TrendTunes Malawi

TrendTunes malawi is a media and entertainment company
0999648453 / 0880173316

JAVA - PERFOMANCE ON REAL VOICE SESSIONS 30/06/2024

Zayambika ku seleku watch JAVA PERFOMANCE at Real Voice Sessions

https://youtu.be/sI8m0r05k_o


City Shots Pictures

JAVA - PERFOMANCE ON REAL VOICE SESSIONS For Booking / Advertising 0888920778 , 0992852122 , 0886815136

30/06/2024

now Soja wapitanso💔

29/06/2024

With TrendTunes Malawi – I just made it onto their weekly engagement list by being one of their top engagers!

29/06/2024

Thanks for being a top engager and making it on to my weekly engagement list! Manzo Kay MW, Harry Chathengo, Fley singa

29/06/2024

Apa Silver Strikers FC yapanga sign Malinga Mafia and Lulu & Mathumela Band as ma ambassador a team...

Moto wake

28/06/2024

Watidzutsanso ndi moyo. alemekezeke wamwambayo

25/06/2024

R.I.P Mr Mwenya 🕊

25/06/2024

zubwera uku mudabwa ask Kauden de producer and Sheriff Crackmapiri Mtuwa

24/06/2024

KHALA SINGLE KUTI MASIKU A MOYO WAKO ACHULUKE🥸

24/06/2024

Malawi na Zambia... BICC 17 AUGUST uku akukhalayo zake

24/06/2024

Mau amodzi okha omupatsa chilimbikitso super star KAY LUXE 0904 ambir mumamudziwa ndi ma comedy a EX pa TIKTOK.....

24/06/2024

"Do the best you can until you know better. Then when you know better, do better."

24/06/2024

Ma female artist ambir kumalawi kuno amati akalowa mu music industry nthaw zambir amangotchuka pa social media bas samakwanitsa kufika palipose like muma Tv, Radios Etc

Kodi zimenez tizit chimachititsa ndichani??

Ife titafatsa tapeza k*t vuto ndima sponsers, ma producer

Chifukwa akangova nkaz ali bwino amamuuza amupange sponser en then amathera pa fb, tiktok, whatsapp ndima platfoms ena. Kod nanga anthu amene sali pa social media angadziwe bwanj??

Apatsen malangizo atsikana amene ali ndi lunso loyimba k*ti managment timaifufuza kaye tisanavomere.


Osaiwara kupanga share komanso invite this page.

24/06/2024

Big shout out to my newest top fans! Matiya Banda

22/06/2024

Uyuso akubwera ndi inayake kuseliku..... Zanyimbo

Photos from TrendTunes Malawi's post 22/06/2024

Congrats ma guys

22/06/2024

uMakhadziwo kuusiya pambari umumu muli mwex tu 🙊

22/06/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Taibu Muhajili, Stonard W Gostino, Gift Kamwendoh. , Max Shado, SpÄrøw Før Rëål ÑkhøMä, Elias Emilio Saize, Geofry Phiri Gasper, Syless Paul, Lovemore Kolope, Chifundo Precious Mzozoma, Lodwell Mac Donald, Ñîtrö Lègèñd, ɭɭ MBÃŁĔŽ ɭɭ, Chisper Madiness, Bruno Goveya, Chriscent Crist Chimphepo, Mfitizalimba Jnr, Frêsh Mitøma, Tina Tilulo, Samwel Kimani, Eckson Msulila, Emmanuel Shata Chimseu, Vinicent Nevason, Priñçe Wâ Bâñdâh, Renient Michongwe, Maxwell Maxwel, Eneless Zachuluka, Lonjezo Simeon, Joseph Chigalu Henderson, Alex Maxie, PHÏLL PÏÑÆH, YOUNG JOF G MW, Pierre Claver Ba, Enock DK Mvula, Starbay Sinoya, Noshipa Jere, Emmanuel Mbambo, K Hanz MW, Emmanuel Kandapako, Lister Baib, Chumankhuku Jo, Davie Paul Charles, Honest Thomas, Buddy Mpalume, Violer Char, Bebe Shãñêl, Kondwan Banda, Kenzo Padana Moyo, Zakeyo Tadeyo, Gloria Kafunga Hildah

20/06/2024

+265 886 81 51 36 whatsapp

16/06/2024

BLAZE yodella - Kumwamba (tribute to the fallen loved ones)
link in coment box

for upload 0994481550

16/06/2024

BLAZE yodella walira pa nyimbo yake a new called KUMWAMBA yomwe akulira onse omwe atisiya munyengoyi

link in coment box

trendtunes malawi

16/06/2024

Area 36 kuli ma guys awawa.... eee Swizz Martin Mwangonde komanso ka nfana aka ka Saviour Artist

muli maimbidwe umu



trendtunes.malawi.kesug.com
0994481550

16/06/2024

for music upload 0994481550 osaiwara leronso tikupanga upload ndi 800 kwacha yokha pangan machawi

15/06/2024

Today tikupanga upload nyimbo pa ntengo wa 800 kwacha okha basi.... for upload 0999 64 84 53 0994481550

15/06/2024

Kuno Ife Tadzuka a thazi.. inu bwa

14/06/2024

FOR UPLOAD 0994481550
ONLY K1000 PER SONG

TrendTunes Malawi

03/06/2024

W***Y SIZ
BLAZE
JKB MDUDS
ELAINAH
....title.... Loading................

01/06/2024

kupatula kukhara ndi ntima okonda anzake ndi otha kucheza munthuyi alinso ndi nzeru...... congrats madala..

" Bye Bye Rent " - Gibo Pearson ali ndi chimwemwe pamene wakonzeka kukalowa nyumba imene wakhala akumanga. Nyimbo zamupindulila Gibo 👏👏

Giboh Pearson Phalombe Musik

17/12/2023

Katswiri oyimba nyimbo za amapiano Zeze Kingston komanso m'modzi mwa amayi omwe amatsatidwa ndi anthu ambiri pamasamba amchezo Dorothy Shonga, lero apanga ukwati wawo.

Awiriwa apha mbota zododometsa zomwe anasintha koposera kawiri.

Malingana ndi ma video a ukwatiwu omwe afala pamasamba amchezo, awiriwa pomwe amayenda kulowa malo ochitikira mwambowo anthu ena amakuwilira mkumati: "Eyo tiyeni!, Tiyeni!"

Napo pamasamba amchezo anthu anapeza zokamba. Susan Symon Longani ataoni zovala za ukwatiwu patsamba lina anati: "Eee za anthu a ndalama izi, ma outfit mbambande."

Naye Jesca Chinombo Hilalio patsamba lomwelo anagoma: "Koma tiona mphasha lero."

(by Innocent Kumchedwa - Lilongwe:12/17/23)

Want your business to be the top-listed Media Company in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address

Lilongwe

Other News & Media Websites in Lilongwe (show all)
NewsDay Malawi NewsDay Malawi
Sector 2, Area 47
Lilongwe, 207247

NewsDay Malawi is your news; political, entertainment, music and fashion website from Malawi. We pro

Chap-Gee Chap-Gee
Mchenga Street A49 Baghdad
Lilongwe

Its all about music..

Magodi Magodi
Area 23
Lilongwe

NO NOISE GANG

Twepol The Dancer Twepol The Dancer
Lilongwe

Break dance videos

Bweka Bweka Investments Bweka Bweka Investments
Lilongwe

A home of story telling and a business centre ,buckle up.

Malawian Patriot News Malawian Patriot News
Chidzanja Road
Lilongwe

_Vacancy, military training,border patrol, peace keeping mission+ to our citizens/May God bless🇲🇼✌️

Malawi Infotainment Site Malawi Infotainment Site
Lilongwe

Platform Where You Get informative Content, Current affairs & Entertainment News Promo 0997656111

SCORE MW SCORE MW
Lilongwe

Home of Sports News (local and International )

Drip masala Drip masala
Lilongwe
Lilongwe, MUSIC

NEW PAGE MUSIC DRIP MISALA

J-max music J-max music
Mitundu
Lilongwe

THEKA Connections THEKA Connections
Area 43
Lilongwe

WE RUN MUSIC PROMOTING @ AN AFFORDABLE PRICE #THEKAconnections