Mwaswera Daily

Music upload, Current news, Promoter, Graphics designer and Web Developer

Photos from Mwaswera Daily's post 11/12/2023

Congratulations to Smart Vinti and Patricia Liwonde for being crowned Mr and Miss Albinism Malawi 2023-24

Eeeee wamkaziyo ena ati ndi zungu❀️maadmn ambali zakuno adyelela masoπŸ˜…πŸ™Œβ€οΈ

Congratulations, inu amene sanasakhidwe muwauze kuti

Izizi izi sanyanyala πŸ˜…πŸ™Œ

10/12/2023

Koma a Great Angels amayiona pamtali mita ,basitu ayitanitsa pulofeti Shepard Bushiri ,kuti azakayimbe nawo ku show imene alinayo ku BICC, pa 25 December 2023.

Pa thebulo ayikapo 1 miliyoni kuti azawalipila akavomela kuzayimba nawo,awa akukana zowapepha a pulofeti ndalama πŸ™ŒπŸ˜…

Great Angels ndi people's choir inu.

ZAYAHWE Sanyanyala inuπŸ™ŒπŸ”₯

Olemba :Jerefire Kabefuh

10/12/2023

ANTHU AKU MCHINJI INU,ULIKO LELO MPILA WA MAKWALALA INU

Lelo pa 10 December 2023, masewelo alipo, opimana mphamvu, pa bwalo la Walilanji sekondale ,komwe ku mchinji uko.

Kumeneko timu ya Waliranji rangers ,ithambisane ndi timu yachinyata fc, ku masanaku,nthawi ya 2 koloko.

Chotsangalatsa masewelowa ,chakuti timu ya Walilanji, muli osewera ambili amene anayitengela Extreme Fc mu chikho cha tnm supa ligi ,koma timu itafika muligimo, ambili anachosedwa timu ya Extreme fc ndi kenaka anabwela ndi ganizo lopanga Walilanji rangers.

Zampila Sanyanyala πŸ˜…πŸ™Œ

Olemba :Jerefire Kabefu

09/12/2023

WANJATIDWA PONAMIZIRA KUKHALA WA POLISI

Apolisi ya Area 3 ku Lilongwe amanga mphunzitsi wa pulaimale yemwe anapuma pa ntchito, Jonathan Nkhosa wa za 51, pomuganizira kuti amanamizira kuti ndi wa polisi ndi kumatenga ndalama kwa anthu omwe abale awo amangidwa powanamiza kuti awatulutsa pa belo.

Wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Lilongwe a Khumbo Sanyiwa wauza Nation Online kuti mkuluyi wamangidwa dzulo ,lachisanu, munthu wina yemwe anapita kupolisiyo kukaona m'bale wake atadandaula kuti njondayi imamuuza kuti aipatse ndalama.

A Sanyiwa ati wodandaulayu pa tsikuli anakhala pa malo ofikira alendo ku polisiko, pamenepo a Nkhosa anayamba kumunamiza kuti iwo ndi wamkulu wa pamalopo yemwe amatulusa anthu pa belo ndipo adamuuza kuti apereke ndalama kuti m'bale wake atuluke m'chitokosi cha polisi.

Apolisi anakwanitsa kumanga a Nkhosa omwe ndi a m'mudzi wa Bwemba ku Lilongwe komweko, ndipo akaonekera ku bwalo la milandu pa mlandu wonamizira kuti ndiwogwira ntchito m'boma.

Apolisi ati akhala akulandira madandaulo ochuluka kuchokera kwa anthu oti aberedwa ndalama zankhaninkhani kudzera munjira yotere.

09/12/2023

M'NYAMATA WINA WAZIMANGILILA

Ku mawa kuno, boma la Lilongwe, area 30 ,m'nyamata wina wapezeka atazimangilila munda wina,chifukwa cha chibwezi.

Anthu ambili anakhamukila pa malo pamene m'nyamatayu anapezeka atazimagililapo .

Ndipo a Polisi pofuna kuziwa zambili zimene m'nyamatayu wachitila izi, anamupitsa thumba, ndipo anapezamo inivulopu imene munali kalata ,chithuzi cha iyeyo ndi bwezi lakelo ndi chimphatso cha unzika.

Kutengela kalatayo ,yawonetsa kuti m'nyamatayu wazimangilila pa chifukwa cha chikondi (chibwezi) ndi tsugwana wina ku area 30 .

Zikumveka kuti kholo la mwana wa sugwanayo ,silimagwilizana ndi ubwezi wa anawa,poti amafuna mwana wawoyo apitilize maphunzilo ake.

Chodabwitsa choti wozimagililayo, wazimangilila pafupi ndi m'nyumba ya bwezi lakelo, ndipo amene anapitsa thumba ndi amayi abwezi lakelo ,ameneso ali apolisi mu thambi ya zofufuzafuza (CID).

Ma unthenga akumveka kuti m'nyamatayu ndi wa kwa sent.

Zambili timva a Polisi akalakhulapo

Olemba :Jerefire Kabefu

08/12/2023

KUHONGA KWATHEKA - Mr Jokes

"Hello Jokefans, ndafuna ndithokoze kwambiri Prophet Shepherd Bushiri pondipanga support ndi ndalama yokwana 2.5 Million pa show yanga yaku Amaryllis Hotel Blantyre yomwe yachitika lero.

Moyo wanga wagwidwa ndi chimwemwe chodzadza tsaya chifukwa support yotere ndiyaikulu kwambiri Komanso ndiyosowa.

Ine ndikuti Zikomo kwambiri.

Mulungu wodziwa kudalitsa awadalitse a Prophet Shepherd Bushiri, ndikuwaptsa moyo wautali."
Mr Jokes

Photos from Mwaswera Daily's post 08/12/2023

Young Virgins Initiated Into Womanhood In Ogu town, Rivers State, Nigeria

The people of Ogu kingdom in Ogu/Bolo LGA of Rivers State on Saturday celebrated Iria, an ancient ceremony that marks the transition of girls who are usually virgins into womanhood

Young virgins were given certificates by the Ogu council of chiefs for passing through the test.

Iria, is considered a rite of passage for young girls as they reach puberty and begin to mature physically

To pass through the test, the girls must first be virgins which will be checked by women of the town, then they will be kept in a room where they will undergo training on womanhood

After passing through this process, the qualified girls will be given certificates showing that they are now adult ladies ready to marry.

It's an Ijaw ceremony that dates back to the 17th century.

08/12/2023

πŒπ”π“π€π‹π„ πŒπ–π€ππ™π€ 𝐒𝐔𝐄𝐃 π…πŽπ‘ π€π‹π‹π„π†π„πƒπ‹π˜ π˜π„π‹π‹πˆππ† 𝐀𝐓 𝐀 πŒπŽπ“πŽπ‘πˆπ’π“ π–π‡πˆπ‹π„ π‡πŽπ‹πƒπˆππ† 𝐀 𝐆𝐔𝐍

MEDIA personality and talk show host Mutale Mwanza has been sued for allegedly yelling at a motorist while holding a gun, an incident which allegedly left the female victim, who is a doctor at the University Teaching Hospitals (UTH), traumatized.

The complainant, Natasha Mulenga, has complained that the incident left her extremely traumatized and she now wants the Lusaka High Court to order the outspoken entrepreneur to pay her damages for assault.

Court records show that the incident happened on November 5, 2023, when the two were stuck in traffic before the defendant, Ms Mwanza, emerged from her car with a gun.

The statement of claim filed at the Lusaka High Court shows that Dr Mulenga was on the material day driving home when she found a broken-down car in Chainda area and that during the time, traffic was building behind the stationery automobile.
The plaintiff submits that she then decided to keep to her lane and pass the scene in order for the built-up traffic to flow.

But before her vehicle passed the broken-down car, Ms Mwanza had started flashing vehicle lights at the doctor's car and decided the defendant then decided to bypass the broken-down vehicle, joining Ms Mulenga’s lane.

The plaintiff submits that when Ms Mwanza blocked her car, the defendant(Ms Mwanza) then proceeded to disembark from her vehicle while carrying a firearm in her right hand. Ms Mwanza then approached Dr Mulenga's vehicle while shouting at her and banging on her vehicle.

β€œArising from that, the plaintiff suffered extreme trauma, post-traumatic stress disorder, severe anxiety, physiological distress, sleep disorder, experienced recurring nightmares about the event and gastrointestinal upset,” she submits in part.

The doctor adds that as a result of the injury suffered, she had to be placed on a mandatory 10 day medical leave due to diminished concentration and had to see a psychotherapist at the Adult and Emergency Hospital at UTH.

She now seeks damages for assault, among other reliefs.

Credit: Mwebantu

07/12/2023

T.I amenyana ndi Mwana wake

Oimba yemwe anakometsa umoyo wathu ndi nyimbo monga Whatever you like ndi Dead and gone, dzana anapindilana ndevu mkamwa ndimwana wake otchedwa King Harris.

Chomwe chinayambitsa zonse ndikunyasidwa kwa Bambo ake omwe ndi T.I podzudzula nkhalidwe wamwana wakeyo. Kusamvana kunafika poipitsitsa kuti mpaka anayamba kusinthana zibakera kufikira pomwe anawalekanitsa. Podzibakira King Harris anauza gulu kuti T.I sangamuuze chochita chifukwa mmene ankakula iyeyo munalibe mmoyo make chifukwa analeledwa ndi agogo ake ndipo amene angamamuuze chochita ndi agogowo basi osati T.I.

Kusagwirizana pakati pa T.I ndi King Harris kwakhala kulipo kwa kanthawi ndithu komanso kwadzetsa mtsutso pakati paanthu kuti kodi Mwana oleledwa ndi agogo amakhala osaweruzika kapena ayi.

07/12/2023

Mbusa alavulira Nkhosa

Mbusa odziwika bwino Otchedwa Michael Todd analavulira mmanja ndikupaka malovuwo pankhope ya munthu yemwe amafuna madalitso.

Munthu yemwe amalandira madalitsowo anasangalala kwambiri atangomaliza kumpaka malovuwo pankhope pake kuti tsopano walandira madalitso omwe amawafuna.

Mbusa Todd amakhala ku USA ndipo wakhala akupempheretsa maiko osiyanasiyana kuphatikizapo kuno ku Malawi.

07/12/2023

Lil Nas X anyoza Mulungu

Oyimba yemwe ndiodziwika bwino ku USA wotchedwa Lil Nas X watulutsa nyimbo zatsopano zomwe zadzetsa mpungwepungwe maka kuchikhritsu. Mwanyimbo zomwe oyimbayi watulutsa monga "Angels" ndi zina, woyimbayo waikamo zina zomwe akhristu aku USA akwiya nazo kuti zikupeputsa chikhritsu.

Poyankhapo zakudzudzulidwako Lil Nas X wayankha mmaso muli gwa kuti "Mabondo ake siomangogwadira zopusa" anatero pouza newspaper ina. Zomwe zakwiyitsanso akhristu kwambiri chifukwa zikutanthauza kuti onse omwe amagwada popemphera amachita zopusa.

Inu mutipo bwa

Wolemba Ngangi

07/12/2023

Likakuona Litsiro

Mpungwepungwe ukukanika kutha kuchipani cha Dpp. Izi zikupitilira pamene dzulo gulu lina linali ndi nkumano waukulu ku Lilongwe. Dzulo mwa anthu ena oyendetsa chipani cha Dpp osapitilira 23 anakumana ku Golden peacock pomwe amafuna kukwanilitsa zomwe bwalo lamilandu linagamula kuti pakutha pamasiku 90 kukhale kutachitika zisankho.

Pakadali pano tikhonza kunena mosabisa kuti chimkulirano chakula kumeneku ndipo ayamba kuonerana pansi. Zikuonetsa kuti magulu angapo sakumvetsetsana kuti apange chimodzi kumeneku.

Aliyense alitcheru kuti aone mmene zithere. Kodi zomwe zikuchitikazi zimanga Dpp kapena zithetsa chipanichi? Zonse nthawi ndiyomwe izatiuze

06/12/2023

Mpachika CCAP Church choir akuitana nonse okonda nyimbo za uzimu kuti pa 17 December akukondwelera kuti atha zaka 50 akutumikira Mulungu.

Auzeni awowo kuti atengane ndi enawo. Ulendo umenewu ndiwa tonse. poyankhulapo yemwe ndi mmodzi mwa atsogoleri a gululi a Mathews Mchambiza Jolamu anati "Ali okondwera kuti gululi lakwanitsa nthawi yotereyi motsogozedwa ndi Mulungu."

Patsikuli akonza zochitika zosiyanasiyana pamaimbidwe komanso chakudya. Gululi limapemphera pa mpingo wa Mpachika CCAP Church omwe umapezeka kwa Manje ku Blantyre.

Tiyeni tikakhale nawo abale athuwa.

Mpachika CCAP Church Choir

Reported by Ngangi

06/12/2023

MANOMA INU πŸ˜“

Zampila Sanyanyala inu

03/12/2023

Hahhaha Blue Eagle's yachinyaso uku ma Eagle 1 ,Mafco 2
πŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…

Moyale 7
Redlions 0

Khangati Moyale yatulukaπŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…wait tipange confirm

03/12/2023

Ateteza chikho ka chi 5 Maule
First round zinathela kulephelanatso
Congrats FCB NYASA BIG BULLETS 2023 champions

Moyale yachinyaso zigoli 7,ma Eagle

Moyale 7
Redlions 0

03/12/2023

Golden boot ndi makwacha aja zapita kwa Clement Nyondo, it's now confirmed , uyu mukuti Lanjesi watulusidwa πŸ˜…ish congrats Nyondo

Zampila Sanyanyala πŸ˜…

03/12/2023

Moyale 6 tsopano ,komatu Moyale ikagomwetsa zigoli ZIWILI ,Blue eagle's ikaluza ndi Mafco ,ndekuti Blue Eagle's ituluka ish.

ZAMPILA SANYANYALA πŸ˜… Ma eagle abandukatu apa waku chipiku

03/12/2023

Kamuzu Barracks 0-0 Mighty Tigers

Moyale Barracks 5-0 Red Lions
Raphael Phiri 35'
Gasten Simkonda 61, 63, 72
George Nyirenda 68'

Blue Eagles 0-1 Mafco
Peter Katsonga 31'

Bangwe All Stars 2-0 Karonga United
Eric Atsiga 21'(O.G)
Friday Osagie 39'

Civil Service United 1-0 Mighty Mukuru Wanderers
Binwell Katinji 1'

Ekwendeni Hammers 2-0 Dedza Dynamos
Isaiah Nyirenda 38'
Blessings Singini 45+2'

FCB Nyasa Big Bullets 1-1Silver Strikers
Patrick Mwaungulu 58',Stain Davie

Extreme 1-1 Chitipa United
Juctice Honde 4' Ramadan Ntafu 63'

Zampila Sanyanyala πŸ˜…

03/12/2023

Inu tsiku lija labaya lokha, FCB BULLETS kuthambisana ndi Silver Striker's ,pa bwalo la Kamuzu Ku Blantyre.

Komano D jong NDI ana ake kuti anyamule LIGI ,afunika kumwetsa tibu wa zigoli πŸ’”πŸ˜…πŸ™Œ

Komano ZEZE chovalila Red ndi white chani??

Chikazati "Zokhumudwitsa ndi zambili Koma tasakha kusangalala".

ZAMPILA sanyanyala πŸ˜… iyi ligi yatha InuπŸ˜…πŸ™Œ

Olemba : Jerefire Kabefuh

01/12/2023

Throwback Competition

Choose the best song

A) Dj Lomwe ~ Rumours of War
B) Tay Grin ~ Ndalabwe
C) JB ~ Khalapansi

30/11/2023

"Program yopanga recruit anthu opita ku Israel ikupitilirabe ndipo anthu akuyenera kukhara ndizonse zowayenereza, monga passport, age 23 to 35, medical check up report done by ABC, Police clearance at Area 30. Mukapanga izi muli oyenelera kupanga interview ndipo mukachita bwino mulowa mu hall momwe akupanga orientation komwe mukapangeso zinthu zingapo monga kusiyana contract komaso kupanga apply visa.

Kwa masiku awiri kapena atatu tsopano oyendetsa program yi ayimitsa kaye kupanga interview komaso orientation kuti athane kaye ndi Batch 2 yomwe ikuyembekezeka kunyamuka week ya mawa.

Koma mkati moyimitsamu anthu ochepa anayitanitsidwa kuti akapange interview kuti apange fill gap yomwe inalipo kapena space yamu ndege kamba ka zifukwa zina.

Ndipo mwina mawa akulu akuluwa alengezaso zakupitiliza kwa program yi yomwe ikuchitikira ku Golden Peacock.

Ngati mulibe passport yesetsani kuti mukhare nayo pakuti mwayi opita ku mayiko osiyana siyana kukagwira ntchito ukhara ochuruka posachedwapa pomwe Boma likukambirana ndi mayiko angapo."

Gerald Chavez Kampanikiza

30/11/2023

"TATHETSANKONI MAUNDUNA ENAWA"~PAC

Bungwe la Public Affairs Committee (PAC) lapempha President Lazarus Chakwera kuti achepetse nduna zake komanso chiwerengero cha alangizi ake kuti apulumutse ndalama mnyengo ino pomwe dziko likukumana ndi mavuto osiyanasiyana azachuma.

29/11/2023

From 3 December, 2023 all Students who are in secondary school will have an advantage to access free additional education lessons through Cecil Juma's page.

Speaking on this initiative, Cecil Juma who is the founder of the initiative and he also own the Cecil Juma's page explained the reason why he has decided to introduce the initiative.

"Online education is a tool that is being used by many developed countries to enhance learning, like in our case we want to simplify learning by bringing the subjects to students, it has to be their reference point. Students can enhance their understanding by going through our lessons online," Juma explained.

He has underscored the need for students who are in remote areas to acquire the quality education regardless of shortage of teachers in their schools.

On the shortage of gadgets, Juma has said that he know many students mostly in rural areas they will have a challenge when accessing these online lessons because of; lack of proper gadgets but in near future his team is expected to work with schools, government and NGOs on how they can make to tackle this challenge.

In the moment, other two University graduate have volunteered themselves to deliver these lessons and the lessons for the whole week will be uploaded on 6:00pm every Sunday.

The initiative is targeting over 100 thousands students from various secondary schools across the country.

Currently, Juma has emphasized the point that students must attend normal lessons from there respective schools hence this initiative is not encouraging anyone to shun the normal lessons in class.

Cecil Juma graduated in February 2023 from Malawi University of Business and Applied Sciences (Mubas) with the Bachelor of Science in Electromechanical engineering.

Reported By Francis Maonjera _Balaka

27/11/2023

Indeed

CHIDZIWITSO

A Mwaswera Daily akuitana tonse amene tili ndi chidwi cholemba nkhani, kaya ndife atolankhani koma tikungokhala, kaya siiwe mtolankhani koma uli ndi chidwi cholemba nkhani, ife a Mwaswera Daily tikukupatsani mwayi olemba nkhani pa page yathu.
Osabisa lunso lako ayi cholinga chathu tikufuna kubweletsa poyera malunso obisikawo.
Amenenso mumatsata zamasewero komanso za msangulutso mukuyitanidwa.

Contacts
Whatsapp +265897472297 (osayimba)
E-mail [email protected]

NB: Iyi si ntchito ndipo sitikulemba ntchito wina aliyense koma kukuyitanani ku platform imene ikabweletse luso lanu lobisikalo kumanso kwa anthu ochuluka.

Regards

26/11/2023

FCB Nyasa Big Bullets are through to the finals of Airtel Top 8 Cup after beating BLUE Eagles FC, three goals to two

Congrats

26/11/2023

UZIMU VIBES AWARDS 2023 WINNERS LIST

Best Male New Artist: Tact

Best Female New Artist: Janet Navaya

Best Male Artist: Simplice Bless

Best Female Artist: Debbie Ntopa

Best Producer: Andy Mponya

Best Music Video: Hallelujah by Stevie Wazisomo Muliya

Best LIVE Act: Kondwani Chirwa

Best Contemporary Artist: Madalitso Banda Vocalist

Song of the Year: Lero by FREE Worship Malawi ft. Simplice Bless

Best Praise/Worship Song: Lero by FREE Worship Malawi ft. Simplice Bless

Best Personality (General): Rudo Mkukupa Chakwera

Best Media Personality: Stevie Muliya

Best Women's Choir: Chinsapo Sweet Melodies Choir

Best Album: Nsembe by Princess Chitsulo

Best Hip Hop Artist: Phronee99

Best Hip Hop Song: Oluwa by David Kalirani

Best RnB/Afro Artist: Theresa Phondo

Best RnB/Afro Song: Blessings by Theresa Phondo

Best Collaboration: Kokoliko by Mastol ft. Faith M***a & Shammah Vocalz

Best Duo/Group: Kelvin Sings & Beracah
Lifetime Achievement Award: Apostle Chitheka Louis

26/11/2023

MASO AWARDS 'WINNERS' FULL LIST 2023

1. Best Male Artist: Zeze Kingston

2. Best Female: Temwah

3. Upcoming male: Pop Young

4. Upcoming female: Lady Aika

5. Best Duo: Aidefest n Kineo

6. Song of the year: Loss by Kell Kay ft ELI Njuchi & Mfumu Hyphen

7. Video of the Year: Tchaa by Tay Grin

8. Gospel Act: Shammah Vocalz

9. Best Album: Ah Yahmi by Saint-Realest

10. Best Collabo: Loss by Kell Kay ft Eli Njuchi n Hyphen

11. Hiphop Act: Bee Jay and Ace Jizzy

12. Dancehall Act: Malinga Mafia

13. Best RNB/pop Act: Driemo

14. Afro Soul/Jazz: Praise Umali

15. Best Live Act: Zeze Kingston

16. Best Producer: Tricky Beatz

17. Sound Engineer: Shadrech Kalukusha

18. Video Director: Essim

19. Media Personality: Super DT

20. Best Club DJ: Vj Ice

21. Gospel Song of the year: Blessings by Theresa Phondo

22. Best Fashion Designer: Ranks45

23. Female Model: Elshadai Masauli

24. Best Comedian: Ching'aning'ani

25. Graphic designer: Half Past

26. Dancing group: Adobe dancing crew

27. Social Media content creator: Chippie

28. Best Poet: Robert Chiwamba

29. Best Photographer: Breezing PiCtures

30. Best Visual Artist: Tapiwa Tee Mlinga

31. Best Corporate Event Sponsor of the year: Ekhaya

32. Best Corporate art promoter/ Procurer: TECNO Mobile

33. Innovative Entrepreneur of the Year : Schizzo Thomson

23/11/2023

TNM SUPER LEAGUE RESULTS

MIGHTY WANDERER'S 0
TIGER'S 0

DEDZA 1 (CLEMENT NYONDO)
BULLETS 0

SILVER 2 (P.MACHESO, C.IDANA)
K BARRACKS 1(OLSON KANJILA

OLSON KANJILA, UJA WACHINYATU YA SILVER ,ENA AKUTI BOLA ANAKACHINYA YA TUNISIA IJA.

CLEMENT NYONDO WA DEDZA 15 GOALS LELOSO WACHINYA

BULLETS NDI MIGHTY WANDERER'S CHONDE ZAMPILA SANYANYALA πŸ˜…πŸ™Œ

HAND WRITING INSIPIRED BY SOURTH BEND JB

Olemba: Jerefire KabefuhMwaswera Dailylyra Daily #

23/11/2023

MWINA TIMAVUTIKA
Mwina timavutika pa nyanja ya nsautso,
Ndi namondwe akuopsa amalondola dzuwa,
Koma m’dziko langwiro zitachoka nkhunguzo,
Tidzazindikira bwino patsogolo

Chorus
Patsogolo mmene mawa abwera,
Pamene oyera adzafika kwawo,
Tidzanena nthano tagonjetsa bwanji,
Tidzazindikira bwino patsogolo.

Zofunika zinthuzi nzosoweka m’dzikoli,
M’thupi njala ndi usiwa m’munda mulibe m’mela
Tikhulupire Mbuye, ndi malinga ndi Mawu,
Tidzazindikira bwino patsogolo

M’mbali zonse zovuta nzosazindikirika,
Njira zosiyana zonka ku dziko la lonjezo,
Mlungu adzatisunga mpaka tsiku la imfa,
Tidzazindikira bwino patsogolo

Ife mwina tigwidwa ndi msampha wobisika,
Mtima upweteka tikanena Mawu olakwa;
Tikafunsa chifukwa chomwe timayesedwa,
Tidzazindikira bwino patsogolo



Good morning

23/11/2023

Kuyankhura Kwa Bon kalindo pa zionetsero zomwe zinachitika mu mzinda wa blantyre ati kudana ndi kuti a city council azilanda malonda Kwa ma vendaπŸ™„

22/11/2023

Wachikwapula chi Thuminitsi
Strongingo ft Jay Jay Cee

Watch full video here

22/11/2023

"NDIPITILIZA KUYIMBA NYIMBO ZOSIYANASIYANA" ~SINDIZO

Nyamata yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti 'Sindizo' pa zoyimbayimba wati iye apitilira kutulusa nyimbo zosiyanasiyana komanso kuthandizira ena omwe akuyamba kumene kuyimba.

Sindizo wanena izi pomwe posachedwapa wamaliza maphunziro antchito ya chitetezo chakundende (Correctional Officer) ku Mapanga Prison Training College.

"Pano ndine Correctional Officer ndipo timaziwika bwinonso kuti Prison Officer/Warder. Mtsogolomu ndikuganiza zopeza ndalama kuti ndijambule nyimbo zanga komanso ndithandize achinyamata aluso la mayimbidwe," Sindizo watero.

Kudzera mu kuyimba woyimbayu anati wapeza Phindu lalikulu monga kupeza ndalama akayitanidwa kukayimba Malo osiyanasiyana kuphatizikapo kupanga maubale ndi anthu ambiri.

"Ndayimbapo malo ambiri maka mu Zomba, ndinakayimbapo ku mpikisano wa zoyimbayimba wontchedwa 'Dolo Wa Mu Hood' ku Blantyre nthawi imeneyo, malo ena omwe ndayimbapo ndi monga ku Balaka, Liwonde, Ntaja, Thyolo ndi ena," adatero Sindizo.

Malinga ndi woyimbayu, dzina lake lenileni ndi Sindizo Sindiwe Simple Chaputula ndipo iye anayamba kuyimba m'chaka cha 2013 komanso kwawo ndi ku Malowa m'mudzi wa Chilemele mfumu yaikulu Chikowi m'boma la Zomba.

Wolemba-Francis Maonjera_Balaka
http://mwasweradaily.com/2023/11/22/ndipitiliza-kuyimba-nyimbo-zosiyanasiyana-sindizo/

Photos from Mwaswera Daily's post 21/11/2023

TIGWIRIZANE CBO ON THE MOVE

A local organisation known as Tigwirizane Community Based Organisation (CBO) which is located at Village Head Mpanje, Traditional Authority Mlumbe in Zomba district on Friday 17 November, 2023 held the meeting to review its developmental projects in which the organisation is undertaking in the area.

In his remarks, Dalitso Muronya who is the founder and Chairperson of the organisation said that the meeting involved local leaders to voice out their views on the projects that the organisation is implementing in the area.

"The meeting was organized in order to provide the chance to local leaders to review the first month's project activities, to foster collaboration, and advocate for national unity in development towards Malawi 2063 and sustainable development goals," said Muronya.

He explained that his organisation is implementing several projects in the area including; Plastic Pollution Free Zomba Initiative, Community Clean-up, Nyasi Mayazi Movement, Bee-keeping, Women's Innovation Clubs, Mwandama School Feeding Program, Environmental Conservation, Child Care Centers, and Governance Programs.

On the similar development, Tigwirizane CBO is working in collaboration with other organisations in the area through partnerships in order to address different challenges.

Meanwhile, the organisation has appealed for more support from well-wishers to donate materials and learning equipments.

"We invite the public to support our Children Based Care Center and Learning Hall project by donating materials and learning equipment. They can Contact us at +265994963141 or [email protected]," Muronya expressed.

According to Muronya, TIGWIRIZANE CBO is a youth-driven organization which empower communities by promoting the youths, women, as well as rights of people with disabilities. The organisation started its operations in 2014 then it was fully registered in 2017.

Reported By Francis Maonjera
http://mwasweradaily.com/2023/11/21/tigwirizane-cbo-on-the-move/

21/11/2023

Why Malawi?πŸ˜­πŸ’”

Tunisia 1
Malawi 0

Timati ZAMPILA Sananyala πŸ™„πŸ™Œkoma zafikapa kusanyanyalako kugatheke bwaji?

Za GABA PANO ai pls

21/11/2023

Mavenda mu Limbe mu mzinda wa Blantyre kutidzimula a city patrol mwa equality ndithu mpaka athawa

[MP3]Ngwazi Jonathani-Zeze ndi Dorothy - Mwaswera Daily 21/11/2023

New Music alert

Oyimba kukhala Ngwazi Jonathan title kukhala Zeze ndi Dorothy.

Ngwazi Jonathani-Zeze ndi Dorothy

Download hereπŸ‘‡πŸ‘‡
http://mwasweradaily.com/2023/11/21/ngwazi-jonathani-zeze-ndi-dorothy/

For upload whatsapp +265881705779

[MP3]Ngwazi Jonathani-Zeze ndi Dorothy - Mwaswera Daily Ngwazi Jonathani- Zeze ndi Dorothy | MP3 download

21/11/2023

"Amene akumudziwa mnyamatayi, akunena kuti dzina lake ndi Chancy Banda, akuti kumudzi kwawo ndikwa Mphikapika , ngankhale dzina lamudzi sindinalivetsetse chifukwa chamalankhulidwe Ake. Uyuyu is admmited pa Nkhotakota District Hospita, ward yazibambo. Komano m'bale wake kapena guardian alibe kuno kuchipatala komano akuoneka mentally disturbed! Please amene akumudziwa awuzeko azibale ake amupeze kuchipatala ku Nkhotakota DHO. Zinthu zambiri zikumuvuta ngat kudya, kusamba, komaso kuyenda! Zikomo"

Joseph Nkasa

21/11/2023

Kit master wa Tunisia wagwela pa lingazi river amalowela ku Bingu.

Confirmed yalelo tawina ndithuπŸ˜†πŸ˜†πŸ™Œ

Mabedi ndinyamuleπŸ˜…πŸ™Œ

Want your business to be the top-listed Media Company in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

Kuyankhura Kwa Bon kalindo pa zionetsero zomwe zinachitika mu mzinda wa blantyre ati kudana ndi kuti a city council azil...
Wachikwapula chi ThuminitsiStrongingo ft Jay Jay Cee Watch full video here #MwasweraDaily #Mwaswera
Mavenda mu Limbe mu mzinda wa Blantyre kutidzimula a city patrol mwa equality ndithu mpaka athawa#MwasweraDaily #Mwaswer...
Mavenda mu Limbe mu mzinda wa Blantyre kutidzimula a city patrol mwa equality ndithu mpaka athawa#MwasweraDaily #Mwaswer...
Tione ozisata filimu yanji ili musimoπŸ™„Komwe waphela zakekoπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚Umhu  mwaswela bwaji kulikose muliko🀣🀣🀣🀣
Saint-Realest Anagwira munthu pakhosi komaso kumupasa ma kick akuti kukwiya ndi kuluzakuπŸ™„Zambiri mu video iyiπŸ‘‡#MwasweraD...
Es Pee Manyazi ft Wikise & Kenlo (snippet )
Ongoing cyclone Freddy crisis(Southern Malawi)march 2023
Malawi southern region flooding crisis (cyclone Freddy)

Telephone

Address

Lilongwe
Other News & Media Websites in Lilongwe (show all)
NewsDay Malawi NewsDay Malawi
Sector 2, Area 47
Lilongwe, 207247

NewsDay Malawi is your news; political, entertainment, music and fashion website from Malawi. We pro

Chap-Gee Chap-Gee
Mchenga Street A49 Baghdad
Lilongwe

Its all about music..

Magodi Magodi
Area 23
Lilongwe

NO NOISE GANG

Twepol The Dancer Twepol The Dancer
Lilongwe

Break dance videos

Bweka Bweka Investments Bweka Bweka Investments
Lilongwe

A home of story telling and a business centre ,buckle up.

Malawian Patriot News Malawian Patriot News
Chidzanja Road
Lilongwe

_Vacancy, military training,border patrol, peace keeping mission+ to our citizens/May God blessπŸ‡²πŸ‡ΌβœŒοΈ

Malawi Infotainment Site Malawi Infotainment Site
Lilongwe

Platform Where You Get informative Content, Current affairs & Entertainment News Promo 0997656111

SCORE MW SCORE MW
Lilongwe

Home of Sports News (local and International )

Drip masala Drip masala
Lilongwe
Lilongwe, MUSIC

NEW PAGE MUSIC DRIP MISALA

J-max music J-max music
Mitundu
Lilongwe

THEKA Connections THEKA Connections
Area 43
Lilongwe

WE RUN MUSIC PROMOTING @ AN AFFORDABLE PRICE #THEKAconnections