. Akuti magobo wagwiria ndipo akubwelera kumudzi akadye ndalama ndi Makolo. Full Video πŸ‘‰ https://youtu.be/at0u44b7f7E

Mukudalira Ineyo, ndife a Malawi anzanu, tipangeni Comment πŸ˜‚

Basitu ndi Weza yi bwaku Illusion πŸ₯³

Dan Lu ndichani chomwe sadapange chokusangalasani ?? Zoona mpaka kumutuluka ? Pangani changu mukamvere Album yake ya nyuwaniπŸ‘‡

Komatu omwe tikuUser ma Tecno fe tikunyozeka 😒

Magileti ndichani mwati kwenikweniπŸ˜‚πŸ˜‚

"BANDERA, ndichifukwa chani udalengeza kuti wasiya kuimba kenako after week wayambiranso, chidachitika ndichani kwenikwen?" Bandera πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡

Mzungu kulakhula Chiyao momveka bwino kumposa winawake pamudzi pano aaah πŸ˜‚ zimvere chisoni nzanga πŸƒβ€β™‚οΈ