Legit Xtra

Entertainment platform which is based in Malawi , promoting your business

17/12/2023

Ana awa achina monikha ati ndi anniversary chomwe chatsitsa nyanga ya njovu ndi chakuti omunawo o biliyati olemba okuti

*I have eaten her since February 2022,and am still eating her*

Monikha has been eaten by biliyati kungodula nkhani

Munyengo ya eating eating ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

17/12/2023

๐Ÿ‘ฆ๐Ÿ“ž: uli kuti kodi ?

๐Ÿง’๐Ÿป๐Ÿ“ž: town umati bwanji?

๐Ÿ‘ฆ๐Ÿ“ž: agogo akufuna ayatsire moto Degree yako ija

17/12/2023

"Zitheka, pakatheka penapake"

17/12/2023

Chingamu choti wina wachitafuna kwambili ukachiponda nde chimakakamila ๐Ÿšถ๐Ÿšถ

17/12/2023

If you want to be a successful artist in the music industry do this below tips.

1. Stand out from the crowd
Work hard
2. Be motivated
3. Learn from other people
Get lucky (by putting yourself out there)
4. Be professional
5. Utilise social media
6. Have a good team and network
7. Work with other musicians
8. Stay humble

As an artist:

9. Have an image
10. Ask people for feedback on your music
11. lay gigs and have a great live act
12 Promote your music offline
13. Grow your audience
14. Work with bloggers
15. Distribute your music effectively

Good morning fam

17/12/2023

Moto ootha gulu sitikoleza pakona๐Ÿค—

17/12/2023

Ati a Ching'aning'ani wo nda father Christmas heyiiiiiiii koma anawa akudziwa kuti mano mulibe olo zoti simungatafune zolimba? Anyways new father Christmas in town

Eeeh follow We For Us Foundation ka, ukunso ma fada Christmas akupezeka ๐Ÿ˜„

17/12/2023

Komanso tuno uja akunyamula katundu olemetsa. Akulemedwa mwana wa munthu ๐Ÿ˜„

17/12/2023

December Yu chonde chepetsani kukwera ma sienta kwaomwe mukumayenda maulendo ataliatali

Ma driver akumathamangitsa kwambiri though imfa sithawika but choyamba pewa Zina zikukupeza utapewa.

Remember kupewa kuposa kuchiza. Nkanatere amawawa chamkatikati

Stay safe

Photos from Legit Xtra's post 17/12/2023

It's now a must to visit Rwanda before marrying ๐Ÿ‘‹๐Ÿ‘‹๐Ÿ˜น๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡

Azibambo mukutipo bwanji?

17/12/2023

โ—โ—โ—โ—โ—so sad ๐Ÿ’”โ—โ—

Mutu wa mtsikana wa zaka khumi wapezeka ukuyandama mu mtsinje wa Nsenjere m'boma la Nkhotakota, patapita tsiku limodzi ng'ona itamugwira.

Apolisi ati Abigail Mkwakwa adakumana ndi ngoziyi pomwe amakatsuka mbale ku mtsinjewu pa 15 December.

Mneneri was polisi ya Nkhunga a Andrew Kamanga wati makolo atadziwitsidwa zangoziyi anathamangira ku polisi ndipo mutu wokha ndi womwe udapezeka ukuyandama mu mtsinjewu tsiku lotsatira.

Apolisi akulangiza anthu kuti apewa kutsuka mbale kapena kuchapa zovala m'mitsinje momwe muli ng'ona.

16/12/2023

Paja ndi December tu uyu nsungi chuma wa bank nkhonde, mwampanga check?? Osaiwala ndi last hope yanutu ameneyo๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

16/12/2023

Stop reporting your cheating husband to his friends. Those are his planners๐Ÿ˜ฌ

16/12/2023

The most embarrassing fruit to eat in public๐Ÿ‘‡

16/12/2023

Fnuny tnihg abuot tihs facbooe uptdae is taht, eevn tohugh wodrs are msesed up facbooe adidcts can sltil raed it.

15/12/2023

๐Ÿ˜‚FACTS ABOUT AFRICA๐Ÿ˜‚....................................................

When our neighbours buy a new vehicle

We either say itโ€™s not the latest or he should have built a house first

We are jealous like that ๏ฟผ๏ฟผ

We withdraw money from atm then count it before leaving

We are cautious ๏ฟผ

We lock our car and then try to open it twice before leaving

We are like that ๏ฟผ

We pay 100k to a witch doctor to know who stole our 10k

We are sometimes crazy ๏ฟผ๏ฟผ

We turn off the volume just to smell whatโ€™s burning

We are like that ๏ฟผ

We never put our car keys or iPhones in our pocket

We are proud ๏ฟผ๏ฟผ

When we go out we turn off the lights just to confuse thieves

We are somehow smart ๏ฟผ

We share beers and ci******es but we donโ€™t share opportunities

We are selfish ๏ฟผ

We are proud to be black though some of our sisters are light-skinned and we like them ๏ฟผ

When the driver is taking an unfamiliar road we remove our earpieces to see clearly

We are just like that ๏ฟผ๏ฟผ

When someone is saying something strange

We remove our eyeglass to hear clearly

We are like that ๏ฟผ

We love and read funny jokes like this one but we never bother to like or comment

We are selfish.

Welcome to Africa

Follow LeLegit Xtratra๐Ÿ™@followerstop fans .....................................................................๐Ÿ‘‰Nรคzzy Jรฑr II๐Ÿ‘ˆ๐Ÿ‘‘

15/12/2023

Away from music

Pamene kwasala maola ochepa kuti chisankho chaku FAM chichitike, kwachitika chinthu chomwe Cha dabwitsa kwambiri.

1. Mmodzi mwa omwe amayenera kukavota nawo wasiyidwa paulendo ochoka ku Blantyre kupita ku Mzuzu.

Khalani pomwepo tikupatsilani zambiri.

๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

15/12/2023

Penapake pa chibwezi paja kumayambanako, zimalimbitsa relationship

Muona bwa ๐Ÿ˜น

15/12/2023

Tchulani nzanu yemwe munayamba kucheza pa fesibuku p***a koma simunakumaneko

Make them feel special ๐Ÿค‘

15/12/2023

Mdani wako ali pafupi nawe, samala!!!

Good morning๐Ÿค‘

14/12/2023

Kudzuka ndi moyo lero ndi chisomo , tithokoze mulungu

Ena amafunitsitsa kuti afike nawo lero koma sanafike , Morning

13/12/2023

Dorothy shonga

12/12/2023

Masiku apitawa Zahara family wrote this ๐Ÿ‘‡

It's been REVEALED, her situation is worse. She's now in an unresponsive state. She's not awake neither speaking.

Vusi Nova confirmed the news.

Worse part, her sisters have taken her bank cards to do shopping for themselves and this has made her fiance to ban them from visiting her and has taken care of the bill.

And now she is. Gone
Rest in peace Zahara ๐Ÿ’”๐Ÿ˜ญ

11/12/2023

We started this brand as a joke , now tili pa over 17,000 organic fans , within 1 solid year , without promoting to big brands, we have been working tirelessly on this brand ...

Although fans engagement has gone down but we are trying our level best to capture fans..

Thanks guys we have clocked 1 year since it's establishment

Share, invite and follow legit Xtra, an upcoming platform Legit Xtra ๐Ÿ™

Thanks guys mwakhala nafe kuchoka last year mpaka pano ๐Ÿ™

11/12/2023

Pop Young anali ku Mzuzu university (mzuni). Achina biliyati sanasiyire pompo koma kumukodola, ndikuyimba nawo

Zomwe wachita camera man eish ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ iwe popizo utionongera ana aku chibwavi

11/12/2023

Mumafikila ndiyotani pa agent mukafuna kutenga k400?๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜‚๐Ÿ–๏ธ

11/12/2023

Apa ndipomwe ndakhulupilira kuti anthufe tinabadwa awiri awiri kwa neba kwabadwa mwana nkhope ndendende ine๐Ÿ™†โ€โ™€๏ธ๐Ÿคทโ€โ™€๏ธ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜‚

11/12/2023

Anayambitsa zolirazi ndi Black Nina kenaka,kheli kheli kuzabwerano madala madala Zeze

Let's introduce crying day pa calendar paja aliyense azilira malingana ndi mavuto ake

Chaizz Againer - Lilongwe City Ep | Ah Shatter 11/12/2023

Chaizz againer kaya agama wayulutsa ep yomwe yapanga dethrone album ya Saint pa number 3 apple music Malawi

Keep streaming mwana osasambayu asambeko ๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡

LILONGWE CITY EP๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ”ฅ??๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ
https://ah-shaatter.elementfx.com/wp/2023/11/14/chaizz-againer-lilongwe-city-ep/

Chaizz Chaizz againerr๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

Chaizz Againer - Lilongwe City Ep | Ah Shatter Stream & Download latest music from chaizz againer lilongwe city ep

11/12/2023

Uyu ndi Nator21 Da Producer yemwe anamikisa nyimbo ya mesa hit song ija ya phophu yang'i ena Amati popizo, Pop young ndi nyimbo zake zambiri

Mumpatsa Ma like angati?

11/12/2023

Anzanu nde ndi awo akukalowa ku banja losililika , inu mwangoti phwiiii muli pa mijedu corner ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Village Journalists ๐Ÿ’”

11/12/2023

Kupambana kwa iweyo sikungasangalatse aliyense

Munthu ndi ovuta , congratulations Zeze and Dorothy Kingston - Cashie Madam๐Ÿ‘๐Ÿ‘๐Ÿ‘

11/12/2023

Ma @followers nonse Mvelani Izi Moyo Ukafika Stage Yoti U Want To Settle Down As A Man.Umayamba Kumvetsetsa Why There Should Be More Qualities 2 A Woman Than Just The Physical Looks.Big Nyash May Be Important To U But Your Kids Will Need A Gud & Luving Mother.Beyond The Sexual Fantasies U Will Need Munthu Oti U Can Build A Gud Home With. Mkazi Oti Amakhala Bwino & Anthu,Be It Your Neighbors, Relatives Or Her Own Pipo.Someone Kind,A Friend To U Moyowu Sumakoma Matsiku Onse.U Need Someone Oti Whatever Life Brings,You Stick Together.Onva Wamvaโ€ฆ

Benito dha legend wrote ๐Ÿ‘†

10/12/2023

@*[100087530373293:0]

Copy and remove ๐Ÿ‘‰*

Boys Only ๐Ÿ˜ฉ๐Ÿ˜ญ

10/12/2023

Bible : don't beat your wife
Quran : don't beat your wife
Court : don't beat your wife
Wife : iweyo lero nde undimeyatu๐Ÿ™„๐Ÿ™„

10/12/2023

Zafika poti munthu kukupatsa 1 1sauzande ukumamuthokoza week yonse๐Ÿ˜ซ

10/12/2023

Ndi nzanu uti angadzuke pakati pa usiku atava kuti kwagwa chigalimoto cha mowa๐Ÿ˜‚

10/12/2023

First born akati alangize amachita kuiwala Zoti nayeso ndi mwanatu๐Ÿ˜Œ๐Ÿ˜Œ

09/12/2023

An one of upcoming platforms in Malawi we here by introduce you our today's woman talk

Today we are Jeding Gloria kadammanja ,

Brief biography

She's An actress, TV personality, she works with some organisations to alleviate and stop women trafficking and gender based violance

She is girls and women role model .
As our culture on this platform we here by congratulate her for her works and efforts she puts in to produce the betterment of women in Malawi ๐Ÿ‘๐Ÿ‘๐Ÿ‘๐Ÿ‘

Osati vutsiru viwiri ivi Monika ndi mnzake uyu Yosefe Wa Legit Xtra Xtraa zochita alibe koma kumangolimba ndi zopanda nzeru zomwe, mukule koma sizoona ayi makamaka iweyo Monika

Want your business to be the top-listed Media Company in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

Pop Young anali ku Mzuzu university (mzuni). Achina biliyati sanasiyire pompo koma kumukodola, ndikuyimba nawo Zomwe wac...
apule kuwalandira choncho anthu mukuenda olusalusa ati ๐Ÿ™Œ
Tipangeni nominate legit fans pa best content creator ๐Ÿ™Tapanga zambiritu even ma leading platforms akhala akuba ma conte...
Iyi ndi leaked audio yomwe mkuluyo amayankhula ndi mkaziyo ndipo mwaukadaulo wathu ife a Legit Eagles taipeza ...audio y...
awa ali ndi chibwana....tikaika ndithu udolo pa zimenezi MUST Watch onelani ndithu osaiwala kupanga share and like ๐Ÿ‘‰MMaf...
jb nayenso uku osaphweketsakoma zonn online ai zikomo๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ
osamataya chinthu ukuchifuna ๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡
kodi izizi nzoyenera pa banja?
ai zikomo kapena kumulomo kwanga mkwakukulu๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ

Website

Address

Lilongwe

Other News & Media Websites in Lilongwe (show all)
NewsDay Malawi NewsDay Malawi
Sector 2, Area 47
Lilongwe, 207247

NewsDay Malawi is your news; political, entertainment, music and fashion website from Malawi. We pro

Chap-Gee Chap-Gee
Mchenga Street A49 Baghdad
Lilongwe

Its all about music..

Magodi Magodi
Area 23
Lilongwe

NO NOISE GANG

Twepol The Dancer Twepol The Dancer
Lilongwe

Break dance videos

Bweka Bweka Investments Bweka Bweka Investments
Lilongwe

A home of story telling and a business centre ,buckle up.

Malawian Patriot News Malawian Patriot News
Chidzanja Road
Lilongwe

_Vacancy, military training,border patrol, peace keeping mission+ to our citizens/May God bless๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผโœŒ๏ธ

Malawi Infotainment Site Malawi Infotainment Site
Lilongwe

Platform Where You Get informative Content, Current affairs & Entertainment News Promo 0997656111

SCORE MW SCORE MW
Lilongwe

Home of Sports News (local and International )

Drip masala Drip masala
Lilongwe
Lilongwe, MUSIC

NEW PAGE MUSIC DRIP MISALA

J-max music J-max music
Mitundu
Lilongwe

THEKA Connections THEKA Connections
Area 43
Lilongwe

WE RUN MUSIC PROMOTING @ AN AFFORDABLE PRICE #THEKAconnections