Malawi 24/7

A better malawi for all it's possible.... Talking about politics and other news across the world

22/11/2023

😭😂😂😅😆😉
1. AMERICAN P0LICE STYLE : Allow
the thîèf to çatch you, then you
cåtch the thîèf.
2. CHINA P0LICE STYLE : Chasē the
thîèf until he becomes tirèd then you cåtch him...
3. ĀRAB P0LICE STYLE : K!dn@pp the thîèfs wife and then
thrēåen the thîèf to surreñder..
4. IND!AN P0LICE STYLE : Sing for
the thîèf until he comes close to
you, then çatch them..
5. MALAWIAN P0LICE STYLE : Câtch any person on the
streēt, bē@t him until he agrees that he's a thîèf🙄😂😂😂

My Cutie 😔💝🎁🎀, Any day that I haven't Made you Smile, I myself wøn't be Happy, please Appreciate Me by Just Likîng the post, please Cutie 😢🥺🥺😔😔🙏🙏

07/11/2023

Believe in Jesus name

14/10/2023

Koma team B yapanikatu kuseliku

12/10/2023

Akutitu ayimanso

07/08/2023

Kwa onse omwe takhala now pa page ino, posachedwa tikhala tikugawa na units a Airtel komanso tnm pothokoza pokhala nafe....

Thandizoli akutipasila ndi a samllen investment

07/08/2023

Nyimbo ya FUMBI tiipase ma % angat

07/08/2023

Mkazi= darling, ineyo ndisanamwalire ndikufuna ndikuuzeko izi!

Mwamuna= ayi darling, usamayakhula kwambiri, ukumva ululu.

Mkazi = komabe ndikufuna kuti ndiulule zomwe ndimachita kuti kumene ndikupitako mzimu wanga ukakhale
mumtendere,,,,,, ineyo ndinkaba ndalama zako kumachipasa chibwenzi Changa, komanso mwana tilinayeyu siwako,,, Nthawi inanso ndinakubela gold watch yako kuyika mu handbag ya sister wako cholinga mukangane, koma amene ndinapanga zimenezo ndinali ineyo. sorry darling.

Mwamuna = osadandawula honey,,, zonsezi ndimadziwa chifukwa chake ndinakuyikila poizoni Kuti ufe,,,,ndiye usayakhule kwambili dikira kaye poizoni alowelere.😳😳😳😳😳😳😳😄😄😄😄😄

01/08/2023

Do Pilots sleep during flight? ✈️

The answer is yes!

Pilots are allowed to take a rotational rest for about 45 minutes or depending on the longevity of the journey whenever the workload is light. This obviously helps the two pilots to stay alert during the most crucial part of the flight.

It is not proper for the two pilots to fall asleep as it is a big risk.

However, on 15th August 2022, Two pilots flying a plane from Sudan to Ethiopia fell asleep when the aircraft was 37,000 feet above sea level, and missed their landing.
luck being on their sides, one of the pilots suddenly woke up and subsequently the succeeded in safely landing the aircraft without any injuries.

Bonus:

What happens when a plane run out of fuel in mid air?

An airliner can land if it runs out of fuel. The only difficulty will be finding an airport within its glide distance but if it doesn’t find one, it would need to land anywhere, as the airliner drops from the air diametrically. So it is not like it will fall off just because it has run out of fuel.

Like and follow our page for more stories...... Please share

16/04/2023

Did you know, Bonya can be a pesticide??

04/03/2023

Part 2.

Kufufuza Galimoto.

Tsegulani website ya beforward kenako pitani pamene alemba search ndipo mulembe galimoto imene mukufuna, zikatheka muone imene yakusangalatsani. ndibwino kusankha galimoto imene ili yazaka zaposachedwa kuti msonkho udzakhale otsika.

Kuwerengera Msonkho.

kuti mudziwe mmene mungawerengerere msonkho lowani pa website iyi https://www.mra.mw/tax-update/calculation-of-duty-for-saloons
pitani pamene alemba Duty Calculator and Services, kenako dinani pamene alemba select, sankhano Duty calculator kenako dinani Go.
kenako pamenealemba currency lembani US Dollar, Pamene alemba CIF lembani mtengo wonse wagalimoto wogulira ndi watransport (mtengowu amakulemberaninso pa webusaiti ya beforward pamene alemba CIF) port charge lembani 300 ngati ili saloon (Tiika mitengo yonse mu post yotsatira) pa year of make lembani chaka chomwe galimotoyo inalembedwa ndipo pa Engine Caparcity lembani ma cc agalimoto yanu. dinani calculator ndipo ibweretsa msonkho wagalimotoyo.

Kugula Galimoto.

Kuti mugule galimoto muyenera kutsegula email account, ndipo mutsegulenso account pa beforward podina pamene alemba create account, ngati muli kale ndi account dinani pamene alemba login.

Kuti Akutsitsireni Mtengo.

mukasankha galimoto imene mukufuna dinani pamene alemba kuti buy now, ndiye kuti mugule galimoto motchipa dinani pamene alemba Enter Suppoters ID (BFSID) ndipo mulembepo 2771942 mukatero adzakuchotserani mtengo pogula galimoto.

mukatsimikizira kuti mugula amakutumizira email kapena message yokufunsani tsiku limene mupereke ndalama.

part 3 tiona mmene tingayankhile ma email awo komanso zoyenera kudziwa.
part 4 tiona mmene mungatumizire ndalama komanso kupeza clearing agent.
part 5 tiona mmene mungadziwire pamene galimoto ili komanso tsiku limene ifike.
Part 6 tiona mmene ubwino ndi kuipa kokatenga nokha.
Part 3 Tiona mmene mungapangitsire regster.

BE FORWARD: Japanese Used Cars for Sale 03/03/2023

Part 1.
Ngati mukufuna kugula Galimoto kunja ma website odalilika amene ineyo ndagulako ndi www.beforward.jp komanso www.sbtjapan.com ndiye zoyenera kudziwa ndizakuti magalimotowa amakhala a second hand ndiye zinthunzi zimene amajambula pafupi ndi body kapena mkati Malo amenewo amakhala kuti Ali ndi vuto nde mumayenera kuonetsetsa. Komanso nthawi zina zinthunzi zimene zimaikidwa zimatha kukhala zosiyandi mmene Galimoto ilili ndiye muli ndi ufulu owapempha kuti akutumizireni zinthunzi zagalimotoyo ndipo amatha kukutumizirani pa email kapena pa WhatsApp.

Tipite ku part 2.
Zoyenera kuyangana pogula Galimoto.

BE FORWARD: Japanese Used Cars for Sale Japan used cars exporter BE FORWARD provides a large selection of Japanese used cars to buy directly from Japan. BE FORWARD also exports new and used tuning parts.

11/02/2023

/7News

Director of Public Prosecutions (DPP) Masauko Chamkakala has dropped all charges that were leveled against Anti-Corruption Bureau (ACB) Director General Martha Chizuma.

Chamkakala has confirmed the development to malawi24/7, saying: "after reviewing the case and after consulting the Attorney General, I decided to discontinue the criminal case against Ms Chizuma in line with the prescriptions of the Constitution and other relevant laws."

Chamkakala has said his decision has been made to ensure that the functionality of the ACB is not impeded.

He says, he has already formally communicated his decision to Collen Zamba, the Secretary to the President and Cabinet.

Reported by condra

10/02/2023

14 facts about Malawi🇲🇼

1.Malawi is a landlocked country located in Southeast Africa, bordered by Tanzania, Mozambique, and Zambia.

2.Malawi's official name is the Republic of Malawi.

3.The official language is English and Chichewa.

4.Malawi has a population of approximately 19 million people.

5.The country's economy is primarily based on agriculture, with to***co being the main export crop.

6.Lake Malawi, also known as Lake Nyasa in Tanzania and Lago Niassa in Mozambique, is the ninth largest lake in the world and the third largest and second deepest lake in Africa.

7.Malawi is known as the "Warm Heart of Africa" due to the friendliness of its people.

8.Malawi gained independence from the United Kingdom in 1964.

9.The country's flag features a full red sun with a rising rays on black field

10.Malawi has a diverse cultural heritage, with over 120 ethnic groups, each with their own unique customs and traditions.

11.Malawi is one of the poorest countries in the world, with a significant portion of the population living below the poverty line.

12. Malawi is also known as "The land of the lake"

13.Malawi has a lot of natural resources like forests, wildlife, minerals, and water resources.

14. Malawi has a diverse range of fauna and flora, and it is home to several national parks and protected areas.

Come and visit Malawi and enjoy......

12/11/2022

AIP koma tigula kapena bas tingozisiya

04/10/2022

Kwanuko akuti chani za kulipila kwa mzipatala!!!

21/09/2022

The cycle life... Send ❤️ to your mother

21/09/2022

mukadikira Ukwati woyera muchedwa, ingolowani wokuda omwewo, mudzikayelera momwemo.

21/09/2022

Amen

21/09/2022

2025 tizamenyelanso ufulu kawili after omwe azigogo athu anamenyela 1964

Photos from Malawi 24/7's post 20/09/2022

BOMA LIPELEKA 311 MILLION KWACHA KWA MKAZI WA SAULOS CHILIMA KUTI APITILE KU CHIPATALA

Boma la Malawi lavomeleza ndalama zokwana K311.98 Million (Three hundred and eleven million, nine hundred and eighty thousand kwacha) kuti zigwilitsidwe ntchito ndi Mkazi wa Dr Saulos Chilima yemwe akufunika chithandizo cha Mankhwala m'dziko la South Africa.

Ofalitsa nkhani mu ofesi ya wachiwiri Kwa M'tsogoleri, Pilirani Phiri watsimikiza za nkhaniyi koma wakana kufotokoza matenda omwe aMary Chilima akudwalawo.

APhiri ati ndalamayi ndi 'budget' ya zonse zomwe zifunike pa ulendo wa Mary Chilima opita ku South Africa.

-Naomi Kamiza


/7

20/09/2022

Business is business but the best business is to mind your own business....

20/09/2022

Koma mukuziwa kuti ndalama zimenezi zingagwile tchito yanji???

Malaw

07/09/2022

Americans:Bebe I'm pregnant☺️☺️☺️☺️☺️☺️☺️☺️☺️

Europeans:Bebe I miss my period🥰🥰🥰

Malawians:Gilibati wandiphera tsogolo langa iwe !!!!!!!🥲🥲🥲🥲🥲🥲🥲🙆🏽‍♂️🙆🏽‍♂️🙆🏽‍♂️🙆🏽‍♂️🙆🏽‍♂️🙆🏽‍♂️

28/08/2022

And you continue believing that wwe is real!! 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Shame on you

25/08/2022
24/08/2022

Continue resting in peace our angel.....

13/08/2022

This painting of a young woman breastfeeding an old man in a prison cell was sold for Euros 30 million. The painting may look perverse but the story behind is from historical records.

The poor man was sentenced to "death by starvation" for stealing a loaf of bread during the reign of Louis XIV in France. The woman was his only daughter and the only visitor to his cell. She was allowed to visit him daily but was frisked thoroughly such that no food was taken in.

When after 4 months the man still survived with no weight loss, the authorities were perplexed and started spying on her in the cell and to their utter astonishment found her to breastfeed her father to the fullest sharing her baby's milk. The judges then realizing the compassion and love of the woman for her father, pardoned the father and set him free....

Want your business to be the top-listed Business in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

Amen
Business is business but the best business is to mind your own business....

Telephone

Address

Kenneth Kaunda Street
Blantyre

Other Business Services in Blantyre (show all)
Action Against Poverty Organisation - AAPO Action Against Poverty Organisation - AAPO
Blantyre

our purpose is to deal with social problems

Limbani Captain Bello Limbani Captain Bello
Blantyre

Be yourself

Best Buy Malawi Business Directory Best Buy Malawi Business Directory
Blantyre
Blantyre

Best Buy Malawi Business Directory is a newly established online business listing platform, publishi

Wlllard  vinikira Wlllard vinikira
Nathereza Village At Thyolo District
Blantyre, WISDOM

Onesmus else mughira Onesmus else mughira
Onesmus
Blantyre

HOWA graphics HOWA graphics
0888811213
Blantyre

Video shoting art making

Kucheza ndi kumasuka Kucheza ndi kumasuka
Vbcrashone@gmail. Com
Blantyre

Quavo  Mw king wa Street Quavo Mw king wa Street
Soche Manja
Blantyre

Artkayz Ve Mayz Artkayz Ve Mayz
Naperi
Blantyre, 303

We are the real and trusted dealers

MODIE MODIE
Malawi Lilongwe
Blantyre, 1010

Yebo Yebo
0995215280
Blantyre