Luso Sport

Trusted source of sports news and updates

05/10/2023

"PHADA AMENEYO SINDIVINA NAWO" - GONDWE

M'modzi mwa akulu-akulu a timu ya Mighty Mukuru Wanderers FC, Chancy Gondwe waulula kuti sapanga appeal chigamulo chake ku komiti yaikulu ya bungwe la Football Association of Malawi ndipo m'malo mwake akamang'ala kubwalo lalikulu la milandu la High Court.

Gondwe walankhula izi poyankhapo pa chilango chimene Iye walandira kudzera ku komiti yosungitsa mwambo kubungwe la FAM potsatira kumupeza olakwa pazomwe anauza tsamba lina lolemba nkhani zamasewero kunena kuti akulu-akulu a mu komiti yosungitsa mwambo anapereka chilango kutimu yake cholipira ndalama zokwana K24.5 million kukhala ngati kuti analedzera.

Kudzera mu chikalata chimene bungwe la FAM latulutsa Lachiwiri, bungweli lalamula Gondwe, amene ndi Mlangizi wa zamalamulo kutimu ya Wanderers, kuti alipire K1.2 million pa milandu itatu imene anamupeza nayo kuti ndiolakwa yomwe ndi kunyazitsa masewero a mpira wamiyendo, kunyazitsa akulu-akulu a bungwe la FAM komanso kuononga dzina la kampani ya Airtel imene ndi mthandizi wa chikho cha Airtel Top 8.

Mukalatayi, FAM linapereka maola okwana 72 kwa Gondwe kuti apange appeal chigamulochi ku komiti yaikulu yosungitsa mwambo kubungwe-li ngati sakukhutira nacho.

Koma polankhula ndi wayilesi ya Times, Gondwe wati alibe nthawi yopanga appeal chigamulochi kubungwe la FAM ndipo m'malo mwake Iye akamang'ala ku bwalo lalikulu la High Court.

23/09/2023

Q. WAS IT A PENALTY OR NOT?

Jaffalie Sanudi: "Pamene anayimba Mwayi Msungama ndinali odabwa kuti wayimbira chani koma nditakaonera kanema wake ndipamene ndinatsimikiza kuti inalidi penalty.

Twaha Silva Chimuka: " Imene ija inali penalty potengera kuti panthawi imene mpira uja amaugwira, mkono wake sunali m'malo mwake [Natural position]

Bullets 1-0 Tigers

23/09/2023

BULLETS YAKANIZA SALIMA KUTSATIRA RONALDO KU SAUDI ARABIA

Katswiri wa timu ya Bangwe All Stars yemwe ali pangongole kuchoka kutimu ya FCB Nyasa Big Bullets, Chikumbutso Salima, sapita nawo mdziko la Saudi Arabia kuti akayese mwayi ku timu ya Al-Faisaly pomwe Bullets yakaniza osewerayu.

Mphatso Jika, mkulu watimu ya Bangwe All Stars, watsimikiza zankhaniyi ponena kuti Bullets silinagwirizane ndi mfundo zina za mundondomeko za ulendowu.

Kutsatira izi, Fanizo Mwansambo ndiamene ayikidwa pam'ndandanda m'malo mwa Chikumbutso Salima ndipo akhale akunyamuka Lolemba likudzali pamodzi ndi Robert Saizi ndi Emmanuel Lino kukayesa mwayi kutimuyi [Al-Faisaly] imene imasewera muligi yaing'ono ya m'dzikolo.

22/08/2023

BULLETS CAUTIONED AGAINST COMPLACENCY

Some football pundits have warned FCB Nyasa Bullets to guard against complacency following their vital CAF Champions League preliminary round 0-2 first leg away win over Equatorial Guinea’s Dragon FC.

The People’s Team host Les Dragons at Bingu National Stadium in Lilongwe this Sunday with a spring in their step courtesy of Gastin Phodo’s brace in Malabo.

However, Bullets legend Kinnah Phiri, who guided the team to the group stages of the continental elite club tournament in 2004, said the TNM Super League champions are not in the comfort zone yet.

He cited as an example the 2021 edition when Bullets beat AmaZulu 1-0 in South Africa, but were booted out after losing 1-3 in the return leg.

Said the former Bullets and Flames coach: “First, let me congratulate them for showing characteristic grit to defy the odds and win by a two-goal margin which is not easy at all.

“But having said that, let me warn the players not to get carried away by the result because football can give you surprises you least expected. So, I urge the technical panel to drum into the players that the battle is not over yet.”

The all-time Flames leading scorer said Bullets need to approach Sunday’s game as if they are trailing.

“It is important that they should approach the game with more hunger,” he said.

On his part, football pundit Parry Chinyama said while the two-goal cushion was vital for Bullets, the win should not get into their heads.

He said: “They have performed beyond expectations, considering how they performed locally before this assignment, provided they should not become big-headed because it can be dangerous.

“If they can maintain the momentum, they will seal the victory here and with home support, they have the potential to win with even a bigger margin.”

But in a post-match interview, Bullets head coach Kallisto Pasuwa said it is important that the players should not throw caution to the wind.

“It’s not a game that we can say we should relax to say we are through to the next round. We need do more to sail through to the next round,” he was quoted as having said by nyasabigbullets.com.

-The Nation-

23/07/2023

BREAKING!

Barca's preseason match vs. Juventus tonight has been cancelled, the club announced.

A significant part of the squad has a viral gastroenteritis.

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Address


Blantyre
1999

Other Sport & Recreation in Blantyre (show all)
Ãtüpëllë Ñk Ãtüpëllë Ñk
Chinyonga
Blantyre, HOMESWEETHOME

Mr Spøtlìght

Fitness Warrior Fitness Warrior
Machinjiri
Blantyre

Fitness first�

Juwii Tropez Juwii Tropez
Ngulud Mission
Blantyre

Onzoh mw "" musician Onzoh mw "" musician
Chikwawa T/a Ngabu
Blantyre

Cupten fantastic thuso Amos wa Lusaka page Cupten fantastic thuso Amos wa Lusaka page
Blantyre

This page focus on football especially super league in malawi

Mthando designs Mthando designs
Blantyre

all made by mthando designs

Hike 4 Fitness Hike 4 Fitness
Blantyre, 4310

We hike for fitness and fun

Malawi sports Malawi sports
Post Office Box 4
Blantyre

Delos mugani Delos mugani
0983664324
Blantyre, 199755

199755

Goat of the week Goat of the week
Blantyre

Trending

Phizo major k banda Phizo major k banda
Phizo @ Pmail
Blantyre