Sada Pee

Hip Hop / Afro Dance Hall Artist, $ong Writer & Beat Maker

21/12/2023

Wavuta ndi Hagu Da kuseliku🤣🤣🤣🏃

21/12/2023

Kani A Catholic nu Moyo Wanu Ndi Umenewo Heeeti 🤔🤔🏃

17/12/2023

Ndikunena Pano Wina Wanditchula Kale SWEETIE " 💖💖😍😍🏃🏃

14/12/2023

Reggae Ikuyenda Mu Ubongo😇🤔

13/12/2023

CHIRADZULU TIKUMANE THIS COMING SUNDAY KWA CHIKAONDA TIKATHILE MALOVU PA MIC🎤

Taonani Taonani👻👻On 17th Dec, 2023

10/12/2023

Tizibwezi Tokumana Nonse Muli Ndi Njala 💔💔🏃🏃🏃🤣🤣

08/12/2023

PENA OSAMADIKIRA KUTI ANTHU AKUYAMIKILE 🙏 ...CHOYAMBA ZIYAMIKILE KAE WEKHA 💖🏹

06/12/2023

Pangani press @ muchione chiswa mitima 💔💔😂🏃🏃🏃

06/12/2023

👩 :😭😭😭😭💔💔💔💔

👨 :🤣🤣🤣 amati atani 🎊🏋

Menemo John atangomva k*t mkaz ankamukana uja wapasidwa mimba ndipo ankana

05/12/2023

A Tay Grin Mwazelezeka Ndichikonditu Inu 😍💖😂😂

02/12/2023

Tikunena Pano Wina Akuyamwisa Ndikuchengetera Mbava, 😁😭💔

30/11/2023

Osamamasuka Kwambiri Anthu Ena Ndakuchikamwa👻😈

29/11/2023

Ndathawidwa Pa Ndege✈️ 😭😭Anthu Apita Ku Israel

27/11/2023

Ngati Mufuna Kuziona Pa DP, Ingotengani 4n Ya Okondedwa Anuwo Mukasinthe Pic Muikepo Yanu 😍💖🍑

26/11/2023

Osamandifanizila Ndi Ujeni, Ine Ndine 👌
🏹
$$3D🍁

25/11/2023

Ubwino Wake, We Learn Through Mistakes 🤣

22/11/2023

Basitu Ndangomuuza Kuti Chibwezi Chatha 💔Wayambapo u Black Nina😭😭😭

20/11/2023

Thank Y'all Amene Mwapanga Like/follow Page Yathu, Apapa Tili Pa 2.1k I know Sichinthu Chophweka. So tiyeni tisalekele p***a, tithandizeni kupanga invite anthu ena k*ti nawo athe kupanga follow page yathui Zikomo ❤❤🙏🙏

20/11/2023

Should I Reply Back This Message On My New 📱iPhone??
👩 : Bea I Love U 💗
Kapena Nzosafunikira🤔🤔

20/11/2023

Mumakwanisa Bwanji Kukhala Opanda iPhone 🤔🤣🏃‍♂️🏃‍♂️🏃‍♂

19/11/2023

Pali Anthu Ena Oti Akangoona Message Yako Mu 4N Mwao Amak*tchula Ziwalo Kae Then Nkumayankha Bwino 💔💔


🙌

18/11/2023

Nde Kukula Mutu Ndi Nzeru Zagwilizana Pati? 🤔

17/11/2023

Nthawi Zina M'mimba Mukati Mulire Zochitisa Manyazi 🙌🤣

17/11/2023

MA BEAT OTI AKUMAKHALA NDIKUZOZA KWAPADERADERA 🎹

Sungapale 🙌
Ukafuna Kutero Akumakubweza🏹🏃‍♂️
Morning Y'All ❤❤

12/11/2023

Mukusowekera Kuonera Kae MY PRAYER Music Video.. Mulungu Sakusiyani Chmozmoz 🙏❤

12/11/2023

Amene Simunaioneletu Mundiuza, Fukwa Nde Eeh 💃🕺🤸‍♂️🔥🙌

10/11/2023

Kodi Mwamuyamika Kale Chisumphi Kamba Ka Moyo, Mmawa Uno🙌🙏

(VIDEO NGATI MADZI OKUMWA) 💦❤

08/11/2023

Almost done.. 🎥🎥 MY PRAYER MUSIC VIDEO 🔥👌
Appline 0886767828

🏹🏹🇲🇼🇲🇼

04/11/2023

Ambirinu K**angidwe K**a Shoeless K**akuvutan👟🙌🏃‍♂️🏃‍♂️

03/11/2023

Ak*titu Machenje , Palibepo D apa😂😂🙌🏃‍♂️🏃‍♂️link 📦👇

03/11/2023

Musamangoziwa Kuwatenga Anzanu Kumowa,, Tamawatengankoni Ku Ganyu Nawo Azizisaka Okha🏹🤔😎

02/11/2023

ENA ANALIRA KOMA SANATCHUKE ATAAA!!! 🤣🤣🏃‍♂️🏃‍♂️🏃‍♂️

02/11/2023

Do What U Love, Love What U Do🏹🎵🇲🇼

30/10/2023

Black Nina Mamuna Salira, Puk*tani Misonziyo Muzinka Chisogolo Basi🏃‍♂️🏃‍♂️

30/10/2023

Mawa Zikayenda Bho Tikuka Shooter Video "My Prayer" (NEW SONG)

30/10/2023

My Prayer🙏🙏🙏

24/10/2023

Ndimapusha Hustle From Mkando Mpaka Chilimba//
Ndikamva Mau Anu Mtima Umandilimba//,,,, 🎵🎵

Ikubwera nyimbo yabwino uku 🔥🔥🙏❤❤

22/10/2023

Maloto Omwe Amasanduka Zenizeni,,Mpomwe Walota Ukukoza Penapake😭😭🏃‍♂️🏃‍♂️

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Limbe
Blantyre
Other Artists in Blantyre (show all)
Mlakatuli Victor Chinkango Mlakatuli Victor Chinkango
Blantyre

Upcoming Poet, Story Writer & Comedian

Sy P Mw Sy P Mw
Blantyre

YEYA YEYA Sy P SAIKONDE 🕺 KUWALA MUSIC PRESETS END N D A MUSIC VIBES 🔥🔥🔥🔥🔥🕺💯💯 0886171429

Nogkax di artist Nogkax di artist
Blantyre

Here we got the music for your pain # one time vybz za nyimbo adah!!🎤🎶🎵🎙️🎧🎚️📸🔊🎵🎶🔉🔥🔥🔥

Hashim Kazembe MW Hashim Kazembe MW
Ndirande
Blantyre

Hello my brothers and sisters this is my official page contact me anytime for your suggestions and business Salam alaikum

Tey Gee Tey Gee
Ndilande
Blantyre

TeY Gee...Is a Rapper..Songwritter...Fashion Killa......

Scya ajico Scya ajico
Blantyre

Auxy Mw Official Auxy Mw Official
Blantyre

OFFICIAL PAGE OF MALAWIAN AFRO-DANCEHALL/REGGAE ARTIST AUXY MW

Amos-Julius-Phiri Amos-Julius-Phiri
Lunzu
Blantyre

Harold kandikole Harold kandikole
Blantyre Chileka
Blantyre, BLANTYRE

Arst

Joshua Milos the Artist Joshua Milos the Artist
Blantyre

Art in every direction is true art and that's what we bring.. art is the art to understand art, here is where you get to understand what art is

Indu$try Music Indu$try Music
Blantyre

Official page for Upcoming Hiphop artist Indu$try Music

Siata Mavia Siata Mavia
Machinjiri
Blantyre, JUMBE

MAVIA BWOY 💪