Mlakatuli kachepatsonga-stonneck matick

Dont judge a book by its cover

22/12/2023

Atakwatidwa ndi Mwamuna wamkulu amvekere
๐Ÿคฃ๐Ÿ™ˆ๐Ÿ’ƒ๐Ÿ™Œ

22/12/2023

Ati "ndiwe nkazi okongola oti sinaonepo dziko lonse lapansi" chonsecho passport ulibe ndiye kwa america umapitako bwanji? Ine Mabodza ayi๐Ÿ˜„๐Ÿ˜„๐Ÿ˜„๐Ÿ˜„๐Ÿ˜ฉ

22/12/2023

๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญNdalama yavuta koma ngati iweo ukudya Mamawa, masana, madzulo usamaiwake kumuthokoza Mulungu๐Ÿ™๐Ÿ’š๐Ÿ’›

21/12/2023

Christmas ya chaka chino palibe zochita gagaga dedede muchimanga ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

20/12/2023

Nazo zitseko zaku bank ๐Ÿฆ zikati zikuyaluse ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™†ngati wangotsika kumene ya kwanyezelera๐Ÿ™Œ๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿง๐Ÿ™†๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

19/12/2023

Kodi ndinu mlakatuli wamkazi wachisodzera?

*FROM YOKANKHA MEDIA TEAM*

*TIKUTOLELA MAINA A ATSUNGWANA OMWE NDI ALAKATULI OKHA OKHA ACHISODZELA*

*PALI CHIKONZELO CHOWAPANGILA SYPHER MWA ULELE*

*KWA MLAKATULI WA CHITSIKANA YEMWE ALI NDIKUTHEKELA ANDIPEZE INBOX ALEMBESE*

AJAMBULILIDWA AUDIO NDIPO PROMOTION ZOMSE ACHITILIDWA,,,

LEMBETSANI KU

+27734482636

NDATHA INE MLEMBI

19/12/2023

Masiku akutsala 12 kuti tilowe chaka china,, ena samaliza nawo koma iwe ndi ine tili ndi moyo wamphamvu pomwe ena ali ku chipatala ena pano chigonere chadzulo sanadzukenso apitirira. Tiyeni timuthokoze mulungu kumupephanso kuti timalizire limodzi chakachi amen๐Ÿ‘๐Ÿ‘

18/12/2023

Amvekere umusiye amene ujaaa..... ๐Ÿ˜Ž

..Mkanaziwa zomwe timapanga tikakhala awiri, simunakayesera kutero sure ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ abwanoni

17/12/2023

Kwa omwe munabwera ku show mwatimvetsa kukoma osanama pitirizani kubwera mukamva kuitanidwa and kwa omwe tinalephera next time tidzakhala limodzi ndidziwa ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅmumve kunyadiridwa nonse

17/12/2023

Mlakatuli uyu Isher Samson lero ndi tsiku lomwe anabadwa komanso akukapezeka nawo ku jacaranda cultural center tatiyeni tikamuthandize kusangalala our Queen of poetry ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

17/12/2023

Kkkkk and you put him on your wall in your house saying that its jesus shame๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

16/12/2023

Zikomo kwambiri nasibeko ,udzandifuna๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ wivi ngati wabisala pamaheji mxeew๐Ÿšถโ€โ™‚๏ธ๐Ÿšถโ€โ™‚๏ธ๐Ÿšถโ€โ™‚๏ธ

Osaiwala mawa ku jacaranda cultural center kuli chi show mbambande guys osaiphonya

C-kay-ft- Azungu Aus-Kay_Lololo-Prod-by-Jay-Emm-Nazzy 15/12/2023

Kufunsira nde sindimatha koma akazi okhawo nde mukamufunse Azungu Aus Kay Mw akuuzani kuti

Chinyimbo cha khisimisi ichi abale anzanga ๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡

Relationship no easy oo. Since 5am my roommate just Dey shout "Listen to me, just listen to me, can u just listen to me".๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ
Listen to my song Lololo ๐Ÿ”ฅ

C-kay-ft- Azungu Aus-Kay_Lololo-Prod-by-Jay-Emm-Nazzy Comment Here

15/12/2023

Best friend of the year โค๏ธ
Mutchuleni Dzina momunyadira๐Ÿ˜ kwacha bwanji?

14/12/2023

Kuli anthu ali mu chikondi nde kuli ena akukakamiza chikondi,ena nde zikuwavutiratu nde kuli anthu ngati ineyo๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ ndakusowani guys tsiku linali bwanji?

13/12/2023

Big shout out to my newest top fans! Mathews John, Memory Kadango, Noria Mataya

13/12/2023

Happy follow-versary to my awesome followers. Thanks for all your support! Olipa Manda

13/12/2023

Kwa omwe muli pa Instagram tiyeni tidzicheza

instagram.com

13/12/2023

Anapangatu regret koma manyazi amagwira sanganene๐Ÿ˜Œ๐Ÿ˜Œ๐Ÿ˜Œ๐Ÿ˜Œ๐Ÿ˜Œ

12/12/2023

Mkazi wanji kumuuza Kuti Chatha osalira kungoti ok or kupelesa๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

12/12/2023

Apa ndipomwe ndatsimikiza kuti anthu timabadwa awili awili ndithu,, kwa neba kwabadwa mwana koma nkhopeyo ndendende ineyo eti? ๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…

12/12/2023

Pa25 December ndpa1 January anthu ambiri amaoneka chomchii ๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด

11/12/2023

๐Ÿ’”๐Ÿ˜ญ BREAKING NEWS | Award-winning singer Zahara has died a painful way. See how she died here๐Ÿ‘‰https://iafrica24.com/ripzahara/

Oyimba wa ku south Africa zahara yemwe anayimba nyimbo yomwe ambiri tikuyidziwa ya loliwe wamwalira may her soul rest in peace ๐Ÿ˜ข๐Ÿ˜ข

11/12/2023

Kwanuko aliko Eliza onenepa? ๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด

11/12/2023

Ndani angadye nsima mitanda iwiri pali chibwezi chake apa? ๐Ÿ˜‚๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚

11/12/2023

Anthu muli busy koma eeee ine dzulo ndati mkaonekere kwa kanjole kenakake ndafika andilandira mwansangala, kenako onse adzatuluka panja. Ndangomva akumfunsa mkaziyo ali "nde tigwire uti wa sienta anabwera dzana uja kapena uyu wachimayala ngati parachute yu?"

Ndangotukukamo nyumbamo pano ndamublocka ndimadana zopusa๐Ÿ˜ ๐Ÿ˜ ๐Ÿ˜ ๐Ÿ˜ 

11/12/2023

Azibambo azanga kodi mukuziwa zoti bubblegum/chewing gum (chingamu) oti watafunidwa kwambiri kenako inu kuzamponda amakumatilira?
Kaya Mwandivesesa kaya๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด? Panopa ndufunikira ma bodigadi koma๐Ÿƒโ€โ™‚๏ธ๐Ÿƒโ€โ™‚๏ธ๐Ÿƒโ€โ™‚๏ธ๐Ÿƒโ€โ™‚๏ธ๐Ÿƒโ€โ™‚๏ธ๐Ÿƒโ€โ™‚๏ธ

11/12/2023

Simphamvu zathu koma chisomo chake kuti tidzuke ndi moyo lero, timuyamikire mulungu

Happy new week guys I love you all

10/12/2023

Times 360 Malawi

Mayi wa zaka 29 Ledina Paul ali pa chisangalalo komanso nkhawa pa chipatala chachikulu cha Ntcheu pamene ali ndi ana anayi a khanda, aakazi atatu ndi wam'muna m'modzi.

Kucha kwa lero, mayiyu anabereka ana asanu pa kamodzi atafika mwezi wa chisanu ndi chitatu, koma m'modzi wa anawa wapitilira.

Mayiyu wati ndi wosangalala ndi m'dalitsowu koma ali ndi nkhawa ku mbali ya chisamaliro cha anawa potengera kuti ali kale ndi ana ena atatu, kusonyeza kuti tsopano ali pa udindo wosamalira ana asanu ndi awiri.

Iye wauza Times 360 Malawi kuti amadalira ulimi kuti apeze zofunikira za tsiku ndi tsiku kotero a kufuna kwabwino amuthandizire ndi mkaka komanso zofunikira zina pa moyo wa tsiku ndi tsiku.

Malinga ndi akuluakulu pa chipatalachi, anawa awagoneka ku magetsi kaamba koti masikelo awo ndi otsika

Mayiyu ndi wochokera m'mudzi wa Mkutumula 1 m'dera la mfumu yaying'ono Mkutumula m'boma la Ntcheu.

Akufuna kwabwino akhoza kufikira mayiyu pa 0994920421.

Wolemba Pemphero Malimba

10/12/2023

NKHANI YOPATSA CHIDWI KWAMBILI.

Panali mzungu wina wa mkazi amene adali ndi mwana wa chaka chimodzi
๐Ÿ…๐ŸŽโ›ฑ๐Ÿ’ฏโคโฃ๐Ÿ’—
komans adali ndi galu. Tsiku lina mzungu adali ndi chidwi akuchokela ku bafa poona momwe galu amasewelera ndi khandalo๐Ÿ’š๐Ÿงก๐ŸคŽโค๐Ÿ’™โค๐Ÿ’ฏโœโœ๐Ÿ™

pamene limangosekera. Mzungu poona izi adayamba kukhulupilira galuyo ndi momwe amachitira ndi mwana yo.๐Ÿ…๐Ÿฅญ๐Ÿฅฆ๐Ÿฅ๐Ÿฅ—๐ŸŒฏ

Mzungu uja adayika chikhulupiliro pa galu uja ndipo nthawi zambiri amamusiya galu uja ndi mwana akamabwera amakhala osangalara kupeza mwana akungosekelera. ๐ŸŽ‚๐Ÿ”ฅโ˜‚๏ธ๐ŸŒŽ๐Ÿ—ฝ๐Ÿฐ๐Ÿ›•๐ŸŽ 

Mwachizolowezi adasiya galu ndi mwana uja iye kupita kumsika koma atabwera madzuro adadabwa kuona kuti mwana uja sakuoneka pamene galu adali ndi magazi kukamwa kwake. โ™ฆ๏ธ๐Ÿช๐Ÿ–ผ๐ŸŽฒ๐Ÿ”ฎ

Mzungu uja adaganiza kuti basi galu wadya mwana uja ndipo adapha galu uja, akupitilira kuyang'ana mzungu kwinaku misozi ya chisoni ikutsik.๐Ÿ’“๐Ÿ’–๐Ÿ’๐Ÿ’Œ๐Ÿ’—

Mzungu atapita chipinda cha pamwamba adazizwa kuona mwana akugon osavulara koma pansi padali chinjok chachikul chitadulidwa ma piece. ๐Ÿงก๐Ÿ’๐Ÿ’—๐Ÿ’–๐Ÿ’–๐Ÿ’–โค๐Ÿ’ฅ๐Ÿ–ค๐Ÿ’ข๐Ÿ’ฏ๐Ÿค

TISAMAWELUZ ANTHU TISADAFUFUZE BWINO CHIFUKWA ENA ATHA KUPULUMUTS MOYO WATHU.๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’จ๐Ÿ’จ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฏ๐Ÿงก๐Ÿ’Ÿ๐Ÿ’—๐Ÿ’”

PALI ANTHU ENA AMENE AMATIKONDA KOMA AKALAKWA CHITHU TIMATHAMANGILA KWAWANJANJA OTI CHITHUCHO SANALAKWE

NGATI UBALE UKUMATHA CHIZAKE CHIKUMATHA MABANJA AKUMATHA KHANI ZINA NDIKUGANIZILANA ZOTI WINA SANAPANGE ๐Ÿ’—๐Ÿ’“๐Ÿ’๐Ÿ’–๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฏ๐Ÿ’”

AMBUYE ATITHANDIZE AMEN AMEN โ›ฑโ›ฑโ›ฑ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅโ˜‚๏ธโ›ฑ.

09/12/2023

A Nzathu December iyii muli pa bill yandani๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿ™„ pangeni TAG

08/12/2023

Ndamusiya pa Sitting room ndati ndikagule Fanta, pobwera ndapeza akuthandiza mayi anga kutukwana a neba Eee akazi enawa๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด

08/12/2023

Ngati waona kuwaka kwa dzuwa, wavala wekha komanso wayenda wekha umuthokoze mulungu pokusamala alinawe cholinga ena sanakwanitse kutero,,, muwerenge afiripi 4 vs 13,,, palibe chomulaka mulungu tsiku labwino.

07/12/2023

Ndee kuli Akazi ena oyitanizana kuti ACHE anthu oipa inu ๐Ÿ˜ญ๐Ÿšฎ

07/12/2023

Mpunga ndeee busy kusakha .koma mwamuna Wa size yanu kukanika kusakha๐Ÿ˜‰๐Ÿ˜‰๐Ÿ˜‰๐Ÿ˜‰

06/12/2023

Nthawi zonse musanapange post chinthu mudzionetsetsa kuti mwalemba spelling molondola pa faceboof pano, coz mukumaoneka ngati mbulitu๐Ÿ™„๐Ÿ™„๐Ÿ™„

05/12/2023

1+1=3

Ngati sinunagwiritse ntchito plastic ๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด bye bye

05/12/2023

Inu amenewo Adona,,mamuna wamwini kumuseva kuti heaven sent? ๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด๐Ÿฅด

Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

Kkkkk and you put him on  your wall in your house saying that its jesus shame๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
I don't know if in africa there is a strong lady like Makhadzi respect to you African queen๐Ÿ˜Œ๐Ÿ˜Œ๐Ÿ˜Œ
Manyau by Wikise1992 apezanso a prophet Habakkuk ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
Ehe๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚zibambwe
Magical Pinga will be with as on 17 December at jacaranda blantyre perfoming his magic live๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ lets meet there๐Ÿฅณ๐Ÿฅณ๐Ÿฅณ๐Ÿฅณ
He wake up and find out that his house was gone ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
Its December ๐Ÿ˜‚
Ati tikuyenera kuvutikatu๐Ÿ˜ข๐Ÿ˜ข๐Ÿ˜ข
Teach a child while she/he is still young๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚they will never disappoint you
Some times do things that will help you๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
When you find someone who care about your feelings just hold on on him
Ati mufera fungo๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Category

Telephone

Address


Chikwawa Road
Blantyre
Other Poet in Blantyre (show all)
Sarah the poet Sarah the poet
Blantyre

Tarzs Diesa_Poetry Tarzs Diesa_Poetry
Dowa
Blantyre

#Change somebody to change the entire universe#

Mulongoti Mulongoti
Blantyre

Unique Poetry stylE

Tikumbuke Harare Poetry Tikumbuke Harare Poetry
Blantyre

A mouthpiece of all poets aiming at voicing their cries to the world

Thoughts on poem Thoughts on poem
Blantyre

we write poems and short stories

Gracious Lungu LG Gracious Lungu LG
Blantyre

For the love of Poems and books

Yanjanani Yanjanani
Machinjiri
Blantyre

[email protected]

Rajab makwale Rajab makwale
Chileka Chikuli
Blantyre

You can earn through your doings....

ESSA INT'L ESSA INT'L
Chileka
Blantyre

Japhali Time Japhali Time
0888686795
Blantyre

Pacer_poetry Pacer_poetry
Kanjedza
Blantyre

Poetry, narration and recitals

BestonJeremy writes BestonJeremy writes
Bangwe
Blantyre