Freedom Fighters of Palestine in Malawi

We are here to discus Freedom of Palestine,and other Islamic state that suffer from

08/11/2023
30/10/2023

Dziko lapansi silikuonongedwa
Ndi athu
Ochita zoipa ayi.
Dziko lapansi likuonongedwa ndi athu abwino amene amangokhala chete pomwe athu oipa akamaononga Dziko.
SAVE PALESTINE đŸ‡ĩ🇸
PROTECT PALESTINE đŸ‡ĩ🇸
PRAY FOR PALESTINE đŸ‡ĩ🇸
SPEAK ABOUT PALESTINE đŸ‡ĩ🇸

28/10/2023

America imalimbana ndi maiko ang'ono ang'ono ,
Onani America yatumiza asilikali ndi zida zawo za Nkhondo Ku Palestine.
Akuthandiza ma Israel kupha ma Palestine.
Ngati America ili ya phavudi bwanji sinatumize asilikali Ake Ku Ukraine kuti akagonjetse Russia.
Bwanji America imalimbana ndi maiko ang'ono ang'ono powonetsa phavu zawo bwanji sangalimbane ndi North Korea or China.
Palestine athu woti alibe zida zikwanira koma akumenyana ndi maiko woti ali ndi zida zoopsa za Nuclear.
Muthu amene amawonesera mphavu zake kwa ana ang'ono ang'ono woti si sayezi yake ameneyo si Muthu woti aziopedwa.

28/10/2023

Kusapota athu amene akuzuzika sikutengera kuti,
Akuzuzikayo ndi ndani?
Amachokera kuti?
Komanso ndi wa chipembezo chiti?
Zimangofuna kuti ukhale ndi umuthu wokonda Mulungu ndi zolengedwa zake.

24/10/2023

Ndizovetsa chisoni komanso zolilitsa kuona athu ena omwe sakuziwa history kumamena kuti ali pambuyo posapota ma Israel omwe akupha ma Palestine to Gaza
Tiyeni tibwelere mbuyo pang'ono tione mbiri ya ma Israel yomwe athu ena omwe sakuziwa history ya athu amenewa.

Adolf Hi**er atasakhidwa kukhala Chancellor wa Dziko la Germany adayamba kupha ma Jews onse amene lero muwatcha ma Israel,
Ndipo atafunsidwa ndi antolankhani iye anayakha kuti,
Ndikadakondwa ndikawapha ma Jews onse Dziko lapansi koma ndikusiyirani.
Ma Jews ochepa kuti kusogoloko muzazindikire chifukwa chimene ndikuwaphera athu amenewa.
Mchaka cha 1945 Nkhondo yonse ya pa Dziko lapansi itatha.
Mu chaka cha ma 1946maiko a ku Europe anawathamangitsa ma Jews ndipo mothandizidwa ndi Rothschild family athuwa anapita ku Palestine kukapepha Malo.
Ndipo ma Palestine anawapatsa athu amenewa malo okuti ankangokhala.
M***a kumamena kuti athu amenewa ndi ana eni eni a Izaack zomwe zili za bodza.
Ana eni eni a Izaack mibadwo ina ndi yomwe ili ku Ethiopia.
Israel imene mukuiona leroyi inachita kupangidwa ndi maiko a Europe ndi America mothandizidwa ndi Rothschild family.
M***a kumadabwa kuti Kodi eni Ake a Dziko la Israel omwe ndi ana ena a Izaack Ali kuti.
Funso limenelo tiyakhabe .
Koma panopa timangofuna tikuziwitssni zoona zeni zeni zokhuza Palestine and Israel.
Ndi momwe Israel ya leroyi inabwelera ku Middle East.
Mau ofunikira kwambiri ndi omwe ananena Adolf Hi**er.
Ndikusiyirani athu ena pang'ono kuti kusogoloko muzazindikire chifukwa chimene ndikuwaphera athu amenewa.

29/01/2023

Sukuyenera kukhala mwenye , kapena msilamu pofuna kusapota ma Palestinians omwe akuzuzidwa pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku.
Zingoyenera kukhala ndi umuthu.
Palestine #
occupation in Palestinians land #

29/01/2023

PALESTINE UFULU WAKO UZALANDIRA LITI?
😭😭😭😭😭😭😭😭

12/02/2021

Mtendere ndi madalitso zochokera kwa Mulungu zikhale kwa inu nonse awelengi a page ino,
Chinde mutikhululukire tatenga nthawi yaitali kubweranso pa Facebook kamba koti tinapangidwa ban kwa miyezi ,
Komabe tabweranso ndipo tikamba choona kuti chilungamo chiwoneke zikomo

Want your business to be the top-listed Media Company in Johannesburg?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Videos (show all)

Telephone

Address

Johannesburg
Other News & Media Websites in Johannesburg (show all)
ITNewsAfrica.com ITNewsAfrica.com
20 Woodlands Drive
Johannesburg, 2198

ITNewsAfrica.com is Africa’s premier ICT News and Information website.

Moneyweb Moneyweb
No 5, 8th Street
Johannesburg, 2198

Moneyweb is a trusted source for business and investment insights.

Pro-Afrikaanse Aksiegroep Pro-Afrikaanse Aksiegroep
Johannesburg, 2191

Klik links onder om u vriende te nooi om van diÊ blad te hou! Ons bestaan as taalorganisasie reeds sedert Februarie 2000 & publiseer nuus, menings & boeke.

Xbox360Gamer Xbox360Gamer
Northriding
Johannesburg, 2169

http://www.xbox-360.co.za

Luxlife Luxlife
Johannesburg

Luxlife is a niche lifestyle community. Look out for new services launching soon.

Yasin Arafat Yasin Arafat
Johannesburg

āĻ†āĻŽāĻ°āĻžāĻ‡ āĻļā§‡āĻˇ āĻœā§‡āĻ¨āĻžāĻ°ā§‡āĻļāĻ¨, āĻ¯āĻžāĻĻā§‡āĻ° āĻ•āĻžāĻ›ā§‡ āĻāĻ•āĻœāĻ¨ āĻ¸āĻ¤ā§āĻ¯āĻŋāĻ•āĻžāĻ°ā§‡āĻ° "āĻŽāĻž" āĻ†āĻ›ā§‡āĻ¨ āĻ¯āĻžāĻ° āĻ•ā§‹āĻ¨ āĻ¸ā§‹āĻ¸ā§āĻ¯āĻžāĻ˛ āĻŽāĻŋāĻĄāĻŋā§ŸāĻž āĻ¨āĻžāĻŽāĻ• āĻ†āĻ§ā§āĻ¨āĻŋāĻ•āĻ¤āĻž āĻ¨ā§‡āĻ‡!❤ī¸

LiMari Louw LiMari Louw
Johannesburg

RSG-aanbieder LiMari Louw se amptelike Facebookblad Insta @limarirsg

Mzansimagicofficial Mzansimagicofficial
Johannesburg

south africas greatest soapies

Ceekay Ceekay
Dlamini
Johannesburg, 1233

him

Sports Corner 2.0 Sports Corner 2.0
Johannesburg, 2065

Football Updates

Amini News2 Amini News2
Johannesburg

Amin news area

Tshephang Matsemela Tshephang Matsemela
Johannesburg