ChiradzuluTeacher Training College Students

Official Page of chiradzulu TTC Students ... private bag 54. For communication and entertainment!

Page of chiladzulo officialy managed by entertainment director .invite your friends to like this page for more updates.

17/10/2023

Happy birthday πŸŽ‚πŸŽ‰ Madam Tadala

15/10/2023

Happy mother's day our lovely teachers and student mothers

05/10/2023

Happy Teachers day

26/09/2023

Akupeleka moni

19/09/2023

Moni a Mwenelu

07/09/2023

Congratulations πŸŽ‰ Semu wa TFAC

07/09/2023

Congratulations πŸŽ‰ Madam Getrude ok your graduation πŸŽ“

24/08/2023

Mwaswela bwanji aphunzitsi

15/08/2023

Henderson Levison. Number 1 pa mayeso a standard 8 Malawi yonse from Nampeya Primary School in Machinga.

We will talk about nsapato ya aphuzitsiyo next time time for today. Congratulations

20/07/2023

Mukukwatilatu aphuzitsi

18/07/2023

Mwaikumbukila man yi?

18/07/2023

Good morning from the most beautiful TTC in Africa 🌍

15/07/2023

Masakasa kuti Pyoooo

28/06/2023

Unduna wa zamaphunziro wati ukuganizira pempho loti uyambe kulola ophunzira amuna m'sukulu za purayimare za dziko lino kuvala ma thalauza.

M'neneri mu undunawu a Mphatso Nkuonera wauza Zodiak Online kuti paakali pano undunawu ukufunsa maganizo momwe ndondomekoyi angayiyendetsere.

A Nkuonera ati akufufuzanso ngati nkoyenera kuti aphunzitsi akazi nawo adziwalola kuvala ma thalauza.

Katswiri pa nkhani za maphunziro a Wesley Mwambakulu wati ku maboma ena nkozizira kwambiri ndipo boma liganizire ana amuna kuti asiye kuvala makabudula.

(by Chikondi Mphande-Dedza:06/28/23)

28/06/2023

WCW
Chrisy Komwe ku Domasi College of education

08/06/2023

TP allowance ikwere ifike pa bwanji.?
Your opinions

18/05/2023

Happy birthday 26th Sir Malinga

18/05/2023

20 pin allowance yaku ma TP mpaka kuzunguza mmuzi monse

18/05/2023

Kumabweza ngongole mazimadamu ndi Sala

Good morning 🌞

05/05/2023

Tapelekani ka fees ko Inu aaah
Account details for czttc
CZTTC
NBM 1001998931
Limbe Branch

04/05/2023

Meet Mateyu IPTE 12 graduate and now Deputy Headteacher. The picture was taken at Hippo Lodge in Lowende where he attended a 10 days workshop.

Kudya ndalama Sala😊😊

30/04/2023

Biggy. Atsogo

30/04/2023

Congratulations πŸ‘πŸ₯³πŸ₯³ Selemani on your wedding day.
Tinalibe Data on that day

23/04/2023

Ichi chinali chi Dolo. Chinakhalapo president wa SRC 4days achichosa

Mackenzie Msiska

Goat 🐐wa IPTE 12

Congratulations, he is now working at department of animal science in the ministry of agriculture

06/04/2023

I remember writing a very good Lesson plan thinking supervisors will come and them not showing up eeeish. Painful

04/04/2023

Hello Ma section Head achinyamata

24/03/2023

Kodi zalowa??

24/03/2023

An appeal has gone out to civil servants to make financial contribution to support the people affected by cyclone Freddy.

In a memo which MIJ Online has seen signed by Collen Zamba Secretary to the President and Cabinet, the contributions should be done in the spirit of 'Tigwirane Manja' as championed by President Lazarus Chakwera.

According to Zamba, the financial contributions come from civil servants except those working in the affected districts from the Southern Region.

Meanwhile, the memo has indicated that those on Grade B and above will be required to pay a minimum of K150 thousand while those of Grade N and below will be required to pay minimum of K500.

The other amounts are; Grade C (K100 000), Grade D (K50 000), Grade E&F (K30 000), Grade G H and I (K10 000), Grade J and K (K5 000), lastly Grade L and M (K2 000).

Zamba has since requested all controling officers to collect all financial contributions in their respective ministries and department and later deposit in the given Bank Account.
-Malumbo Ngwira-

Photos from ChiradzuluTeacher Training College Students's post 22/03/2023

Ati alindi fuso Sala wa🀣🀣

19/03/2023

Deep inside I'm missing Phala nsaname.

19/03/2023

There is a story behind this picture. By just seeing the condition of the chalkboard thousands of stories can be told.

Good morning malawi

18/03/2023

Unduna waza ma phunziro walengeza kuti ophunzira m'maboma khumi omwe akhudzidwa ndi namondwe wa Freddy sabweleranso mkalasi msanga mpaka telemu ya mawa.

Kalata yomwe undunawu yatulutsa yati, undunawu utafunsa nzeru kwa akatswiri; maphunziro awayimitsabe ku sekondale ndiku pulayimale mpaka pa 31 March, 2023 pomwe telemu yachiwiri ikuyenela kutha.

Mneneri ku undunawu a Mphatso Nkuonera wati ophunzira adzabweleranso kusukulu pa 17 April pomwe telemu yachitatu izidzayamba.

Undunawu wati ophunzira omwe akukonzekera mayeso, abwelera ku sukulu pa 27 March, kuti akakonzekere.

Undunawu watinso ophunzira m'maboma omwe akhudzidwa ndi namondwe wa Freddy adzalemba mayeso awo atelemu yachiwiri, telemu yamawa.
(by Andrew Viano - Lilongwe:03/18/23)

18/03/2023

Meet Jasica Cyclone Fredy has made her an orphan and homeless. She is at Nguludi camp here in Chiradzulu. All her parents died due to the heavy rain.

She rescued herself when she was covered with mud (this was a miracle)

She doesn't have a home and someone to Care for her life after the camp.

Let's include her in our prayers. May the Good Lord protect Jasica

17/03/2023

Luciano Muleya, apulumuka lokumbakumba
He wrote """"
Ndiyamike kumwamba populumuka ku ngozi yakudirizika kwa septic tank yomwe inali ku seri kwa nyumba yanga chomwe ndinapondapo πŸ™

Zulo utsiku chama past 8 mwana Joshua anamva Mimba then ndinaganiza zomuperekeza ku toilet yomwe ndinaimanga pamwamba pa septic tank yomwe ndinakumbisa kuseri, and by then munali mutazaza madzi being utsiku sindinazindikire kuti yachita ma crack . Nditafika ndinapondapo uku nditamugwira mwana pa mkono , nthawi yomweyo ndinamva ngati chivomerezi ikulowa pansi , ndinamukankha mwana uja koma force yomukankhira inali yochepa popeza ndinali ndikulowa pansi ndi building yomwe inali pamwambapo ndi slab yomwe tinawaka. Up to now sindikumvesa kuti Kodi anamusomphala ndani mwanayo ndikukamuika pa mtunda , ndikukhulupira ndi angero Ake amulungu . Mwazisomo za ambuye force ya madzi omwe anafwamphuka pansi pomwe khoma limalowa inandinyamula mwamba mene ndimagwa pazenjepo ndinapezeka ndaima pa njerwa zomwe zinagumuka , mwachangu ndinadumpha kukagwera kumtunda , Praise God . Kenako nditaganiza zamwana ndimafunaso ndigwerepo kuti ndimuyang'ana kenako ndinamva voice makutu mwanga kuti tacheuka nditangocheuka ndinamupeza mwana wangoima alibwinobwino . And ine ndinapezeka zovala zouma kumbuyoku only trouse kusogolo ndinangonyowa ndimadzi pang'ono and sindinavulale only ma Scratch pachala . Chodabwisaso denga MOTi lindivindikire linakapezeka lagwa 5metres away from place . Ndaona Angelo amulungu ndithu akutipulumusa this was not me fighting hard for our lives but God himself and his Engels and izi zimachitika tiripo anthu awiri okha and up to now anthu sakuziwa what happened until nditawafotokozera , anthu akafika pamalopo palibe akukhulupira the way paliri . Izi ndizomwe ndingathe kufotokoza koma Zina zimachitika even me I don't understand.

Ngakhale ndingayende mchigwa Cha nthuzi wa imfa sindizaopa popeza ambuye alinane , ndipo imfa sindikuiopa popeza yandirephera , my God is greater and powerful πŸ’ͺ , I can not die b4 my time . Now am at work 🀝

17/03/2023

Sad news. 😭😭😭😭😭

Effie, a teacher at Mikombe Primary school In Thyolo watisiya atagwela mu toilet malingana ndi nvula yosalekeza yomwe yanyowesa nthaka.

Rest in peace Dear Teacher

15/03/2023

Kasupe palipose mu campus muno. Livilivi and shire hostels now Ali ndi misinje yawoyawi near pochapila paja

15/03/2023

Mwa m'boolamu simuli bwino. Mvula yaononga eeeish

15/03/2023

Kwanuko nvulayi idakagwabe? Kuno ku CZ yaima Kaye

14/03/2023

Good night Sir ndi Madam

14/03/2023

Kukakhala kuzolowela phala ndikwanu. Muziweko kugula 🍞 for breakfast iyaaah. Phala mudya Monday next week

Want your school to be the top-listed School/college in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

ModerationπŸ€£πŸ˜ƒ

Category

Telephone

Address

Private Bag 540 Limbe
Blantyre

Other Education in Blantyre (show all)
Ntcheu District teachers Ntcheu District teachers
Blantyre

QUALITY EDUCATION FOR ALL

Snow-White Private Schools Snow-White Private Schools
Naperi
Blantyre

We offer Nursery, Reception, Primary and Secondary Education. Snow-White Schools is situated at CI old zoo and Naperi near Bethel stage.

Help a Needy Childrens  - HNC Help a Needy Childrens - HNC
Blantyre, City
Blantyre, CHILIMBA,SUYA

Let's help childrens to achieve their goals.

MyMan-InMalawi MyMan-InMalawi
Development House, Victoria Avenue, Corner Henderson Street
Blantyre, 312

MyMan-InMalawi is an Africa originated influencer platform that sets young people on a path to econo

Sign Language Inclusive for Development - SLID Sign Language Inclusive for Development - SLID
Manja
Blantyre

Teaching sign language to the nation

2 Wheels 2 School Project 2 Wheels 2 School Project
Blantyre
Blantyre

Helping secondary school students in rural Malawi by providing them with bicycles, repairs, school bags, notebooks and paying for their school fees.

Southern Africa School of Taxation Southern Africa School of Taxation
Blantyre, P.OBOX572BLANTYRE