Ali odala iwo amene amva mau amulungu ndikuwachita

Ali odala iwo amene amva mau amulungu ndikuwachita

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ali odala iwo amene amva mau amulungu ndikuwachita, Automotive Service, Rondebosch East, Cape town RSA, Cape Town.

10/01/2024
28/12/2023

Nchifukwa chiyani anthu masiku ano sitikhala ndi chidwi ndi ma post a mau a Mulungu? Kodi taiwala zomwe Mulungu amatichitira pa moyo wathu?...

Buku Loyera Catholic 10/11/2023

Mas. 41 : 1

Ngwodala munthu amene amaganizirako za amphaŵi,popeza kuti Chauta adzapulumutsa munthu wotere
pa tsiku lamavuto. (Tizikhala anthu achifundo ndi anzathu actually omwe alibe kalikonse)

Buku Loyera Catholic

Catholic Bible 28/10/2023

2 Chronicles 7 : 3

Moreover, all the sons of Israel saw the fire descending, and the glory of the Lord upon the house. And falling prone upon the ground, on the layer of pavement stones, they adored and praised the Lord: "For he is good. For his mercy is everlasting."

Catholic Bible

08/08/2022

Iye adzaŵapukuta misozi yonse m'maso mwao. Sipadzakhalanso imfa, chisoni, kulira, kapena kumva zoŵaŵa. Zakale zonse zapitiratu.”
Chiv. 21:4

30/07/2022

LAPANI NDIKUSIYA ZONSE KUTI MULUMIKAZANE NDI AMBUYE

Miyambo 28 ves 13 mau akuti 👉 Wobisa machimo ake sadzaona mwai, koma wakuwavoreza, nawasiya adzachitidwa chifundo.

Abare and alongo anthu ambiri mwai wanu umavuta kuoneka kwainu pazifukwa, kubisa machimo ndikusalapa pamaso pa AMBUYE ndiye tchingo lalikulu pa mwai wanu. komatu kuphwanya ndikuphwasula tchingo ili ndikuvomereza machimo athu nawasiya, ndipo tidzatichitidwa chifundo, pakuti AMBUYE MULUNGU amafuna mtima ogonja ndikuzichepetsa pamaso pake.

Miyambo 28 ves 14 mau akuti 👉 Wodala munthu wakuopa kosalekeza, koma woumitsa mtima wake adzagwa mzoipa.

Abare and alongo khalani oopa MULUNGU nthawi zonse kuti musamagwe mu uchimo, koma ngati muwumitsa mtima posalapa ndikumapangabe uchimo, dziwani kuti mudzakhala mukugwa mmavuto opanda polekera chifukwa simukhalaso muchitetezo cha AMBUYE.

AMBUYE atamandike ndipo akudalitseni pamene mukuwerenga uthengau. Ameen.

Want your business to be the top-listed Autos & Automotive Service in Cape Town?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address

Rondebosch East, Cape Town RSA
Cape Town

Other Automotive Services in Cape Town (show all)
WestCoast Mobile Mechanic WestCoast Mobile Mechanic
35 Neptune Street, Paarden Eiland
Cape Town, 7405

West Coast Mobile auto mechanic - based in the Paarden Eiland area but serving all areas in Cape Tow

Bo Kaap Auto Detailers & Carwash Bo Kaap Auto Detailers & Carwash
12 Oscar Close Westgate
Cape Town, 7785

AM - PM² Services AM - PM² Services
Thomas Close, Grassy Park
Cape Town

Buying and re-selling of cars . Registration . Valuation. Change of ownership . Spray Painting . Pan

SUCCESSFULLYMULUNGISROOFING SUCCESSFULLYMULUNGISROOFING
Cape Town, 1988

HI MY PEOPLE WE ADVERTISING MY PERFORMANCE WORKING WHATSAPP ME ON 0628053493..... WE DO WETERPROOFING AND ROOFING AND TIMBER STRUCTURE AND ROOFING REPLACEMENT AND ASIBESTOS REMOVAL...

Taylor's Auto worx & Car sales Taylor's Auto worx & Car sales
36 Carol Street Lentegeur Mitchells Plain
Cape Town, 7785

Sales and Service of motor vehicles Minor & major repairs as well as licensing and registration of

Gardean Auto Repair & Diagnostics Gardean Auto Repair & Diagnostics
34 Stella Road, Montague Gardens
Cape Town

Professional Auto Repairs & Services (all things car related). Advanced AI Mobile Diagnostics.Try us!

D.E CAR Service's D.E CAR Service's
Cape Town, 7441

All mechanical repairs on all type of vehicle's

Vemach  Repair Services Vemach Repair Services
.
Cape Town, 7441

Vemach Repair Services is a vehicle and machinery solutions company.

Webez Auto Mobile Webez Auto Mobile
Silversands
Cape Town, 7100

''Do not Scrap it, We will fix it'' At Webez Panel Beaters and Accident Repair Centre we hold ourselves to the highest standard of integrity and ethical behavior. We strive to keep...

Ziggy's Auto Repair Ziggy's Auto Repair
48 Pollsmoor Road
Cape Town, 7945

Located at 48 Pollsmoor Rd. We specialise in all types of auto repairs including Engine Repair, Comp

Art Motorsport Art Motorsport
UNIT 13 STELLA PARK 57 STELLA Road Milnerton
Cape Town, 7441

We offer the following services: Software Remaps ECU Calibrations ECU File Services Standalone ECU fitment and Tuning Vehicle Diagnostics Auto Electrical Custom Fabrication Race ...

K & M Engine Rebuilders K & M Engine Rebuilders
Cape Town, 7800