Heaven Promotions
Strictly for entertainment business and this is an Eastern Region Music outlet..
Kungopeza ma messages mu foni bas ati chatha, kungochedwa mwamuna kufika pakhomo basi tu akaziwo Ulendo aah kumaupeza mtima.
"Roick Ress" walakhulira azibambo onse munyimbo yotchedwa ULENDO yomwe waswa ndi D_20$MangochiD_20$MangochiD_20$Mangochi komanso walimbikitsa kuti zithu zikavuta osamafooka.
Check: https://www.reverbnation.com/chowepodcastmusiccom/song/34675983-roick-ress_ulendo_ft_d-20
Dzuwa ilili wina atengera nalo Matenda π€§
Hayee Hayeπ
Nyimbo zaChiyao zidayamba kalekale koma awiri awa Atoht Manje & WalyCriss adaiponyera level inaπ.
Continue Rest in Peace Makosanaπ
Oyimba dzina lake ah thoko /yark negro watulusa kanema wa nyimbo yake yomwe akuitcha ndizibwela
https://www.youtube.com/watch?v=83XsVS9g3Vk
Komatu zambiri zikuchitika kunja kuno, Tipwetekanaπ
Panopa mu Johannesburg muli mziii, a Malawi onse ali m'nyumba zawo.
Sikuli bwino eeh
Happy Birthday Afro Dancehall Lil kellz
Wagwetsa nyimbo yatsopano "2FA Challenge"
https://youtu.be/Ao1KjbjmnfI?si=4Y_K8rzwGm4BonhB
Who are the rising artists in your area deserve the 2024 Music Awards??
Ndi oimba uti kudera lanulo yemwe wachilimika akuyenera katundu uyu chaka chino ?
Mwezi wa October, Veteran Naxykid of Zongaza Muzik akutulutsa nyimbo yatsopano.
π₯
Zinthu ngati izi zimasowa ndipo mwai ukapezeka pangani nawo ndithu.
Kwakonzedwa "Tchena Tikacheze Pakapinga" yomwe ikuitana nonse omwe muli pachikondi ngakhalenso omwe muli single kukhala ndi nthawi yabwino ndi moyo wu. Tsiku ndi Sunday pa 13 October , malo ake ndi "Love Garden" zochitika zonse zikuyamba 2pm mpaka 6pm.
Kuzakhala kudya ndikumwa kumeneko komanso ma dance mkati pati, nkhani yaikulu ndikuupepetsa moyo wu bas. Tawaimbireni or WhatsApp omwe akulongosola pa +265 885 63 77 87
Nsanje si Umuna , mwana uyuyu Greazy Moh Ndamooh ndi nyimbo yatsopano wagwetsayi ndithudi achina Burna Boy amusilira kwabasi eeh π₯π
Mutu wanyimbo "Alhamdulilla" , tiyen tumupase tikaonere ku YouTube konko https://youtu.be/Lkb_G_hbIek?si=GBnKd_ki9NSRyb5h
Anthu ena akusokoneza nkhani...
Mwezi watha Dan Lu adalephera kupita ku Convention ya DPP popeza anadwala mwadzidzidzi , ndipo mwezi uno wayamikira MCP pazitukuko zomwe akupanga.
Apa mwamvetsa eti ?? πββοΈ
Mutangothetsa chibwezi iyeyo amvekere ππ
Nthambi yoona za nyama zakuntchire mdziko la Zimbabwe yati ikuyembekezeka kupha Njovu zokwana 200 ngati njira imodzi yothandiza anthu omwe akuvutika ndi njala mdzikolo.
Bola anzathu, ku Malawi kuno njala yo itafika penipeni tingatani ?
Omwe tidabadwa nthawi ya katundu uyu, tatchulani filimu imodzi yomwe munkaonera ?
π
TK Entertainment yapanga sign Favore & Lamah ndipo lero akumana ndi Sife , team yonse yakunganaπ₯βοΈ zili ku studio eeh kwachema.
Osamadandaula ngati nyengo zanu sizikuyenda bwino, chifukwa chithu chomwe Mulungu adati azapanga painu ndichanu basi, olo ena akukhomeleleni ndichanu basi.
Manager & Producer wa Bandera π Yungcon π₯
Ntchito bwana mukuigwira π
Osamapanga zithu mwachizolowezi kuti nyimbo zabwino koma ujayu anatchuka kale uja mmmm tamverani luso lomwe lili mu Ghetto.
Uyu dzina lake ndi REAMO 265 dzulo wadropa "TINA EP" koma akulu akulu ππ₯
Check the first comment π
"Ndli ndi plan yotulutsa nyimbo yomwe ndaimba ndi artist wankulu ku Malawi kuno,, komano page yanga yomwe ndnali ndi ma followers ambiri idasowa nde ndatsegula ina, ikangokwana olo 2K ndithudi ndigwetsa Bomba" - Greazy Moh Ndamooh watsindika.
Mwana uyuyu muli luso eeh π Check the first comment π
Bungwe la National Water Resources Authority lalangiza anthu omwe anakhuzidwa ndi vuto lakusefukira kwa madzi m'boma la Mangochi kuti asabwerere msanga m'madera omwe munakhuzidwa ndi madziwa pomwe pali chiopsezo chakusefukiranso kwa madzi maderawa nyengo ya mvula ikubwerayi.
Mkulu wa bungweli Engineer Dr Dwight Kambuku ndiyemwe wanena izi pomwe watinso mulingo wa madzi Nyanja komanso mitsinje ikulu-kulu ya mdziko muno ukuyembekezeka kukwera kuchoka pa 477.0 cubic metres kufika pa 477.22 cubic metres pofika pa 1 Desembala chaka chino, zomwe zikusonyeza kuti madziwa akwera ndi 22 cubic metres ndipo
malinga ndi bungweli ndi mlingo wokwera kwambiri
kuyerekeza ndi zaka zambuyomo.
Komatu anthu sakugona eeh πKing Jodamu wakumananso ndi Nepman ku South Africa ndipo akujambula video ya nyimbo yomwe adaswa ija "Money"..
Link ili bokosi mo, muimvere π
Finally, New Music Video π¬ Lil kellz "Changa Ndi Changa" π₯
Mwana uyuyu akulimbikira kwambiriπ
Check: https://youtu.be/CKxtNjOvLqI?si=cgFg5A_Ivf_B48qP
Andale ena m'boma la Mangochi ati anthu ochita business wa Kabanza achoke kamba koti samavota nthawi yazisankho popeza ambiri mwaiwo si am'bomali.
Wandale yu yemwe wakana kuzitchula dzina watinso town yi sikukongola ndi anjinga komanso zikupereka ulesi kwa anthu kugula galimoto zawo zoyendera.
Simmene kulili, eti inu mukuona bwaa?
Congratulations Bandera music pamene Video yake "PA Home" yafika 100 Thousands Views pa YouTube pa miyezi itatu.
Rising artist kufika apapa simasewera.