Macheza

macheza everything everything

24/03/2022

Pamudzi pano takulandirani nose omwe mwangotijoina kumene, dziwani kt ndi udindo wa aliyense kupanga post nkhani or dzithunzi .
Masukani

11/08/2021

Mmmm

04/08/2021

Tinasowa kwakanthawi tsopano ticheze bas

29/11/2020

mulibwanji ma landlord!

15/11/2020

2020 ndiye akutha ndichani chomwe takwanilitsa komaso chomwe chatsala kt tikwanilitse.

19/06/2020

Mkaki mmodzi amuna 5 chimenecho chikondi kapena m'eeting ya zokonda amambo?
Mulikuti anthu kodi lero?

14/06/2020

Akazi anu akanadziwa mmene amavutikila barbaman pokumetani kuti muoneke bwino mmmmmmmm akanakusiyani kalekalee

09/06/2020

Zomba mental hosptal
Dokotala:- ukumanva bwanji?
Wamisala:-tsikulililonse ndikumalota anyani akusewela
Anyani akusewela Mpila wamiyendo
Dokotala:-ndikupatsa makhwala sudzalotaso
Wamisala:-makhwalawo mundipatse mawa chifukwa lero akusewela ma final nde ndina beta

30/05/2020

Ndevu zinayenela amagalimotowa osati kumayenda nazo wapasi
mmmmmmmm

17/05/2020

Akazi anga asiya phone patebula koma pabwela message yakuti mbuzi yako ija ili pompo? Ndiye kuti akuweta mbuzi ine osandiwuza?

08/05/2020

Zatha izi mwina tiveko zina mmmmmm

12/02/2020

Malawi walelo

Want your business to be the top-listed Media Company in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Chikunlucky5@gmail. Com
Lilongwe
265

Other Newspapers in Lilongwe (show all)
NewsDay Malawi NewsDay Malawi
Sector 2, Area 47
Lilongwe, 207247

NewsDay Malawi is your news; political, entertainment, music and fashion website from Malawi. We pro

Mayii Malawi Mayii Malawi
Nkhotakota
Lilongwe

Nkhani zomwe zomwe zangochitika...muno mu Malawi....

AVANT Publications AVANT Publications
Off Murray Road, Area 4
Lilongwe

News updates you can trust

The Independent Digest The Independent Digest
P O Box 500
Lilongwe, 00265

The independent is Malawi's leading weekly business newspaper which focuses on cutting-edge, investigative articles cutting across the political, social, and economic divide. Our m...

Sydney Ng'oma mzimba Malawi Sydney Ng'oma mzimba Malawi
Emoneni F, P, School P, O Mzimba
Lilongwe, 197222

ZAUKU NDI UKU ZAUKU NDI UKU
Nkhuff
Lilongwe

Malawi

The Citizen Weekly The Citizen Weekly
The Citizen Towers
Lilongwe

A weekly newspaper published by pan-African media company, African Reporters

Michael Pamwangu Mwangosi Michael Pamwangu Mwangosi
Lilongwe

Malawi together

Exams Result For Msce Exams Result For Msce
Lilongwe

music and videos available

CHIkondi chathu stories CHIkondi chathu stories
Malingunde Hill Side
Lilongwe

CHIKONDI CHATHU stories NDI PAGE YAMUNTHU MODZI DZINA LAKE SOLOMON MDONDWE NDIPO CHOLINGA CHA PAGE INO NDIKUPHUZITSA NDIKUTI TIZAKHALE NDIMALAWI OPAMBANA K

Sighting from a far Newsline Sighting from a far Newsline
Lilongwe

Its a page that will be discussing a lot of trending issues in our country Malawi. Non political pro